BREAKING NEWS - SAMEER SULEMAN WAKAZIPEREKA EKHA KU POLICE ATAMVA KUTI AKUSAKIDWA KUTI AMANGIDWE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 7 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 119

  • @DianaBulukutu-zx7nq
    @DianaBulukutu-zx7nq День тому +8

    Mulungu ndiwabwino nthawi zose koma satana sanawineko nkhondo nthawi zose mulungu amapambana

  • @jacobutonga3765
    @jacobutonga3765 День тому +9

    Mulungu wawumitsa ntima wa chakwela kuti ukulu wa yehova ukawonekele,.zidachitikapo izi ku Egypt.mulungu wathu sagona tulo,

    • @DianaBulukutu-zx7nq
      @DianaBulukutu-zx7nq День тому

      Mulungu salakwisa popanga zinthu muchilichose timuyamike mulungu basi mulungu amatha kuwononga zinthu zina cholinga zina zikozedwe😊😊

  • @lacfunnytv1251
    @lacfunnytv1251 День тому +6

    Kwa amene ngakhale close to those guys, muwauze azivala ma mask akamangidwa and they should avoid handshakes

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s День тому +3

    God is righteous all the Times.

  • @billybanda7280
    @billybanda7280 День тому +8

    MCP will never rule this country again!!!! No matter what!!!

  • @JamilaJafali
    @JamilaJafali День тому +1

    Allah akutetezelen brother samil

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg День тому +6

    Chitukuko mukulephera mukungoziwa kumanga anthu pathako pamanu

  • @JoseKeyaton
    @JoseKeyaton День тому +7

    Zopanda ntchito zimenezo olo atamanga akulu akulu onse a DPP Koma ovota ndife amene asakutimangafe tionana kovota komweko osaopa DPP more 🔥🔥 🔥🔥🔥🔥

    • @isaaczuze
      @isaaczuze День тому +1

      Chisilu iwe osakhala chete bwanji mbuzi iwe ....muzingodya ndalama zokuba kuchokela Kwa chibekete chanucho .....chakwera ndi mbuzi ya .munthu .....munthu wosamva zonena za anthu

    • @GraciamHarrisonthom
      @GraciamHarrisonthom День тому +1

      Kkkkkk amwene palibe chotukwanira munthu apa akuti anthu okavota ndiomwe sanamangidwe meaning anthu akavotera dpp olo atamanga akuluakulu onse koma dpp izavoteredwa

    • @HestingsChibalo
      @HestingsChibalo День тому

      ​@@GraciamHarrisonthom Akozeni azanu mwina samve bwino 😂😂😂

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda День тому +2

    Suleman ndi great man

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf День тому +3

    May the powerful but unseen God lead His people in every situation. May Him be the best Jugde in all the trials. ✝️🛐

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n День тому +3

    Ayishosha akhaula chaka chino
    palibe chomwe tapindula ndi ulamuliro wanu mmalo mwake tazunzika
    Gospel Kazako ankati mukukonza dziko kumene mwapangaku ndikukonza dziko kapena kuwononga?

  • @JosephMakatha
    @JosephMakatha День тому

    Koma lero kwaphulik nkhani 😢😢😢

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b День тому +1

    Komatu mukuchedwa ndiku manganako bola mutamapanga campaign izi muchedwazo

  • @ManMen-kp2ze
    @ManMen-kp2ze День тому +1

    Mulungu waumisa mtima wa Chakwera kuti kuyipa kwa MCP konse kuonereree

  • @YusufJafali
    @YusufJafali День тому

    History is the best teacher

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День тому +1

    Koma sanamuone......mzungu Peter muthalika.....sana mangetu munthu anthu Tinalakhula.....mene tigathele koma mcp ayi...zikomo tionana koka vota😢😢😢😢

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august День тому

    Uku ndikutha kwa MCP akuopa DPP uku kuli akatundu tangolowa 2025 ayamba kunjenjenera kumamanga nao anthu ndiye a mcp muva mazi simunati yembekezani pa 16 September

