Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
Norman is right,the fact that aperson is working in the government does not bar aperson from being rich . Malawians justify poverty as being honest and truth
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
The most evil person during Peter Mutharika regime is this bastard called Norman Chisale, very evil creature from Ntcheu. Akufanana ndi malemu a Fokus Martin Gwede omayenda ndi ma warrant of arrest m'thumba. Oyipa uyu, mbuzi, mphaka, kanyimbi.
Big up Norman Chisale ,I love your courage 🔥 Ambuye apitilize kukumenyeran nkhondo ,,,I'm one of your supporters
Ndpo nthawvyamayankho ikubwela big tipanga zobwezera ntoporao
Komano pa point ya human rights Peter Muthalika he really respects
The lady was carefully selected to handle this interview am impressed with how she has handled this heavy interview. Professional indeed
😊
God bless Mr chisale komano mokupemphani ndithu pepani uyu akufuna kut mumukhululukileyu imvani kulila kwake kut ukulu wayehova ukhalebe pa inuyo yesu anat muwakhululukile chifukwa sakuziwa chimene akuchita
Musaiwale kut munthu payekha alibe vuto koma satana akamulowa amapangisa munthu kuchita zimene choipa chili mwa iyeyo chikufuna please ndikuziwa ndithu ululu ndi ochuluka kwambili koma khululukani ambuye apitilize kukupasani moyo wamphanvu madaliso avumbebe kut wamasiye apeze popumila
Am watching this interview kachikenaso Norman Chisale yu ndi #1 kwa amene alipa chilungamo akudziwa kuti big wa ndi real man osangoti mwakati poti umadana naye.
Leah you the best journalist...well done to Me Chisale
Mr Chisale isn't my relative but ndawamvesa he is a real soldier, BRAVO CHISALE. BULL Sheet kayun.
Chisale ndimunthu wabwino kwambiri wamanga ma church wachita zambiri Ambuye akudalitsen achisale long live
Bravoooo big man chisale i salute you
Chisale akumva zowawa chifukwa cha anthu ansanje but Chisale is the best Man in Malawi he spend his money to help the orphans and community, God bless you always and protect you Mr Chisale.
Zoonad ol evn Ines zimandiwaw, km Amalawi if nsanje😢
@@user-or8cw6md7t amalawi amamukonda munthu akafa, that's why dzikoli lili lobwerera mbuyo,
Great man Norman Chisale. Oceans of luv to you and your family.
Azodiak tamakhalani ndi ma bottle amadzi mukamapanga interview ndi anthu please
Komadi man
I support 😂😂😂good
Kkkkkkkkkk Norman Chisale !!!!! Ur a big Man. Wandiwaza kwambiri Msungeni all the way from Zambia.
Msilikari adzakhare msilikari mpaka kare. Big up bro N. Chisare❤❤
The one who talk the truth doesn't fear and it's really true that the truth pains big up Mr Chisale
Am agree with you 💪
I agree with you.
Interviewing a well trained professional soldier should be different with interviewing a well trained professional economist💪🏾💪🏾Bravo snipper Norman Paulosi Chisale🤣🎉🎉💥💥
Chisale your number 1 well trained soldier
Akuzuzika ngati yesu chisare ndi Good Samaritan athu abwino amazuzika
Gud interview love you questioner and Mr interviewer Norman
😂😂😂 so in love with his courage 🤦🥰
great mtolankhani , kip the fire burning girl
Steven kauni samalani komwe muliko chisale ndiokwiya
Definition of having readership, fire 🔥 chisale
Koma Chisale uyuyu eeeeeeh 🙌🙌🔥🔥🔥
Bravo Bravo 👏 😁 Soldier...
Soldier never die chisale more 🔥
Great man ,i like u
Well trained,,, the bodyguard from bejin
He is very emotional and trying to run away from facing justice. No one accepts to be guilty in public and whatever is doing here is normal for suspects. 42years doesn't match with the way he looks unless he tells us kuti amasamba Nyanga.
True leadership timakunyadilani mr
Mr Chisale I hear ur story it's very bad and am very happy with u ustand with God dnt give up mukuyakhula kwako mulungu akumva ndipo mulungu amalora Kuti ana Ake andutse mmavuto ndicholinga Choti ukulu wake ukaonekere God will be with u mwaiwe muli usogoleri
Big up Mr chisale
The real legend khaaa wauuza ngamo
Tikukuvesesani mr chisale.
I like the energy tht u hv Mr chisale as a soldier...big up❤
This was nice chisale seems a good one though ndindale
Chisale usatiuze kuti akhale wo opa mulungu suyo chakwera wo opa mulungu akutizunza
Norman your statement is clear and comprehensive but what about Chthyola, Chimwendo Banda, Kunkuyu etc ??
Mulungu akhale patsogolo basi Mr chisale Angoni
Those who are saying bravo chisale you need special prayers..this guy stole our money tax payers money....he accumulated wealth within a short period of time....hotels cars houses etc he is backing himself apa he can't admit it.....and you are busy kumunyadira 😮Malawi ndife ogona too much.....he is lucky he is outside otherwise he belongs inside
This lady 🙌🙌🙌🙌🙌
This guy is some how mad
Komatu chisale ndye akumulakwla
Watching from zambia
Political prosecution has ever been in existence since our independence....please follow the rule of the law always! Clear conscious is the medicine...God is watching and will judge everyone right..
