Chipani Cha DPP Si Munda Wa Munthu - Nicholas Dausi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 сер 2024
  • DPP Spokesperson Hon. Nicholas Dausi says the DPP is not someone's personal estate. It is a party of the people and the people are free to elect a leader based on the party's constitution.
    Mneneri wa DPP Hon. Nicholas Dausi wati DPP si munda wa munthu. Ndi chipani cha anthu ndipo anthu ali ndi ufulu wosankha mtsogoleri potengera malamulo a chipanichi.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 38

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому +3

    Adad omweo

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Рік тому +1

    Whether you had a meeting or not, we need Arthur Peter Mutharika. Iweyo uzamvotere Nankhumwayo.

  • @mandamandamanda2208
    @mandamandamanda2208 Рік тому +2

    Adausi munalidi mchipani cha dpp inuyo? 2020 dpp siinaluze masankho Koma anthu okhala ndi mtima ngati wa inuyo ndiamene a Nakonza chiwembu chomulanda boma mwaupando kuzera mumakhoti athu

  • @cadohjabu5565
    @cadohjabu5565 Рік тому +1

    aaa inu nde Sitingakuveleni Mabodza anuwa Dad bas ap

    • @cadohjabu5565
      @cadohjabu5565 Рік тому

      A Dad number 1 apa basi osati zanuzi a Dausi a Malawi sitidzakhulupilaso Munthu wamba kulamulilaso dziko IA Malawi

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 Рік тому +1

    Who started DPP Party was Dawus or who? I've one question to you Dausi in Malawian parliament, is there any opposition leader?

  • @kestinmacheso-zc7cz
    @kestinmacheso-zc7cz Рік тому +1

    Namkhumwa ngat akulephela kuyendesa paliament monga munthu wosusa ndiye angayendese dziko molongosoka. A daus sakudziwa chomwe akwelacho kut ndi chan

    • @esthergweje4038
      @esthergweje4038 Рік тому

      Kkkkkk nankhumwa zikumuvuta ku parliament angovomera zilizonse ndiye u President azautha bwinotu anthunu musagulitsepo chipani apa anthufe tikufuna Peter yemweyo basi

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 Рік тому +1

    Ngti mukuona kuti adad saima mwalimba madzi daudi wankhala mcp kamudzu alipo ndy mukuona ngti muthu angamvere zainu palimbe mongopola moto adad2 akuimaso tinasiya kunkhulupilira adakhwi dziko lamalawi linapenya pano.

  • @ibrahimwezely-pn6te
    @ibrahimwezely-pn6te Рік тому +2

    Uyuyu simunthu wamba

  • @user-nx8gy8lq4q
    @user-nx8gy8lq4q Рік тому

    Honourable dausi talking exactly

  • @lyiemax
    @lyiemax Рік тому +1

    Komabe we need adad omwewo

  • @peterjoshua2595
    @peterjoshua2595 Рік тому

    True speaking mr Dausi

  • @mussahcassim4963
    @mussahcassim4963 Рік тому +1

    Awa akufuna zosangalatsa thupi lawo

  • @felixntaika6201
    @felixntaika6201 Рік тому +1

    Sunati ulirad kuyendesa dzikotu sikuyendesa banja zimafunika anthu adzeru iziih sukuvesa mpati bankha iwe kkkkkkkkkk adad akuwinabetu ufune usafune

  • @peterjoshua2595
    @peterjoshua2595 Рік тому +1

    Muthalika never inspired me 😮 need new face in dpp

  • @patrickgnsulup6675
    @patrickgnsulup6675 Рік тому

    Mr Dausi alakhula zoona zake Ali ndikhutu amve

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 6 місяців тому

    Pamtumbo pano dausi ndi amene akuombela manjawo

  • @MathewsMANDUTU-lh6oo
    @MathewsMANDUTU-lh6oo 5 місяців тому

    Adausi awa ndye akalamba ndi nzeru zomwe,, hule uyu

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e 5 місяців тому

    Iwee dausi tadzingodya nawo za mbava chakwera ukakhala usatanic ndi wake mudzikangomwa nawo magazi boma lokupha lokuba loipitsitsa

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i Рік тому

    A Dausi zisiyeni...ngati mwatopa ...pitani ku MCP komweko....koma DPP adzsimira Mutharika.