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr День тому +2

    don't throw hope god watching everything

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x День тому

    Mulungu yekha odziwa akhala nanu nose woipayoo athawa yekha

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День тому

    Ndipo the dc Ananena karetu kuti anthu Adpp dere mumagidwa ambili mukozekere.....relo ndiizi......Achi hana ..nde ena onse mukozeke....the dc anatero...koma Boma ili😢😢😢😢😢😢🙌

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 День тому

    Amene anatinamizanso za BLACK BOX ujanso amangidwe .Why only opposition leaders are being arrested?

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix День тому +3

    Koma m cp inuyo mukuzuza anthu koma choti mudziwe boma rikasintha nose mukafera kundende zitsiru inu

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i День тому +1

    A Chakwela kumbukilani kiti munali m'busa , bwanji mukuzunza ana a mulungu , remember your actions will come back and bite you

  • @RoneckKagoro-pn5cl
    @RoneckKagoro-pn5cl День тому

    MCP ikuoneka kuti ikufuna izipanga zithu zolakwika koma anthu asamawadzudzule ndiye akamapanda kudzudzulidwa ndiye iwowo akukhala ndi dziweto kapena khuku

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d День тому +2

    Chipani chochititsa manyazi kukanika kwavmanga anyamata azikwanje bac zaiii sakunama Samia sulaiman pakhani yo funa ku mumpaka mcp ndi chipani chokumpa kaaa amayenela auze mtundu wa Malawi 🇲🇼 ka

    • @HenzelMikolasi
      @HenzelMikolasi День тому

      Awamanga bwanji anyamata azikwanje pomwe amawatuma ndiomweo, evil people

  • @JoseKeyaton
    @JoseKeyaton День тому

    Akuziwa Kuti thawi Yao yatha ndie amangiletu azao Chaka chamawa ndi iwowa omwe akhare ndendemo God for bit

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 День тому +1

    Aaaaaaaaaa akufuna kuwopseza opposition, mind u anthu amenewa especially suleman asadwale or kufa in next 5yrs tidzangodziwiratu kuti ndi boma la MCP to be responsible

  • @HopeMakoka
    @HopeMakoka День тому

    Ndiri sure kuti ulamuliro Wa chakwerawu ulibe tsogolo n ndi Wa one party system, opposition leaders khalani maso achoke awa Malawi sikuwafuna

  • @Kamwachale
    @Kamwachale День тому

    Nanga zaka 5 za boma la MCP akugufuza nkhani za Salima sugar lero ? What stupidity and lack of seriousness in serious issues.

  • @LeonardFolokiya
    @LeonardFolokiya День тому

    More Dpp top members will be arrested including peter Mutharika,munthawi yawo zambiri sanaziyendese mwachilungamo ayi.. it's time to learn kuti moyo umasintha ukakhala patop usamaone ngati wafikapo ayi munawonjeza amalawi anakwiya nanu munthawi yanu kololani zomwe munafesa basi

  • @yamikanijoseph9381
    @yamikanijoseph9381 День тому

    Kodi poti tikupita kumavoti anthufe tikapalamula lamulo, lamulo lisiye kugwira ntchito chifukwa choti kuli kuponya voti mu September? Anthu enanu mitu yanu ndiyotani, fundo kaperekani zomanga dziko, advisory to the ruling government, not condemning, be constructive, osamakalipira boma, likondeni boma polankhula mwaulemu, pozindikila kuti even DPP nthawi yawo inaliso ndi zofookaso. Kusiyana maganizo sikuoneka pokha pokha tikunyozana, titha kusiyana maganizo and argue constructively, anthu tiphunzireso penapake to Talk with dignity, zikatero no arrest warrants will be seen. Koma kunyoza leadership ngakhale Mulungu amadana nazo.