Your the best Leah
I like sir Norman Chisale he's been good in speech osamaopa pa chilungamo
Chisale ndikatumdu🤗
Mr Chisale i understand your pain please please firgive him isbus for your own good, you saud you are Christian our master jesus taught us to forgive those who do us wrong before we ask to be forgiven
Mr chisale attitude in this interview shows kuti bambowa ndionama..😂
Ndipo sukunama uku ndiwabodza auze mtundu wa a Malawi kuti ma billions a chuma anawapaeza bwanji osamangobwebweta zopanda phindu, kufuna anthu akumvele chisoni.
Ndinu mabulutu guys
Akunama uyu, wakupha komanso wakuba, chitsiru chimangidwa chisiyeni, sakudziwa kuti apita kundende.
Mbavaizi aaaaaa awonongachumachamalawikwambili
Chisale🔥🔥🔥🔥🔥
One thing i like this guy he talk straight
Kkkkkk ayayaya malawi tingogulisa tigawane dollar zo
Kulavula Moto munthu wamkulu, Lord have mercy on him
1986 he was already working as a soldier but he is saying is 42 years old eeeeeish!!! 😂😂😂komatu munthuyu akuoneka ndiokakala mtima mayankhulidwewa atha kupanga zoophsya. He is saying kuti ndiopemphela koma akuti sangakhululukile aSteven Kayuni 😭😭 chonsecho amayenda ndi bible , mawu a Mulungu mwamunthuyu mulibemo.
Soldier sakugawa kamba
Big up boss
True leadership
Aaaaaa mbalame iyi
Bravo Mr Chisale
Chisale💪💪💪🇲🇼🇲🇼
Norman is right,the fact that aperson is working in the government does not bar aperson from being rich . Malawians justify poverty as being honest and truth
Uyu mafunika brain Banda osati ana awa
This woman is brave
Fire 🔥
Fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
This was a hot 🔥 one lol 😂
mbuzi chisale ukuona ngati bambowakowo sangawine ameneyo wapha albino wakwa na
MCP ikazachoka m'boma idzazunzika kwambiri
Powerful talking and intelligent, proud of you @Norman Chisale
Intelligent ya ku machende amalawi mapanga support zingawenga bwanji, kupusa
Mukuyamikila chisale man? After all what he did now you're embracing his work.... don't you know people lost trust in DPP and one of the biggest reason ndi iyeyu
People never lost trust with DPP...anthu tinanamizidwa kuti tizaona zabwino...pano misozi yatha mmaso yayamba kutuluka ndi misozi ya magazi chifukwa Cha bodza la CHAKWERA ndi chilima.
respect to you both you building Malawi in this interview ..
Courage muli nayo...komano kusa kululukako kuchita kuoneseratu kuti muli ndi mtima wakupa
😢 or uli iweyo kut munthu akunamizele mulandu wa murder. Uthakumukhululukira?
Sukudziwa chomwe ukunena, sukuona kuti Chisale amuzuza popanda zifukwa?
Ndamva chisoni pokumva nkhani yanu bambo Chisale 😢 koma chilungamo chilipo ndipo momwe mwadutsa inumo enanso adutsamo ili ndidziko. Abale whyyy a police athu mmatero, olo ndiliineyo ndingaophwezetu ndipo ndikanamizilidwa ndimakwiya kuposanso achisalewo 😂😂
Kkkkkkk aaa zoona. Msilikali kiching, amba chilungamo n how he's feeling with de way they r treating him
Yeah azayakha zomwe amamangila Norman chisale
Dpp yangoyenera kubweler 💓💓🙌🙌
Lea ndi makina respect
Nice interview
🔥🔥🔥🔥
Wow!!
Wabodza iwe umakhala kukawale pa rent bingu akulamula unalibe kanthu unaba chuma bingu atamwalira ku state house
Eeeeeeeeee ai zikomo kwambili koma Mulungu arimbariyakhe
I love you Mr noman❤
Once a soldier always a soldier
Exactly
42 years old? Did I hear that well? 🤔 Interesting.
Ambuye Awakhululukiredi😢😢
Muluzi wa agalu ndiumozi, Chisale i fill your pain
Chisale katundu omanga ndi mawaya
Aaaa😮zaka 42 ndeine ndili 15 years 😂😂awa ngabodza
Chisale nd galu ndthu
Uyu ndi nsamariya wathu ku Ntcheu
😂😂😂😂😂😂😂moto kuti buuuuu L malekano umatimilila koma bwinotu akubandula mbakela bwana ameneyo 😂😂😂😂😂
The most evil person during Peter Mutharika regime is this bastard called Norman Chisale, very evil creature from Ntcheu. Akufanana ndi malemu a Fokus Martin Gwede omayenda ndi ma warrant of arrest m'thumba. Oyipa uyu, mbuzi, mphaka, kanyimbi.
Leah , bravo 💪
Takhulupirira ndiwe wachabechabe mbava
❤❤❤❤❤❤
Mbava chisale
Chisale mbava yayikulu mumalawi
Once a soldier always a soldier❤❤❤