Mulungu adatipatsa ndithu mpulumutsi wa dziko la malawi ndiye Peter muthalika koma unkhutukumve ndikukomedwa ndi amabodzawa kudatipweteketsa koma osadandaula abwezeletsa adad apatseni mavoti ❤❤❤❤
Ooooh my prayer is God give him long life Peter Muthalika kuti 2025 mupulumuse dziko la Malawi kuzera mwa Peter Muthalika chonde Ambuye mupaseni moyo wautali 👏👏👏👏👏👏👏👏🧎🧎🧎🧎🧎
Please 🙏 adad come to help your beautiful peoples 🙏 we need you pls 🙏 this 💯 government is nonsense government 🙄 chakwera walephera kuyendedza dziko la Malawi 🇲🇼 bas 🇲🇼
Smartmatic will not work. Chimenechija olo achikakamile a MCP,, sichigwila .. Wait and see The whole information they have already embedded in it, is going to be erased and they won't even understand.. Just wait and see 😂
Apaseni Džko awa bas❤❤❤❤ Džko limawakala adad
Awa ndi amfumu osati chakwera kuthako sete zilithooooo
Aaaa mudziweni yesu
When we say aDad we really mean it❤😊
Km peter ndi akatundu, boma ilo APM MY VOTE 💙💙💙 y
Please God help this Muthalika to take us out of this terrible economic crisis that we are facing right now
Kwa anthu amene akonda dziko lawo kut lipite pasogolo ayenena kunga zapot kwa adad ndamene amakwaniza kunsiza katundu okomela amalawi please votela adad
May God continue bless peter muthalika ❤❤❤❤❤❤
@@RobertNedsonamen God please
Nanga ife kunalibekotu ukuuuuu tikanapitako nanga
APM MY VOTE ❤❤❤❤
Pali athu ena anangobadwa ndi chin'dalitso monga ngati adadi inuo ndi chiyembekezo chathu ndipo osalola kuti akubeleniso iyayi✔️💞💞💞💞💞💞💞
ndipo live
Mbambande chi team icho
Mulungu adatipatsa ndithu mpulumutsi wa dziko la malawi ndiye Peter muthalika koma unkhutukumve ndikukomedwa ndi amabodzawa kudatipweteketsa koma osadandaula abwezeletsa adad apatseni mavoti ❤❤❤❤
😅😅😅Hehe he ana agogo mwagundikatu UTM my vote ❤❤❤❤
@@LinlyMathewezako izo dpp my vote heeeee boma ili likudza Chaka cha mawali wow dpp ooooeeeeeeeeeeeee
Ooooh my prayer is God give him long life Peter Muthalika kuti 2025 mupulumuse dziko la Malawi kuzera mwa Peter Muthalika chonde Ambuye mupaseni moyo wautali 👏👏👏👏👏👏👏👏🧎🧎🧎🧎🧎
My vote pitala mose uja uyuu winayu iii
Uku simungapezeko nyawu or imodzi mzambuye izii
Good luck🎉
Chisale osawasiya adad umakwana ❤❤❤❤❤❤❤
Pangoline wa malawi 💙💙
Boma iloooooo my vote❤❤❤
Nyada mai nyada mai 😂😂😂😂apita woyeeeeeeee
You will win
Our vote ☝️☝️☝️☑️☑️☑️
Mulungu akutisungila APM ndicholinga 🎉🎉🎉🎉❤❤❤my vote I Iove APM ❤❤❤❤
Adad awoo more 🔥 more 🔥 kuti buuu BOMA lathu anthu ilo we love you dad❤
Chakwera, ndi gulu lake anutsegula mmimba mwamagazi lero.
Lero ndachiona Chifukwa chomwe Chakwera akukakamila Smart Matic
Kodi iwe sumadziwa iiii 😂😂😂 mantha mesa akumuchititsa mantha APM....!!!!
Please 🙏 adad come to help your beautiful peoples 🙏 we need you pls 🙏 this 💯 government is nonsense government 🙄 chakwera walephera kuyendedza dziko la Malawi 🇲🇼 bas 🇲🇼
Apm long bas ❤
Koma vuto ndiloti anthu onsewa alowesedwa kale mu smartmatic avotera kale MCP 😢 😢😢😢 adad try your best to rescue malawian
Ambuye akusamalireni nthawi zonse
We together ADaD ✊✊
Amalawi tiyeni tivotere muthalikayo basi ,hopefully better ❤
Boma !!!!!!!!!!!!!!!
Person blessed with leadership
Smartmatic will not work. Chimenechija olo achikakamile a MCP,, sichigwila .. Wait and see
The whole information they have already embedded in it, is going to be erased and they won't even understand..