  • @Wyson-bo3sp
    @Wyson-bo3sp День тому

    Mdima ungachuluke Maka sungagonjetse kuwala, mulungu wakuyetsani koma mwalephela

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 День тому

    Mcp nyamanu ndithu kodi afiti inu okupha anyalugwe nchito yanu kumanga anthu mulibe zochita akanga ndiwamba nditukwana kwinaku

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley День тому

    Ok nanu muzaziona Ndithu kuposera pamenepa muzaziona musazalire

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka День тому +5

    Koma mr chakwera mulungu akuyendereni mwapadera koma mulungu salakwitsa kalikose

  • @GadgetSquare-n7h
    @GadgetSquare-n7h День тому +1

    Komatu aziziwa kuti asuleman ndi amwanamveka sabvota okha tionana pa 16 sept pano

  • @yamikanijoseph9381
    @yamikanijoseph9381 День тому

    There is no opposition in talking shit about the ruling party.

  • @ManMen-kp2ze
    @ManMen-kp2ze День тому

    Chitukuko cha MCP nchomenechii, njala mu dziko, kusowaaku kwa mafuta a, kugwa kwa chumaa, kuopsyeza anthu ndi zikwaanjee, kumanga anthu onse olomba mitima a ku opposition,

  • @HenzelMikolasi
    @HenzelMikolasi День тому

    Koma anthu awawa ali ndi zolinga zazikulu eeh eeh kulamula kokhakokhako zoipa zonsezi muchitira amzanu

  • @KUCHEKATULI
    @KUCHEKATULI День тому

    Bwanji kumangidwaku akungomangidwa anthu osusa boma onkha?
    Akuboma sakumamangidwa chifukwa chani?

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis День тому

    MCP mangani kaye. Omwe adampha anthu ten aja inluding akasambala amfiti otamba masana inu okudya matewela amanyi amwana

  • @EnerstMwitha
    @EnerstMwitha День тому

    Chanjezo mayi yolamu komaso inu anduna azichitezo asapangidwe chipongwe ndipo akamphedwa pavuta ife tilipambuyo pa summer msuluman osaipa tilipabupo ngati abiyeni palibe ine ndisitha basi chifukwa zanga sangakhale chikangawa andimpa ndithu chipani choipa ndithu mbili sitidzawala ndipo tidzampizitsa ana athu kuti asadzaiwele zachipogwe zomwe mr chikangawa anatichita anatichita abiyeni we will not forgetting forever naver never never never never never limbini m'tima summer msuluman osaipa

  • @HambeyaniChalie
    @HambeyaniChalie День тому

    Kwa ine achita bwino kukadzipereka kokha wapeleka bwino umboni wako omwe amafuna kuwaphawo kuti omwe atchulidwawo ayimbidwe mlandu kamba kufuna kupha munthu ndi mlandu

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale День тому

    Awo a times ndi ma cadet a dpp

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka День тому

    Campaign wanji ameneyo

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer День тому

    Achita bwin ndip akwanilitse zomwe akufuna pamoy wa asuleman coz chakwera Ali ufit iti akufuna magaz amalawi ose ndy ap sitikuona zachilendo

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis День тому

    MCP mbuzi za anthu mukudzipangabe decampaign

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo День тому

    Moses kumkuyu paja ati amangidwe anasunga black box

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 День тому

    Zonsezi kwoopa Dpp salima sugar what??? Thawi yonseyi munali kuti kumadikira ma election ndipo inu amcp mmene mukuberra inu ayi zikomo..

  • @salmankhanofficiel.5018
    @salmankhanofficiel.5018 День тому

    Wa Bakili muluz TV uja si muthu wamba

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz День тому

    Nkhaniyo ndiyowona mcp ikufuna kupha anthu 17 sure?? Kodi amene muku supporter chikangawa mulindi umunthu??? Chifukwa chikangawabwagulitsa nyanja fertilizer dollar palibe chikuyenda sure basi eeeeesh mutitukwanitsa

  • @blackcobra-b2y
    @blackcobra-b2y День тому

    Zakhala bwino zimene amalakhula akalankhulile pa court!

