HOT CURRENT 14 JULY 2024 |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 13 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 97

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Місяць тому +8

    Go on Guy's we wait to see the changes in Malawi eeeee from Bakili muluzi up to know am in RSA because of politics of Malawi throwing as away not thinking of coming back to home eeeeeeeeesh

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 Місяць тому +6

    Chilima was assassinated that's the truth what more do u want to hear?

  • @user-lj8ug5lq8c
    @user-lj8ug5lq8c Місяць тому +2

    Guys keep it like this ,this is Hot current we know from those days congratulations

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj Місяць тому +2

    Manganya ndi mcp anapha chilima.

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Місяць тому +3

    Usi si wa UTM. Munamuwona muja amarandira udindo muja? UTM yachita bwino kuwaturuka.

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому +2

    Ngozi ija singozi ngozi ,,komanso yonse taona ndimafinso

  • @BambordKabambe
    @BambordKabambe Місяць тому +6

    😂😂😂😂😂 chaka chino ndi CHONG'ALURA

  • @JohnNjerenga
    @JohnNjerenga Місяць тому +1

    Kkkkk akut ipondeni fadha

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Місяць тому +1

    Apa ndiye mwabwelatu chilungamo chimenecho

  • @EstherChimombo
    @EstherChimombo Місяць тому +1

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯💯

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk Місяць тому +5

    Times muziwe kuti chilima agwila bwanji ntchito ndi chakwela mu 4years

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Місяць тому +2

    Masapota a UTM tonse tatuluka ku mgwirizano Chifukwa tinkasapota Chilima.Usi alibe masapota.

  • @user-oh9bh1cl3b
    @user-oh9bh1cl3b Місяць тому +1

    Well spoken guy's adzimva akawalalawa

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Місяць тому

    Walephera Chakwera kulamulira kuchedwa 4yrs ndipo akhala akungodandaula DPP mmalo mopanga ziganizo msanga

  • @OrtonKabbichi
    @OrtonKabbichi Місяць тому +2

    Sizachilendo olo pa ngozi ya ndege ija anachedwanso kukafufuza ayambe kuchotsa ameneo onwe amaenera kukafufuza za ngozi ya ndege

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 Місяць тому

    Mtsukuluzi ukulankhula mopusa, kufooka kwa Ussi kunayamba Chilima alimoyo. Ndipo. Chilimma anali atamuzindikila Kale Ussi ukathyali wake.

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Місяць тому +3

    Inu ussi siwa UTM 😂😂😂😂ameneuja ngawa MCP

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Місяць тому

    Chakwera so asamale zomwe wawona Nzake wa kwa merica zija zichitikanso kuno.

  • @symonmakata938
    @symonmakata938 Місяць тому

    Changucho chiyambile pa kafukufuku wa ndege inapha chilima kenako the public ikhala ndi changu

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Місяць тому +3

    Dziko ndilathu osaonesa kutopa azibambo ipondeni thawi ino palibe kuopa ng,alulani basi ng,ambani

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d Місяць тому

    Usi atha ngati nankhumwa sure, olo kuthesako akufuna kukhaulisa manganya coz anamuziwa kuti uyu sitili limozi ndi wa mcp.

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Місяць тому

    Dziko nkumasawukaaaaah!!!!!!!

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Місяць тому +1

    Masapota ake ati omwe atsatire Usi ku MCP. Musanamizane palibe yemwe angavotere MCP true member wa UTM

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita Місяць тому

    ngati bola Allience latha ndibwino kukhala opanda president cs chakwela polowa m boma unali mgwilizano maka utm inali ndimavoti ambiri kuposa mcp we must have emergency presidental election

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому

    MCP yayambitsa nkhondo yoopsa yokha amalawi sangasangalale nazo izi
    Zotsatila results zangozi kuli ziiiii mpaka pano what do you do

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Місяць тому +1

    Keep it up Guy's ife ndalama tidya koma sitidzawavotela talira kokwana sife opusaso pano

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy Місяць тому

    Akuchedwa Nd pule yomweyo😂😂😂😂😂

  • @imaculadaAndre-ns1py
    @imaculadaAndre-ns1py Місяць тому

    Fiti ndifiti basi awa sangaulule chilingamo kwao ndikunama basi koma ife chilingamo tinachipeza kale

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Місяць тому

    Akuti mbwexe😅😅😅😅😅😂😂😂

  • @catherineKalinga-m4c
    @catherineKalinga-m4c Місяць тому +2

    🤩

  • @AishaChipande
    @AishaChipande Місяць тому +2

    Chakwela azuzula bwanji pomwe iyeyo anaphaso muzake

  • @EsnartMbalale
    @EsnartMbalale Місяць тому

    Ipitilile ndiyabwino coz ikulakhula mosatenga bali

  • @imaculadaAndre-ns1py
    @imaculadaAndre-ns1py Місяць тому

    Tamusiyani maganya abakhala komweko adzatiuza zenizeni abawatola zifukwa adzapange sewelo mutu wake chakwera anapha zake chifukwa chaudindo

  • @OfwaMwambila
    @OfwaMwambila Місяць тому

    Alot of people re in marriages that ended a long time ago but due to kids u re forced to still living together that's what I think was the case of SKC&usi.

