Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Remember to subscribe ❤
Hie
I'm frank jambulani from k.u. Namadingo nikape.
Title ndizomwe mukulongosola apa sizikupeleka sense collaborations ndikukanganilana malo zinthu ziwiri zosiyana
Don't forget skeffa chimoto as well brother man keep it up
Ankulu apa palibe chomwe chikumveka muzangoyambanitsa anthu😂😂
Palibe iwe suzitsata khala phe yabaya is the hit corab with zambia whether u like or not
@@moosathomas6440 vuto kumva nd kumvetsetsa nd zindu ziwili zotsiyana inu mveranitso kawiri chomwe mutatolemo mundiuze
@@moosathomas6440 I didn’t say is not hit bra Km nkhan ndyot chanzeru mulibe mu video yi🙌🤣
Palibe chomwe chikumveka zikuoneka ngati mukufuna zoti anthuwa adane
Kkkkkkkkkkk and wanena kale kuti anthufe ndipachibale,,,wakhuta mbatata uyu
Yeah
Man mumatimvetsa kukoma zed koma please mutifufuzileko zomwe zinadanisa Diamonds plutnumz ndi Harmonize
Pali ubale wawukulu chabe osat kulimbirana malo
KWakumalawi kukayimba ku zambia winaso ndikukayimbaso sikuti ndikulimbilana
Duwa and Yabaya nyimbo izizi zivuta
Mukufuna tiphunzilapo chani apa? Kapena nkhanizo yeniyeni ndi iti?
Kkkk kayatu other wise ma artist amadana
Inenso ndi organized family
Muyenela kudziwa kuti Zambia ndi Malawi timayakhula chichewa ndipo ndife amodzi muzonse
Inu palibe chikunvekapo apa
Asam,penatu mumatibalalitsatu man
Kod inumukufuna chan
Uhuru zambiata
Fantastic
Ndinu opasula
❤
Skeffa ndi daliso
Eli njuch ndapaya
Koma don't compare Eli with doc Eli wachepa
Tatiuzeni zanzelu abale
Skeffa nayenso dolo
🔥🔥🔥🔥🔥
Mmmmmm

K
Wakumalawi kukayimba ku zambia winaso ndikukayimbaso sikuti ndikulimbilana