Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Sewero lophuzisandthu . Tikuphuzira kuipa kwamiseche, kuyipa kochedwesa matenda kupitanawo kuchipatala, komaso osamaganizirana zaufiti. Koma vuto ndiloti mumawachedwesa masewerowa kubweresa. Pamene mwatipasira iri, padusaso nthawuyayitali musadabwerendi wsewerolina😢😢😢😢
Gaga and tonde musaza. Mwalile chonde
Mukumachedwa koma kupanga post tonde wadula , , , , is best morethan mfumu kazi or mdyangu comedy
Gaga # 1 chifuniro osamuiwara nthandizi kkkkkkkk
Koma Gaga uzathera mmanja sure!!!! Miseche four much kkkkkkk
Mude ndiwe wabho koma comwe ukufuna sitikuchidziwa😂
We are proud of u,gaga umusamale tonde akupha ndi mwana kkkk,watching from durban
😂😂😂 ndakayi ngati ndeu yatonde ndi gaga ingazathe kkkk
Gaga ndi Tonde pali udani ooopsa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Anapondetsera pakhasala yachibelokero pa khomopopo
Gaga akufuna kutenga malo a Tonde 🤣🤣🤣🤣
Gaga ndi Tonde kukanganila m'godi
Iyayi Gaga waonjeza mabodza
Gada utaphedwe ndi mwala from Tonde. Kkkkkkkkk Chiphwanya eeeeeee unaipreka cancer ndiwe😂😂
Gaga anakonza mabidza ngati nkazi
Komaso akumachedwesa timawakondatu makomede anuwa
I'm watching in south Africa
Osayiwala next ikatuluka
Pena pake sizikukhala bwino mukumaduphisa kwambiri sewero lathela pena ikamazayamba ikuyambilaso pena why??? End tsiku lomwe mumatipasila sewelori ndi thursday mukutipasa lero zimene zili zosiya kwambiri try to improve that thing plz
Kodi ma episode awa anajambulidwa liti kunjako kukuoneka green, kummwerako pano kuyenera kukhale kwauma
😂😂😂😂gaga the great snapper
This is my property 😁😂😁😂 tonde the great
Zili bwino kwambili koma zomadumphitsazo zilekeke
Tonde mwala wakula iwe
Tonde timamutsata koma kuchedwesa kwambiri
Gaga maboza azatha kkkkkm
Kkkkkkkkk koma gaga. Ndimavutoso ena eish
Mr Gonxo worshiping from benoni south african
Mumakwana guys kkkk
Good play
Gaga mulizinthu
Makwana
Moni kwa abambo a dora😂
Koma atonde ndi miyala mmmm
Guys mukuchedwa kwambili kupanga upload mpaka 3 weeks
😂😂😂😂😂😂 gaga
mumakwana
Mwatimvetsa kukoma gyz 😂😂
Kkkk Gaga ndi Tonde anakonza
Thanks takhala tikudikila
Koma Gaga mamboza
Zoonad Gaga
Keep up the good work
Koma lachedwa bwanj tonde
Amakwana chimphwanya
Kmtu mukuchedwetsatu
The problem with u guy's... You are taking long time to give us comedies... Try to do as how mdyangu doing🎉
Those people from mdyangu they got sponsor while these people from Tonde they don't have any sponsorship that's why they takes so long to give us, so is sample to us to help them as we can so that we can make them easier to give us new episodes
🎉🎉🎉🎉 umatha
Kkkk ilibwino kwambili
🤣🤣🤣🤣