Iweyo Dausi ukuganiza kuti anthu angadye stadium. Ndikupempha inuyo a MCP don't trust Dausi olo anthu akwào samàmukonda ai monga ndanenela kale kuti he is a sweet talker
You can't join your mother, it's not a choice It's by nature, you can join the party 'coz it's a choice, just because DPP it's not a party, it's Mutharikas family business that's why things are going this way, I understand it's not a problem for jobseekers, the yes bwanas 😂😂😂
Anthu akuononga malawi ndi amenewa
Day wa one kuzachimanga Kaye chikachapike mutu ku maulako
Anthu adyera amakhala ndi mbalume ndikuonera chitsiru chimenechi chotchedwa Nicholas Dausi
adzafa imfa yowawa kwambiri
Osapsa mtima ndale za ku malawi ndi part of entertainment 😂
Uziwa et zongovela izi dausi macheza awa ahaaa kuwatengela upusa adha@@petereliezer3795
The king is back🌋🌋 welcome Mr Dausi , home is best
Dausi kujiya kumeneko. Limbikira akupasa u minister. Udyeretu. This is your last term.
Ill never stop following him or atasitha chipani🔥💯...... He's just a vibe person 😂
😂😂😂😂😂😂 munthu osokoneza ngati uyu ine sindimamuonepo ayi,kuchenjela kwake koopya heavy
Dausi greatest of all times, good vibes😁😁😁
Ndipo inenso sindidzasiya kumukonda 😂😂😂
Kwambiri kumalowa chipani chabwino osati chipani chamunthu
❤😮 of😢😢
@@jacobjerome6538😅😅🎉😢😅😅🎉
Awa ndi achitsiru kwabasi
chisilu chimenechi ife pambuyo pa adadi
Ako nde wasiya kut nawe bwampini
❤❤❤❤ Ambwana umatha
That's great move Mr president and braval to Mr Dausi you are taking a good choice .....
Chakwera ❤ Dausi❤
❤❤❤❤❤
Politics is the game of thrones
Ndipo kwambiri
Ukalande mcp,, DDp waikanika, sungaithe dpp ase wachepa
Apm my vote
Politics is the game of Numbers 😂😂❤
❤
Mbalame yokuba iyi achita Manyazi APM akulowa boma❤❤❤
Boma lake liti?😂😂
Zokaikisaa kwambri ku dpp kukuchitika za nsete kwambri zikundikhumudwisaa kwambri
Osakaika....DPP ikulowanso boma...khulupiliran anthunu
Never
Ndipo kwambiri 😮
Imeneyo ndiyo Democracy aliyense ali ndi ufulu wopita komwe akufuna ineso ndiponso ku UDF don't blame it's my rights to do so, thanks
Democracytu taionatu ife ndipo ndakulupilila kuti anthu a dpp analidi ademocracy ndipo anthu aja asakhala ademocracy. Nthawi ya dpp akaitana amcp kuti akhale pamonsi amakana lelo Iwo aliboma akawaitana a dpp akumabwela semene zikuoneselatu kuti dpp ndi imene imaziwa democracy ndiime phopo bwanji
Dausi is too clever. Eish ! 🤐🙌
My man Hon. Nicholas Harry Dausi
Dausi I like this politician whether he changes side to MCP I like his character
Ukatelo afuna malo ukoooo😂😂😂😂 ichiiiiii
Welcome back
Feel free this is your original party, takulanfirani madala
A rolling stone gathers no moss...
no this is politics
These Greedy politicians doesn't care for the Needy
Munthu oipaaaaa,, wadyela.. Osakonda dziko
And when he left MCP for dpp he did well neh?
Wise up
Zoona boss
Abambowa ndi achitsilu chonchi kani
Keep going Dausi
The servant of the people ( do service to the people)
Hon. Dausi thank you simunanyoze Dpp and APM.. Zikomo.
🔥🔥🔥🔥
Iweyo Dausi ukuganiza kuti anthu angadye stadium. Ndikupempha inuyo a MCP don't trust Dausi olo anthu akwào samàmukonda ai monga ndanenela kale kuti he is a sweet talker
Inu mmafuna anene kuti chani chomwe bomali siikudziwacho?
Dausi ndi machine ayiseye 🔥
Dausi ndikatundu 😂😂😂🙌🙌🙌
Yee
Malawi walero womvetsa chisoni zedi nkhalamba zingotipusitsa zili pheeeee
😂
Ku Mwanza samufuna uyu.... Kubisa mawanga mbuzi iyi... Fisi wachabechabe.... Sadzawinanso ku Mwanza
Dausi , leaving DPP, knowing that it's worn out and no direction, it just moving like a dragon fly, Martha😂😂😂😂
Koma Dausi ndi mbuzz eti
Mukunama mufunseni Dr Joyce Banda mpaka kuthawa mudziko muno
Late Nelson Chikalamba Khonje anali waku Khondowe Nkhata-Bay north anakana mai ake omubereka
You can't join your mother, it's not a choice It's by nature, you can join the party 'coz it's a choice, just because DPP it's not a party, it's Mutharikas family business that's why things are going this way, I understand it's not a problem for jobseekers, the yes bwanas 😂😂😂
Sadziwa chomwe amafuna uyu
Mwamuchosa ndiye umafuna azifinyika
Malawian politics
Dausi, Dausi, Dausi..........ayi zikomo Ambuye akuone ndithuuu.
