ZOMWE AYANKHULA A CHAKWELA LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 32

  • @dysonfysonchifundo2284
    @dysonfysonchifundo2284 2 місяці тому +1

    Palibe chomwe ndikutolapo 😮

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh 2 місяці тому +1

    Thank you very much mr President
    Mau Achilimbikitso kwambiri
    Tinkhululukileni ngakhale timakunyozani ndife Amalawi
    Timati anali wabwino atachokapo
    Your a Father for everyone
    Please forgive us

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому +1

    Achisiru awa Chikangawa party pamaso ngati wachilungamo koma wakupha zedi

  • @geralddickson6
    @geralddickson6 2 місяці тому +2

    😂😂😂😂 Zikhale Ng'oma Koma Amutchula Apa Kapena Ndi Kape Basi Kkkk Angomutuma Zopusa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins Місяць тому

    Simunati ma cadet mulira

  • @MaryNyirenda-nq3mh
    @MaryNyirenda-nq3mh 2 місяці тому

    Afiti anthuwa 😢😢😢😢😢 atiphera anthu osalakwa ambuye ziwoneseleni mlipati 😭😭😭😭 ambuye mukuloranji kut satana atizuze chotele ambuye mulipatiiiiiiiiiiiii tipulumuseni anthuwa akuwoneka ngat ndiwokuwopani inuyo koma lilibodza akukhozelabe ziwembu kwa anthu osalakwa ambuye timenyeleni nkhondo awoneneseni kut ndinu mulungu 😭😭😭😭😭🙏

  • @geralddickson6
    @geralddickson6 2 місяці тому +1

    Aaaa Mesa Kod Munati Simanali Busa Ndeno Lero Mwati Munaliso Busa kkk😂😂😂😂

  • @GeoegeGRSHala
    @GeoegeGRSHala 2 місяці тому +1

    Zoona bra

  • @SamboMaria
    @SamboMaria 2 місяці тому

    Speechless

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane 2 місяці тому

    Azisilu inu nkhope ngat amakaka

  • @KingstonPhiri-g5h
    @KingstonPhiri-g5h 2 місяці тому

    Galu kwabasi ameneyi chikangawa yi

  • @MathiasEgama
    @MathiasEgama 2 місяці тому

    I think alhomwe samaziwa kuti pa history ya Malawi from 1964 palibepo mu lhomwe

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому

    Achakwera mapwala ako iwe kuno area 25 kuno tikuti iwe ndi mbunzi yachabe komaso chisiru chamunthu kwambiri iwe koma ndimunthu wabwino bwino

  • @UladMusah
    @UladMusah 2 місяці тому +1

    Achakwela palukundu punu alipwisi

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 2 місяці тому

    Ndikhale mbuli pankhaniyi

  • @KennethDzama
    @KennethDzama 2 місяці тому +1

    Pot smulakwitsa ambuye km muonen uyu

  • @MadalitsoMeyah
    @MadalitsoMeyah 2 місяці тому

    Koma akupuma akulu amenewa awa

  • @Malume2024
    @Malume2024 2 місяці тому +2

    Wakupha uyu

  • @Hopenandola-zg6kz
    @Hopenandola-zg6kz 2 місяці тому +1

    Ine uli si prendent yaine ayi

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому

    Zomwe ukuziwa kupha ndi kuba basi

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona 2 місяці тому

    Zakumusi kwako

  • @captainmdima1102
    @captainmdima1102 2 місяці тому

    Thanks

  • @EdsonChiwereChieere
    @EdsonChiwereChieere 2 місяці тому

    Kkkkk kulira kwa macadet kma ndye mukadalira anthu ajelasi inu 😂😂😂😂 mpka 2030 mukulira

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri1799 2 місяці тому

    This President will not freely rule Malawi in the absence of Chilima. CCAP stop inviting this man to your church programs.

    • @PociahMack
      @PociahMack 2 місяці тому

      Asiye chifukwa chani. Bingu amamuyita ndipo amapita ndipo olo chakwera upresident utatha, amene adzakhale pa mpando azitayitanidwa ndithu.

    • @DicksonLutere-p9k
      @DicksonLutere-p9k 2 місяці тому

      Walodzedwa Kodi ase

    • @DicksonLutere-p9k
      @DicksonLutere-p9k 2 місяці тому

      Fodyatu akupengetsani

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 місяці тому

    CHILIMA MUNAMUPHA CHIFUKWA 1, KU MCP MITIMA YANU KOMANSO NKHOPE ZANU NDIZONYASA. 2, MUKUFUNA MUKHALEBE M BOMA 2025. 3, KUBISA MILANDU YOMWE MWAPANGA AND ETC

  • @JanuaryGwere
    @JanuaryGwere 2 місяці тому

    Kodi ndi zachipani

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 2 місяці тому

    Ma cadet chonde polani moto mavuto si alhomwe okha plz

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 2 місяці тому

      Kkkk koma ndiye wayankhula ngamotu 😅😅😅