Just wait and see 😂
Thus for real bro, Ana achepa 😂
Munthu owopa MULUNGU ndi ameneyu not mbava ija komanso WAKUPHA uja Chikangawa APM my future my vote ❤🎉❤❤❤❤
Ambuye akusungeni bwana Apm
My vote Apm
❤❤❤❤❤❤our own pangolin boma ilooooooooo
🔥🔥🔥🔥That's adadie
Apm is man of ability a leader not a politician
Boma ilooooooo,,,,,,,,
Boma iloooo❤❤
Komatu izizi izi! Wina agwa ndi BPP sure
Shaaa fuel crisis pati magalimoto mbwe. Kuvina Kuiwala njala, Koma Amalawi.
My president
Uyu ndi tsogoleri osati zinazi
Zili bwino ambuye awapatse moyo wautala ndikuti skhale bridge yoolotsa a malawi
Boma ilooo🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Adad boma Peter muthalika osazaphwekesa
Amec akutuluka 😂😂😂
Bomaaa iloooooo ❤❤❤❤
My father my father ❤❤❤
Kkkkkk mwagwilako dzanja la apule
Mix Pa home group 😂❤
Boma ilo apm my vote adad timakunyadlan
Apo olembawo akukhala ngati aulemu coz aona kt amene akulembetsayo ndimunthu wamkulu
Olo atabera mavoti motani Peter akuwina basi
kodi ndikuberakonso zitheka! when Jesus say yes, no body can say no.
@@lameckjulius5440 you are right if Jesus say yes nobody can says no
ndiposo palibe kuponya ma vote angonyamuka waku state house
Boma❤
Katundu amene boma silikugona nalo tulo ,nde ndi piter mthalika ana omwe kwawo akadafuna makpe
Utumiki ochokera kwamulungu uyuuu osati zinazi zawakanika anja awasiile adadi
Nde azituluka daily bwanji aaaaaaa ,,,wina athawa ku state house😂
kkkkkk mangaya ndamudusa ine pa lunzu ndikupita ku mwaza koma ndikuferanji chabe mayi asikono siandare ndi adzeru kuposa bambo monga muziwira😂
Mfumu ya dziko iyi😂😂
Peter mutharika woyeeeee
Kokalembetsa tidziyenda ndi mipando, wobvota ndi wobvoteredwa pali distance yayikuludi
Tapangani za machine
Kwachema❤
Uyuyu ndi president wa Pfuko la MALAWI straight
❤❤❤❤❤
Boma ilo adad oyee
Apm machinery
Chipani chozachivotera ndiye ndichimenechi
Awa ndioti analamulapo ndipo zitchiyo zao zikuziwika kuona Ali ndikoka athu akusata khalidwe lao olo mutawauza kuti wakalamba zikungolowa khutu ili kutuluka linalo awa namuna olengedwa ndimulungu opand Zina laubusa koma oyenda muchilungamo
Lembetsani mwina tione Zina
Eeeee km ine ndikudandaula kamba ka smartmartic basi
Osaopa akulu mulungu wa Abraham yokobo ndi Isaak akuona momwe dziko lafikila pano
Eeeee koma chisale anamvela kuwawa adad eeee
Mutharika walowa kale mu 18 yard box tingodikira 2025 kuti aike mpira mu ukonde basi
Osaiwalatu smartmatic 😂😂😂Koma apa olo kubelako ayambira pati?
My vote is for APM
Muthu waMulungu uyu wosati awawa uuuuuu
Munthu wamkulu kwambiri.
Adadi❤❤❤❤❤❤
Dpp ❤
Boma iliooo💙🧢🧢🧢🧢
❤
My vote APM
Eeee koma chisale adad anamvela kuwawa
Ineso ndaona choncho😂😊
Chisale safuna wina azimutosatosa APM😂😂😂 zachibwana amakana Chisale
😂😂chisale zachibwana sapanga nawo 😂😂
Boma ilooo🎉
My vote. DPP❤ munthu odalitsidwa ndi Mulungu amaoneka❤❤
Kodi machine amenewatu sazagwira ntchito ndipo aboma angotaya nthawi yawo padera tikudziwa kuti akuopa milandu komatu azakalowabe
Thandizo lathu lokhalo lopezekelatu
Professor
Adida
Our hope
Odiiiiiii ukooooooooo
Anthu amatsutsika mmitima Yao chifukwa chosankha molakwika, lero Peter angolondedwa ngati ngumbi APM woyeeeeee moto kuti buuuuuuuuu mulera khungwa wathu
Kodi mukuziwa Kuti chakwera wapeleka mimba 😂😂😂 chakwera amakonda dog style
Live 😅
Palizina zimakhara zochokera kwamulungu osamakakamira zinthu achakwera mupezezeka mwagwera nazo ku chimphompho ndithu
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
President koma uyu, osati boma linasowetsa SKC, aaaaaa
Apm my vote