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d 6 місяців тому

    Choka iwe dausi wadyera iwe

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 11 місяців тому

    Choka galu iwe bakhalani ku MCP komweko wathedwa nzeru komanso dollar 💵 inakutherani pano mukufunafuna podyera

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 11 місяців тому

    Inunso a MCP mukulubwalubwa Kodi chakwera ku MCP anavotedwa ni ndani? Kuchoka pa a tembo kufika chakwera atembo anakapikisana ni a chakwera? Agalu inu zaunyau basi za michira lendeéee

  • @user-oo5bx1rl3j
    @user-oo5bx1rl3j 6 місяців тому

    Iweyo Dausi ndiye umaganiza kuti DPP ndi munda wako? a DPP anakutola ndikukusambitsa iweyo ndi sopo wamakaka ndiye wayamba kuinyoza. Iweyo unali ndani Kamuzu atamwalira. Ngati simumadziwa DPP inachokela ku UDF. Iweyo unazolowera kupha ndi John Tembo umaganiza ngati kuti ineyo sindimakudziwa? Ndiye ndikuuze upite ku CI Ku Montfort Parish olo Bishop House ukafunse za ine . Unali ndani iweyo apa sindingakukumbe iweyo.. waiwala iweyo nthawi imeneyo

  • @BrightMhone-jw1qn
    @BrightMhone-jw1qn Рік тому

    Koma chilungamo APM azaluzitsa chipani Kodi munthu wina kuchipaniko kulibe? Ngati kulibe basi 2025 iwalani Za DPP kuzalowa muboma mupakana muzapeze munthu wina not APM plz

  • @chinomwephiri1183
    @chinomwephiri1183 Рік тому

    Awa ndaakatundu

  • @MathewsMANDUTU-lh6oo
    @MathewsMANDUTU-lh6oo 5 місяців тому

    Koma 2025 dziko lonse likufuna adad iwe zitha mau

  • @user-hb2hr5oc9l
    @user-hb2hr5oc9l 11 місяців тому

    iwe dausi wadyela upeze Malo amodzi oti uzikhala ukungoti uku wapita Koma bwanji kukalamba dzelu kapena zantha

  • @chazembaunderson-dm2lu
    @chazembaunderson-dm2lu Рік тому

    Choka iwe nkhope ngati manyi opondedwa nditayala ya trakita kodi anthu nonsenu mukufuna chani mukufuna ife anthu cholinga muzitidyesabe mayianuwo muona kuti azakuvoteleni ndindani

  • @selemannyirongo4882
    @selemannyirongo4882 Рік тому

    kkkk mukumva anyani inu a Mzomera ngwira ndi Magogo Gondwe ndi Jappi mhango

  • @emmanuelchirwa3420
    @emmanuelchirwa3420 Рік тому +2

    😅😅puwa person who are you,pls thank before you talk,sanje basi ,polanimoto abrother ,muzafandi bipi malume, kulankhula zopanda kumanga chipani ,akupasanindalama Kuti mukalankhule zopanda pache ,nkhondo siyimanga muzi polanimoto, APM ayimaso basi,

    • @hambalisaeedphiri
      @hambalisaeedphiri Рік тому

      Kungoti kuyipa moyo komweko agalu inu ndi amene mwatiyika pa moto lelo malawi akuvutika chifukwa cha astana inu bwanji osapanga chipani chanu

    • @patriciahtikhiwa662
      @patriciahtikhiwa662 Рік тому

      Wina ayi adadi omwewo Nakhumwa ayi bolanso tupere

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Рік тому

    Mwati sagwirana ma jurrata😂

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib 11 місяців тому

    Dzimitu Dzanu 😏

  • @user-qv4ko6ps4j
    @user-qv4ko6ps4j 6 місяців тому

    Mbolo yako dausi