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki Місяць тому +1

    Akuyambisa kuchedwa ndi achakwela ndipo ife tinalakwisa kumuika munthu onamizila ubusa Ngati uyu pa mpando

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Місяць тому

    Mbwelera zokha zokha za mcp kkkkkkk koma pankuku!!!!!!

  • @BestonStima
    @BestonStima Місяць тому

    Mcp ivutika chifukwa isanalowe m'boma amalawi ankaopa nkhanza za mbiri yawo
    Lero in their 4yrs rule patuluka nkhanza.
    Do you think they can reign???????????

  • @robertnambazo9936
    @robertnambazo9936 Місяць тому

    President osaziwachomwe akuchita he is so relaxing President President uyu ndi bubu shatapu zake

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa Місяць тому

    Koma ma guys inuo hahaha munatopa nalo dzikoli simufunaso zachikape

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Місяць тому

    Manganya ndi wa mcp not utm

  • @johnmhango9405
    @johnmhango9405 Місяць тому

    Briefcase parties end just like that.

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Місяць тому

    Uyakhura za chidodoyo ndiye ili mbudzi yoyambisa chakwera samasata zinthu that’s y anyamata ake angomisewera basi.

  • @SteveChapola
    @SteveChapola Місяць тому +1

    A mcp chipani chokupha

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому

    Sitizalola report. Wonder you are very Intelligent than pankukuyo

  • @GodfryMalishe
    @GodfryMalishe Місяць тому

    Salute u guys 😂

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy Місяць тому

    How many meetings manganya has been attending?? Can he allow to apart from the alliance coz it's obvious manganya it's won't allow

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 Місяць тому +1

    Eeeeeee yankhulani guys ❤

  • @lukedumbula2724
    @lukedumbula2724 Місяць тому

    Very true wonder and jona, a PULE akuchedwaa

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Місяць тому

    Pa nkhani yochedwetsa chitukuko, tingomuchotsa next year basi, sali fit Chakwera to be a President.

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому

    A Usi si president wanthu,,munthu mkazi wake tamuziwa polumbilitsa mkumazitama kuti ine sindinayendepo ndi mkazi wanga,,muthuyu angayendese chipani

  • @RafiqueChibwana
    @RafiqueChibwana Місяць тому +1

    You guys u don't share kamba here really keep it up guys kkkkkkkkk

  • @JaphetSakala-pq4fl
    @JaphetSakala-pq4fl Місяць тому +2

    Kuchokela pa ifa ya VP chilima kufikila pasiku la mavoti UTM ILI PA TOP ONE. or Dpp ndi mcp ita phatikizana. UTM IKUTENGA BOMA TIZAIPEPESA NDI VOTE.

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Місяць тому

    Lero munabweratu a jonah kkk wonder akuti back to sender eee Chakwera dzimvere mumtolo

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Місяць тому

    Eni ake a UTM ndifeyo ovotafe Tatupu ndife awowo dyela Paolo asaleko tilibe nawo film

  • @PartsonKamkuzi
    @PartsonKamkuzi Місяць тому

    Osawopa ayi a malawi ambiri tikuyang'anira inu kut muziyakhura mosawopa apa

  • @CosimassShyman
    @CosimassShyman Місяць тому

    Wakulu andevu zamwayi amayankhura Chichewa cha boo

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa Місяць тому +1

    Ng'alula iwe

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому

    😂😂😂😂😂 anyamata inu mwandisangalatsatu chikufunika ndichimenechi osanyangerera kulankhula chilungamo kubandaluka basi sizoopaso ayi

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p Місяць тому

    Kaya DPP kaya ilibe ndalama iwinabe 2025

  • @user-rd9pd9hr2l
    @user-rd9pd9hr2l Місяць тому

    Inuyo munabwera ngati coming 🔥

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Місяць тому

    A pule ayamba kupemphera ku CCAP kamutu kataya

  • @joneskalitsilo6556
    @joneskalitsilo6556 Місяць тому

    Exactly Wonder bambo wanzelu amakonza mavuto amu nyumba mwake not kutuluka nkumakadandaula panja or kubwalo kuti mnyumba mwanga sitikudya ana anga sakuvala bwino, sitikudya bwino! Nde ana Inu muzivala bwino, muzidya bwino, ukuganiza kuti anawo azitenga kuti?