  • @Kamwachale
    @Kamwachale День тому

    The police is too stupid. Thought the police could have arrested chimwendo Banda, zikhale Ngoma and the other person for being suspected to kill Suleiman. What type of silly and unprofessional thing is this of Malawian police

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j День тому

    Chikangawa party yatha ma plan

  • @RAYMONDMpingasa-y8s
    @RAYMONDMpingasa-y8s День тому

    Kumangana nthawi yake sino mulekeletu

  • @KelvnGrin
    @KelvnGrin День тому

    Sibwino kumamangana thawi itasala pang,Ono kuvota zingobetseratu kuipa kwabomali ndithu nanga kale lonse adalikuti amwanaveka mmm mmalawi ayi

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 День тому

      Ndipo inu thawi yonseyi am adikila chani ndipo mmene kubera amcp aaa anthu awa ndiwoyipa zedi💔

  • @TsuzenThomas
    @TsuzenThomas День тому

    Boma lamanyi nde amanga anthu angat kod, bwino wake okavota ndfe amalawi tizakaonana pa September 16 hiyaaaa

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale День тому

    Apeleke umboni okwanila tidziwe zowoona

  • @floneyspedi3072
    @floneyspedi3072 День тому

    Chakwela mosabisa mau anapha chilima pamodzindi anthu ena

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo День тому +3

    Amalawi tisafooke tipemphere molimba

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 День тому

    Apolisi a ku Malaŵi ndi zimene amazidziwa sulemani sanachule munthu pa DPP TV koma,anali otumidwa ndi MCP, chifukwa DPP ndiimene ili patsogolo akufuna kuifooketsa DPP

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l День тому

    2025 ndichaka chotaya mwazi mumalawi mcp ndiyankha

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon День тому

    OSATI WAKAZIPEREKA KOMAKUTI AMUITANITSA MUSAMAONJEZERE NKHANI . KODI MCP IKAMAMANGA ANTHU NDIYE DEMOCRACY YO ILI PATI MCP IKHAULATU

  • @GeorgeSathula
    @GeorgeSathula День тому

    Koma chakwera ali ndimtima wamanyi omwe uja wa mu 1970 omangana uja cholinga anthu azingoti inde bwana unya chakwera

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi День тому

    MCP nokha muziipitsira mbiri yanu apapa bwezi mukukoza zithu kuti anthu mwina akhale ndi confidence mwainu koma the more mukumanga anthu the more you are giving votes to DPP

  • @donzkauwa6584
    @donzkauwa6584 День тому

    Mulungu awatetezele

  • @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
    @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb День тому

    Koma Mulungu amafunikadi nthawi yamavuto ayi zikomo

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 День тому

      Iwe umati asalaso mr chikangawa ndi team yawo...aziona black box tikuifuna ife

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata День тому

    Ayi mkaladi ameneyu ayenera kumangidwa chifukwa mphavu ili ndi a police.

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d День тому +2

    The Dc wamisala adawona khondo adanenatu padzana

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson День тому +1

    Mcp mcp mcp ayi ndithu

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 День тому

    Chakwera tawelengani book of eksodo pharaoh anatani pa ana a Israel inutu mulangidwa koophyaa ndipo muzakhala munthu osowa mtendere malawi yense akukudandaulani inuyo bwanji koma????

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v День тому

    Kodu moti mu mcp mulibe chinyengo wamangako ndani??

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz День тому +2

    MCP ikuyesetsa kupweteka DPP kufuna peter mutharika atulukile

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 День тому

    Osatopa osafooka komanso osaopa ,
    Tizafela mbendela ya malawi , komanso mcp sikukulowanso m'boma

  • @hashimmtelera9536
    @hashimmtelera9536 День тому

    Tsono akuti Republic versus Sameer Suleman? Who is republic in this case?mmesa it's an individual not republic

  • @rittakawiriza
    @rittakawiriza День тому

    Tatopa ndi boma longokhalila kumanga anthu mmalo mukonzanso zinthu Maka Maka kulimbans ndi njala ,mankhwala mzipatalamu,nkhani Za kusowa Kwa mafuta, Kodi democracy ndi ye ili Pati?