😂😂😂
🙋♂️🙋♂️🙋♂️🙋♂️🙋♂️🙋♂️
Atha bac
Uyu ndi swiswili uyu Dausi!
Ichi nd chitsiruuuuu
Olo chakwera sakumutorela kuyankhula ichichi aaaaahhh
Mbuzi iyi
Welcome to MCP Mr dausi
Kkkkk tizilpa koma, we are sinners, too much lies and hypocrisy
Shaaaaa Kalulu
Ndausi ndi opusa kwambili
Why???
Ndipo ndi mbuzi yachabe chabe
All the best
Nkhope kunyasa ngati manyi
Nonsense!!
Awa ngadyera
ineso ndikumva sugar ndima comment dpp is winning this game
Ngamisala awa
Kkkkkk ndale zimampangisa munthu kukhala chitsiru ndithu
Ichi ndi chisilu ndithu.
Nice
Machende ako chi nicholasi dausi omafuna udindo ku dpp mukuziwa kuti APM sakucheza ndi ana
Monica ndiye watchena ndipatse number yako
A chitsiru awah 😎 ndiye ukuwona ngati mene wa choka ku dpp ife tikukusowa umatipasa bzy saname buzi iwe
Tinakutulukani adausi ahule pa ndale,,😂😂😂😂
Chi Vibe 🎉🎉
Even president akuziwa Kuti ndi tambwali uyu.kuthwa pakamwa zaziiiiiii
Politricking at crimax
A president akukupusitsani ameneyu wadyela mndalama uyu. Koma palibe oposa DPP pa chitukuko olo kumwamba kukudziwa mulungu ndi mboni
Dausi abambo oputsa heavy
😂Ineyo sakomenteso 😂 ndikugonva kukoma ndi makoment ndawaonawa 😂😂😂zadziwika kut dpp ndi boma basi ❤
Apm woyeeeeeeeeeee❤❤
wapanga bwino dausi kuchitaedwa ku chipani Cha dpp , akunama uyo afuna kukudyelani ndalama chenjerani nayeni ameneyo akukupusitsani ndinthila kuwili mumasokoneza kwambiri
Oyee!!!!!!!!
Ulibe mfundo Nicholas dausi. Iwe ndiwadyela basi palibe chimene unachita cha nzelu ku mtundu wa a Malawi. Ndiwe mbuzi ya munthu masikini weni weni
Musavotere anthu woyenda ndi mphepo ngati amenewa
Iyi ndembuzi yeni yeni ndithu machende ako galu
Mpaka kutukwanatu wasiya machende abambo ako kutchula aazako
Mbava is shame to my motherland country, Guys we must know that we gonah be same like zim
Chisilu ichi chokuba chifuna chikwama ichi
typing....
😂😂😂😂.....my question is where is chilima since I don't see him wht going on 😅
Awa kkkkkkk maliro wo mulira ambili
Iziiii ndichifukwa dziko silikupita pasogolo Kuba omwewo amabawo akungodzungula ndimaudindo kumangosintha zipani
Ndipo kwambir awa akubwezeletsa chitukuko pambuyo
Kodi vice anajomba this day?
Daus
Awa ndiwosokonekera awa,,, zakuziwa chimene akufuna panoyo pa moyo wawo.. Akungosokoneza Malawi
Akuluwa
This man is stupid, with such kind of these people thus y Malawi is going nowhere
Dirty game 😅 interesting game.
Dousi Dousi Dousi, umafuna chani kwenikweni?
Dausi watha bas. Ndipo saoloka pa ndale ai😂😂😂😂
Wakulizani Dausi makape
Be careful with him he is a snake in the village not in the grass ,he did a lot of bad things during kumuzu
Zaziii
Kkkkkkk Koma dyela ndimatenda pakulira iwepo dausi mmmmhu
Eti eti kape weniweni
Zovetsa chisoni ndipo abambowa afika pa uchisiru ndithu
Dawusi usazaende Dela lakwathu ku zomba tizakugenda ngati kwanuko anakwanisa kumubera chakwera wakoyo carpert ifekuno tizagenda conivo
Amadyera mphotho bambo Nicolas Dausi .Amakometsa kumene kuli madyo .
Mbuzi yamunthu iyi
be careful Mr President anthu wa amayimbila ng,oma komwe kuli mpunga, cholinga azidyabe ,ovutika kumangofutuka ,Mulungu akuona
Zitsiru za anthu izi
Iwe ndi wa congress iwe wachita bwino kukuthothora ku mcp
Dziko la Malawi linatembeleredwa anthu opanda umunthu ngati awa ndi omwe akupangisa kuti anthu azivutika