The Podcast! is just Cool keep on giving us more! 💥💥 However the one not On Camera is bringing some confusion abit as far as Podcast Quality z Concern. Try 2 eliminate his side Plz he's no longer needed!
10 may next time put on the glasses 👓 of your size, pulling up glasses now & then disturbing the show but i like your energy/the way you talk,Desire be more active and guys stop mixing topics...it will be much better & more interesting
You are just mixing stories, make sure you stick to one at a time, do some research of stories before presenting them osati mwina mwina ... Otherwise you are more welcome.
Akuluakulu muzifufuza kae nkhanizi nkukhala ndi info yokwanira bwino before presenting them. For example, pa nkhani ya Pasuwa ndi Mponda, they are interim coaches osati a permanent koma the presentation is like anthuwo they are there for good in such a way. Who can leave his or her permanent job chifukwa cha ka ganyu? Pa nkhani ya Shumba ndi Aika mmayeneraso mupange research kuti anthuwo ndindani before everything. You can do better.
The Podcast! is just Cool keep on giving us more! 💥💥 However the one not On Camera is bringing some confusion abit as far as Podcast Quality z Concern. Try 2 eliminate his side Plz he's no longer needed!
This is one of the best. Ambuyo anja ndinaonera koma iyi yonkha yandikwaza kwambiri kungoyamba ndi topic ya mzelu
Am liking the video just seeing desire in it. 🤗😎🤩💯
What a great conversation !! Ten out of ten .. 😮🔥🔥
conversation ya nyatwa, mkazi okuda bho, bere la bho🔥🔥
umakwana ase ndipo yamabereyo ndi fact
first time watching koma i knew wina anena iziz and nayeso anadziwa wina afa zwee hahahaah
😂😂😂
Ngini ili bho 10may atakhala host itha kubhebha heavy nkupezaso dolo Mmodzi ozitsata akhale 3 ndi fact Checker kupewa za Mwina Mwina
dope stuff
Good start 👌 👏 👍
nkaz yo akumazitengera personal
Keep it up
Pa national team coach munabwera opanda research.... Those guys are just temporarily interim not as 10 is portlaying..
Nkaziyo matama thooooo ngat kut sanyera
The third who is not on camera akusokoneza
This is better than Gossip Malawi 🔥😅
Kod 10 May wamaliza kupepesa kuja
Anakuuza zot temwa Nd waku Lilongwe ndan ndiwaku rumphi ameneyo
I think this podcast should stick ku Zopakulanazi you guys are accurate and resourceful that side 😂😂 ..the rest zitayeni
Kupakula Beans 😂😂
10 may next time put on the glasses 👓 of your size, pulling up glasses now & then disturbing the show but i like your energy/the way you talk,Desire be more active and guys stop mixing topics...it will be much better & more interesting
Mkaz ndi ndaan kod😂😂
Muti nchani kod😂
Apa nde bolaso tikuferanji😢😢
next time mukhare serious cuz nde episode imenei 1.5 pa 10
e mkazikumene ukufunikila kukwelakumene malole inukutani muzitiwonetsa kumene zinginizo
Makwana bwana ten may 😅
Ali ndi bele la bho I think ndioonela😅
Akulankhulira mmimbawo bwanj
Mkazio bele labwino
Mwaza
Ife sitikumvesa man 😢
Iy ndii kwa gwanji
Zukhala bwanji kodi ndingomva mmhuuu mh mh ngati akubandulidwa
Why is there a third person speaking off mic and off camera?
Desire has some good points🥱.. im giving the program a 10😂
😂😂
Aaaaaaaaa ma guy tapezani fans yosata ngini izipanga program osati awawa
Wow
You are just mixing stories, make sure you stick to one at a time, do some research of stories before presenting them osati mwina mwina ... Otherwise you are more welcome.
Sizikumveka ... mukuti chanii
Basi taona mumafuna tionezo
Iwe ndisakupeze mkakusiyaso ku ndende kuja white udamkondetsetsa
❤️🤣💪
Program yabwinoo
Right
Ndiye osavala bra bwanji asisi
😂😂😂 mwaganiza bwanji man
Intro, just pointing out zomwe ena amachita, osangobwera nkuyamba zanu anthu aone and asiyanitse okha bwa
Akuluakulu muzifufuza kae nkhanizi nkukhala ndi info yokwanira bwino before presenting them.
For example, pa nkhani ya Pasuwa ndi Mponda, they are interim coaches osati a permanent koma the presentation is like anthuwo they are there for good in such a way. Who can leave his or her permanent job chifukwa cha ka ganyu?
Pa nkhani ya Shumba ndi Aika mmayeneraso mupange research kuti anthuwo ndindani before everything.
You can do better.
Its Temwa Chawinga
🔥🔥🔥🔥🔥
Mungophatikiza nkhanitu palibe chomwe tikumva ifee madala
The girl needs to chilll let other speak, come on 🤷🏿♂️
Zukhala bwanji iwe jahkev
Desire
10 may zili bhoo
jaa kev alikut kod?
Nkhanizo zilipo zingati mwati?
You are taking sides guys
Anthu musanayambe kuonera koma mwathamangira kaye kuma comment? why
Why someone intervening when he is not on camera, and try to introduce a topic not just mixing
10 minutes in nkhani simunayambe??? Boriiii g!
Koma a Malawi are you serious first episode u r expecting everything to be perfect so sad😢
@@phillipbanda4477 Feedbacks are essential! Good or bad!
Very Puwa Kwambiri
Izi siza aliyese. Hype zero
Tione kut zikut bwanj
Not what I was expecting.......
Your not giving that "MAD" vibe
8/10
Iiiiiii aaaaaa
kodi inu mwasowa zopanga pologalam mwayiyambayi ilibe mutu olo mukungakabwa zabwelela pitani muzikangonyengana uko agalu inu zazi