  • @FrazerMunyinda
    @FrazerMunyinda День тому

    Chikangawa party

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe День тому

    Nthawi yonseii anali kut abomaoo chikangawa nyau party

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z День тому

    Tingoyamba kuchita ziwembu apolice basi

  • @Noel-y6t
    @Noel-y6t День тому

    All this is purely political prosecution .MCP please stop this torture and killings. Malawi did choose to say no to this in 1994.We are democratic country that need to be put into practice. Zenje lokumbira wina mawa umagweramo ndiwe mwini.Dont say i did not warm you guys.

  • @fahadcade512
    @fahadcade512 День тому +2

    Ambuye mulungu kumwambako rangani chipani cha mcp ndipo yemwe akuchuridwa kuti chakwerayo ipani akapume akuzuza midzimu yambiri

  • @MaxwellChabwera-y7x
    @MaxwellChabwera-y7x День тому

    Chakwera pamtumbo pako galu limodz ndi otsatira ako ovota ndife

  • @MASEKOMGWAGWA-s4k
    @MASEKOMGWAGWA-s4k День тому

    Koma kumalawi

  • @AustinGomani
    @AustinGomani День тому

    Mcp yamagazi

  • @MabasoMafa
    @MabasoMafa День тому

    Sanalankhule bwino ayenera kumangidwa osamutulusa

  • @SpencerWhayo
    @SpencerWhayo День тому

    This government is full of shit

  • @LloydKasuwel
    @LloydKasuwel День тому

    Zaboza izi

  • @JamilaJafali
    @JamilaJafali День тому

    Mavotitu awa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze День тому +1

    Koditu munthu wokuba amaopseza anthu kwambili .....kodi mr suleman alakwa chiyani komatu ili ndi ziko .....zinthu zimasintha .musaone ngati mukhala pamenepo mpaka muyaya ..koma ndikanaziwa sindikachita ....munthu kumuolosa msinje lelo watiukila ....ayi tizaona

  • @BonifaceMwanza-r6y
    @BonifaceMwanza-r6y День тому

    Zosakhala bwin

  • @ChikondiSabe
    @ChikondiSabe День тому +2

    Bon kalindo ananenat paja kut amanga akulu akulu azipani zina

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza День тому

    Mcp ikusowa zochita

  • @FredrickMoirchitalo
    @FredrickMoirchitalo День тому

    This government has gone to the dog

  • @okoma247
    @okoma247 День тому

    Achimwene chonde mukamawerenga nkhanizi muyesese kupanga pronounce “r” as it is and “l” as it is. Am sure mmene mumapita ku Secondary School, you had been taught to pronounce r as it is and l as it is. You keep pronouncing “r” as “l” so the news doesn’t appealing because it seems like all Malawians can’t speak English which is a pain.
    Please try to exercise on pronunciation

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm День тому +1

    Chipani ichi chili ndi masiku ochepa ndpo akukhalira kuophyeza anthu kumanga anthu chakwera ife sitikumufuna olo pang'ono

  • @JosephKwimbayani
    @JosephKwimbayani День тому

    Sizachilendo

  • @BobJoshua-q5n
    @BobJoshua-q5n День тому +1

    Ngakhale mutamanga onse but we will not vote for MCP but DPP
    address your careless management of our economy
    we have hunger lack of fertilizer and many more and you MCP must do something because you caused all this

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA День тому +3

    Kma mcp your dys are numbered 🤞

  • @DanielChinula
    @DanielChinula День тому +1

    More fire mcp amayankhulisa ameneyo dpp idatikwana

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson День тому +1

    Asachenjele pakuti ali m'boma izozo ndi zoona mcp ndiyakupha kumene tidzaonana akadzaluza.