chitsitsimutso choir-Chifunga (Tribute to Dr Saulos Klaus Chilima)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 чер 2024

КОМЕНТАРІ • 48

  • @tiyamikekazima9804
    @tiyamikekazima9804 Місяць тому +14

    I don't know why Malawi has never recognize Chitsitsimutso choir in a special way.I have known this choir since I was in Primary school.Respect to this choir❤❤❤❤❤The best choir in Malawi.

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 11 днів тому

    Analakwisa kwambili inakakhala kuti ndingozi athuwa sanakamwalila ayi mwina anakangovulala Koma siku Lina mulungu azaonesa zose

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 11 днів тому

    Achakwera ngati simulapa ndithudi magazi aanthu awa adzakhala pamutu panu mpaka tsiku lodzayamkha mulandu kumwamba chifunga chikunenedwa apa ndinu😢😢😢 akuti tsiku lina dzuwa lidzawala chifunga chidzachoka meaning tsiku ina inuso mudzakhala nyembo 😭😭😭😭😭 imfa ya chilima pafupifupi aliyese akuloza chala inu mwachita kutani inuyo lapani mudakali ndi nthawi 😭😭😭😭😭

  • @florakapachika8501
    @florakapachika8501 26 днів тому +3

    Great ❤❤job well done guys mwaimba momveka bwino ndipo movetsa chisoni how l wish malawians could recognise you.may the soul of SKC continue resting in peace taluza great man you will remain in our hearts forever bwana 😢

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 17 днів тому +1

    You're really our heroes keep on going, may living God continue blessing you guys

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b 10 днів тому

    Uzakungunukatu siku lina amalawi azaziwa zonsezo coming soon kuti tiziwe chilungamo mr chifunga uzakungunuka siku lija likubwela ukungunuka zuwa la yehova likazawalamo

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6d 17 днів тому +2

    Very very brilliant song guyz mumatha kupanga compose nyimbo mwaliladi mosanyengelera ayi may his soul rest enternal piece

  • @wondermsibe1708
    @wondermsibe1708 Місяць тому +3

    Well done guys chifunga ndi chakwera yah yah

  • @wondermsibe1708
    @wondermsibe1708 Місяць тому +3

    Ngozi anayipanga yinatheka Koma kutuma anthu opanga chisoni kukamaliza chifunga chakwera mmmmn ndalama unabwereranji athu ataya chipangano Mai ine mmm😊maso gwaaa

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 12 днів тому

    Iwe chifunga😢😢😢

  • @user-el3tk9qd2o
    @user-el3tk9qd2o 28 днів тому +3

    Chifunga tsikulina chidzakungunukadi nyimbo yokhudza

  • @user-xv6hs7kd1l
    @user-xv6hs7kd1l 12 днів тому

    What a song..chifunga chinatiphweteka..tikudikira dzuwa layehova❤😢

  • @AndrewBiliat
    @AndrewBiliat Місяць тому +1

    Legends in music at the same time RIP Dr. Chilima

  • @williamskaudzu3523
    @williamskaudzu3523 22 дні тому +1

    Continue Resting in Peace SKC. You were our hope for a better Malawi. All in all, we Praise God Almighty in everything 💔

  • @DanielChiwawula
    @DanielChiwawula 13 днів тому

    Lukas Kaphereni and others RIP

  • @preciouschifundo9390
    @preciouschifundo9390 28 днів тому +1

    Great work

  • @LoizioPhiri
    @LoizioPhiri 4 дні тому

    😢😢😢😢😢😢mmmmmmmmmmmm chifunga cikungunuke pompano

  • @josephmakwete2915
    @josephmakwete2915 18 днів тому

    Chisisimutso imatha kuimba hvy ❤❤

  • @DanielChiwawula
    @DanielChiwawula 13 днів тому

    Zosamvesetseka Koma God is good

  • @comfortBechani-z7q
    @comfortBechani-z7q 15 днів тому

    This choir is number one in malawi

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 12 днів тому

    Mcp paulendo basi

  • @MARYMARY-ho8qt
    @MARYMARY-ho8qt 16 днів тому

    One hell of talent here❤❤❤❤

  • @sahaluhanga5727
    @sahaluhanga5727 16 днів тому

    Dzuwa la Mulungu likubwera iwe chifunga

  • @luciaelisa872
    @luciaelisa872 Місяць тому

    What a touching song ,RIP SKC😢

  • @preciousmaele190
    @preciousmaele190 28 днів тому

    Zoona iwe chifunga chakwera kupha anthu osalakwa

  • @GiftAlubi
    @GiftAlubi 29 днів тому +1

    Rest in peace doctor chilima

  • @IshmaelWilliam-z4w
    @IshmaelWilliam-z4w 22 дні тому

    Great

  • @user-cb5me8wp1k
    @user-cb5me8wp1k 29 днів тому

    Ikufunika aitane ku nyumba ya pre akaimbe nyimbo yabwino

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 12 днів тому

    😭😭😭😭😭

  • @Jessymsowoya
    @Jessymsowoya 6 днів тому

    😭😭😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 29 днів тому

    Uzakungunuka

  • @giftkolopo6483
    @giftkolopo6483 Місяць тому +1

    RIP SKC

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e 29 днів тому

    Zoona imfa ya chilima ndi anthu ena ndi yovetsa chisoni

  • @kennethgondwe5534
    @kennethgondwe5534 Місяць тому +1

    Chitsitsimuso choir is the best

  • @princelonje7833
    @princelonje7833 17 днів тому

    Rip chilima 😢

  • @IreenNgwira-k2z
    @IreenNgwira-k2z 15 днів тому

    RIP SKC😢

  • @StivinBazarBazar
    @StivinBazarBazar 18 днів тому

    Ameni

  • @chimssululu3740
    @chimssululu3740 23 дні тому

    😢

  • @MussahWilliam-py1ff
    @MussahWilliam-py1ff 27 днів тому

    Chifunga

  • @WinfridahNjobvu
    @WinfridahNjobvu 16 днів тому

    Mm mm God why

  • @solomonmunthali610
    @solomonmunthali610 29 днів тому

    Literature

  • @patriciakenmuir
    @patriciakenmuir Місяць тому

    Please taponyani nyimbo zambiri za chitsitsimutso