Joe Gwaladi live in Cape Town
Вставка
- Опубліковано 5 жов 2024
- Our Cameras witnessed this energetic (Professor) Joe Gwaladi performing for the first time in Cape town at Pakwathu Braai restaurant.
follow us
Facebook - / reflopictures
Instagram - / reflopictures
Twitter - / reflopictures
Read our monthly magazine on the link below
www.reflopictu...
Well done our Professor your number one❤❤❤❤❤
We love Joe gwalad much ❤❤❤
❤❤❤
work well done❤🔥
Machine
Gwaladi woyeee
professor Joe Gwaladi💥💥💥
Wati professor
I'm from zimbabwe and I'm a big fan but this was bulshit this Joe need some respect
Agwaladi inu ndi number wanu, muli mu gulu la oyimba akale osaguga, anthu amalawi timakukondani kwambili, langizo ndiloti zija mumapanga mukalezela musiye anthu amakutengani ngati ndinu amisala
Aaiiile!!!🤣🤣🤣 man joh.
Ati agwaladi alibe chuma
Band siinamuthandizeyi ataaah anthu ake a band amalephera kuimba zida aaaaaaa or keyboard kulephera kuichuna aaaaaaaaaaaa
Mmmm koma hule uyu kkkk
Next time adzatenge band yokutha kuyimba bhobho
Ndipo live
Zoonas band siinamuthandizeyi ataaah, band imayeneka iziyambitsa nyimbo yokha n amadziwa kulowetsa zida bwino Koma apapa sanamuthandizeyi koma amadziwa kupanga perform bwino
Suzatheka
band yo tu zot wina ali mu off key zosawakhuza
Kkkkk Ati ayambe kumbuyoko abele amenewo ma randiwo
Ine gwaladi amandiwaza can I have his number
❤❤❤❤