NGATI SIMUKUDZIWA NDI ZANU KOMA MCP YAYAMBISA GULU LA YOUTH LOTHANDIZA MCP KUZAWINA ~ KOMA TILIMBA?
Вставка
- Опубліковано 21 гру 2024
- Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika
Ka kumpoto kuliso vindere nthena wanyamata waulesi nthena 😮😮
Anyamata a MCP akumpotowo akutaya nthawi yawo, 😅😅😅😅😅za ziiiiiiii!
Kupasidwa udindo kwa vitumbiko mumba kusatikhudze,iyeyo akukhutisa mimba yake ndi family yake asatipusise achinyamata akumpotofe.vindalamahyo idyani mpoto ife tidzakulizani ndi mcp yanuyo.sitidzakuvotetani ayi..
Umphawi sizinthu,anthu kulolera kumanamiza chakwera zowona?
Komatu apa zayambika yasara payiniya😂😂😂😂
Nonse amene mukusapota chakwela mitu yanu sikugwira
Ndipo ndi zitsilu zonunkha mkhwapa ndi mkamwa😅
Mavuto ake amenewa kufuna kuzavotera chakwera kuvotera satanatu kumeneko
Za ugalu
Palibe anga joine chakwera youth club chakwera must go
Apite
Anthu over 20 million alembetsa ndi angati?
Vanthu vinyake nivakuzweta mitu, Chakwela machine yakunyumba yako.
Vizeleza olo mahala 0 wavihonga nama 5000
Koma athu mukusangalalatu, Ife ndiye tilibe achibale m'boma. Vote yanga ndizai..
Chakwera nzeru ulibe ukufuna kiphetatu malawi
MCP Paulendo bs 4yrs yakwana bs kungobela zisakho ndizayenda maliseche atizuza kwakwana
Ine ngti muntumba weniweni awo chifulwa chauphawi akuenela kutelo kit apeze mgaiwa kunyumba kwao loma chakwelayo akumunamiza akafika mmamowa anyamata omwewo akumati aaimwe tidyenawo zaBoma????
Zaziiiiii kupepela kwambili kuvote mcp ndi chakwela
Wakwiya ndi mfiti, agalu a DPP munya muona , Boma ndilomweli sitikusintha
Awa akufuna Chan kwenikwen
Bola azidya mumabanja mwaomo
Nanga amene sakukhutitsa mimba make ndindani poti aliyese wandale ndichocho
NONSE NDI ACHINYAMATA ANUWO MUKAGWELA LIMODZI
Amalawi sidzizatheka malo molimbana ndi nyanja yimene akulandaniyi ku Tanzania
Zabodza zimenezo aphili mukunama
Nkulu wa achinyamata laku mpotoyo mkofunika azidya zamasamba coz thanzi lawo likuthawa
Akufuna kumudyera ndalama
Agalu a DPP inu, ndani angaiwale nkhaza zanu zija, DPP never again in Malawi
Chikangawa must go
Tiona 2025 kuti guru iri rikafika pati cifukwa oro sara anamucura Abraham mbuye cifukwa ca usogoreri wabwino nde awa a ngoti cakwera macini macini oziwa kuwaonesa mbwaza amarawi
Za usiru izi ndiye chimanga
Ndiye zichani
Komadi kuli zisilu paziko athu zimabatile phwiiiiii kumapangana zachikangawa muthu okupha zakutu kupotodi kuli phwepwa zawathu
Mhuuu
Nanuso a mcp munya manyi nthawi yanu ikutha mumalimbana ndi dpp ngat dziko muno chipani chilimo dpp bas kuyiwopa munya 2025 adad boma tikufuna tizizadya katatu ife feteleza ngabwingabwi zinthu zotchipa osati zalerozi zingokomela anthu olemela okhaokha akumudz akunya nyekhwe
Mapwa..,,,,.....ako
Musanamize achinyamata do not mislead
Adzaona wokha munthu woti adzamuvotere
Umbuzi weniweni
Angofuna kukugwirisani tchito anyamata inu
Kuzatema anthu ndi zikwanje
Olo mutani, chikangawa is already dead and buried
Tatopa tatopa komaaa chakwera tsikurina
Zauchitsilu bas
Mukunyadi muwona
Zabodza izi palibe ANTHU 7 million
Adyeleni amc wosavutela chipani cha kupa inchi
Too late
Zachamba
MUKUZIYAYITSA NTHAWI GUYS
Mukuwabisila chitumbuka pathako Pake chakwela iwe chachimwendo thongo lako
Adyeleni ndalama
2063my Foot 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Achinyamata inu mitu yanu sikungwila 2063 ? Mukuganiza mofoila osamalima fodya wanu bwanji
Vindele vinyamata ivi ulesi wekhawekha wakumuwovwilani vichi chakwera winu uyo mxeeew
Ndipo vakukhoza Soni kuombera manja North Va ziii
Zamboza izi angalu inu tonse talembesa zayerekezeni kumbela mudzawona nyekwe chikangawa
Skeff
Achinyamata ake at sasamba iwe
Kkkkkkkkkkk dyeleni wa mcp yo 😂😂😂😂
Amalawi lembetsani kuti tikvotere moyenera
Anyamata ake ogonja kale ngat ameneo