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 Місяць тому

    Nkhaniyo ndiyoona, a President akugona kwambiri pachiongolero, dziko silingatukuke ai

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Місяць тому

    Anaphedwa ku Mwanza aja ndiochepa.pano ayesetsetsa kupha ambiri.athakati sadzasintha.Malawi Congress of Perishers

  • @DarlingtonMaya
    @DarlingtonMaya Місяць тому

    Gyz mmmatha

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому +2

    MCP ndi Yakupha

  • @PartsonKamkuzi
    @PartsonKamkuzi Місяць тому

    Iwe pankuku osamayakhura mowopa apa

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI Місяць тому +1

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn Місяць тому

    Mumakwana mabigi

  • @Amos-tr6ro
    @Amos-tr6ro Місяць тому

    Koma makosana inu MMM mwanditha keen on on our behalf

  • @jackmambo2638
    @jackmambo2638 Місяць тому

    Kod amaphang’ombe ali kut😂😂

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Місяць тому

    Did. Mcp ask Afford

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki Місяць тому

    Aganizq bwanji mwakuya kuposa anthu zosatheka ubongo unatha chifukwa ankadya zopasidwa Za chaulele

  • @user-tg7ni7wh2c
    @user-tg7ni7wh2c Місяць тому

    Eeh 😂

  • @johnmhango9405
    @johnmhango9405 Місяць тому

    A kaliati ndi a njawala nzokonza izi, akufuna apange handpick Kabambe, can't you read between the lines? Typical of atsogoleri a dyela.

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r Місяць тому

    Emusipi ofunika isale yokha. Anthu woipa awa

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 Місяць тому

    Decisiveness palibepo

  • @yusufjab786
    @yusufjab786 Місяць тому

    Ndipo inuyo kumeneko mumaitha 😂😂😂 akuchedwesa ndi chakwera

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Місяць тому

    You. are. wrong. it. Is. People. at. the. grassroots. who matters not individuals

  • @PartsonMdeza
    @PartsonMdeza Місяць тому

    🤣🤣🤣 iponden fadah kkk

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn Місяць тому

    Ofufuza ngozi akuti, khoswe akakhala pakhate sapheka

  • @SteveChapola
    @SteveChapola Місяць тому

    Asiyeni atuiuka chifukwa chake achakwera apha chirima ndipo ndizoona

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf Місяць тому

    Osamayiwala ku mudzi kaamba kokomedwa ndi maidyaidya chifukwa tsiku Lina amadzakusandutsa mtsamiro wa mfumu ikadzamwalira.

  • @michealchaomba9761
    @michealchaomba9761 Місяць тому

    😂😂😂 President wake utiyo mukudikira kuti azuzuleyo

  • @MarthaBanda-ye4pt
    @MarthaBanda-ye4pt Місяць тому +1

    Koma Wonder Ati kukura mtima 😂😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥uyatseni basi ng'alulani basi

  • @user-ru4px8os2v
    @user-ru4px8os2v Місяць тому

    Anthu ake ndi chimwendo banda,howeh mkaka,zikhaleng'oma ndiomwe akuyenela kuchoka

  • @ThandiMbewe
    @ThandiMbewe Місяць тому

    Musamamuzile zochita president, yekha samawona???

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus Місяць тому

      President wake uti
      Ma comments 100 wa MCP yekha .chita manyazi😅😅

  • @SteveChapola
    @SteveChapola Місяць тому

    Chakwera ndiwofoka koma kumagaanthu chimenecho ndiye chitukuko.chake

  • @NdazionaKumcheza
    @NdazionaKumcheza Місяць тому

    Ine dakalira malemu za chipani tizitaye uko aaa

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani Місяць тому

    agaluwa alilimosi ndi chachera

  • @PartsonKamkuzi
    @PartsonKamkuzi Місяць тому

    Osamayakhura ngat akupatsani za lent kung'alura basi ukuva iwe ndevuzamwayi !!

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s Місяць тому

    Inu a times muyang'ane mgwirizanou kuchokela mmbuyo inunomwe mumaunikira mgwirizanou mmene umayendela chilima asanamwalile asiyeni ausi ali ndigululawo odya zake alibe mulandu

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn Місяць тому

    Mumakwana mabigi