BASI KU NDIRANDE SIKUZATHEKA TAONANI ZOMWE ZACHITIKA PROF, ARTHUR PETER MUTHALIKA ATANGOFIKA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 99

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 15 днів тому +4

    APM MULUNGU wazatheka bwanji apitilize kukutetezani kukudalisani ndi kukupasani moyo wautali 🙏🙏

  • @SimonMochede
    @SimonMochede 15 днів тому +2

    God bless APM and bless Ndirande too, proud of you Ndirande people

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 15 днів тому +2

    Gd bless Adad. My vote💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 15 днів тому

    Kuyendesa boma sikumafunika nthumbidwa zowonadi izi zimafunika akulu akulu ooooo ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @FraiserChilingulo
    @FraiserChilingulo 15 днів тому +2

    APM YEHOVA Akumenyereni nkhondo❤

  • @CharmaineGoncalves-k7e
    @CharmaineGoncalves-k7e 15 днів тому +1

    Chakwera n Chimwendo n Nkunkuyu atsegula mmimba mwakamwazi APM more fire 💪

  • @SaimonDavide
    @SaimonDavide 15 днів тому +1

    Ali ndi mwana agwiritsee, kundilande,more Fireee!!!!!!!!

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 15 днів тому +2

    God bless APM . MY VOTE

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 15 днів тому

    God bless you Apm💙💙💙💙💙

  • @BeatrinceChanza
    @BeatrinceChanza 15 днів тому

    Adadi omwewa kut wa wa wa my vote my vote ❤❤❤ chikangawa atsegula m'mimba.

  • @IdirissaCharles-s8g
    @IdirissaCharles-s8g 15 днів тому +1

    ❤❤❤❤❤❤ my vote adad dpp 🔥 chakwera uziona ndimanganya wakoyo wava

  • @RuthSignal
    @RuthSignal 15 днів тому

    Adadi my vote ❤

  • @GeoffreyMarko-v3s
    @GeoffreyMarko-v3s 15 днів тому +9

    Ife kuno ndirande chikangawawa ayi 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @tinkaphethi1395
    @tinkaphethi1395 15 днів тому +3

    Limbe Market was filled up and people were waiting for APM...It our hope that the organizing team will consider..for a continuation of the whistle stop in the City of Blantyre...Manase, Chilobwe, Zingwangwa, Manje, Limbe market, Chigumula and Bangwe

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 15 днів тому +2

    😂😂😂😂Komatu APM ndiozodzedwa guys I think Angelo kumwamba nawonso Ndia DPP sure😂😂 Bomaaaa ilooooooooo ❤❤❤❤❤❤

  • @BarnetMwanyula
    @BarnetMwanyula 15 днів тому +1

    Azabwereso wina uja utsiku tizaone like this . Tizaone ngat sazayenda chozemb

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 15 днів тому +2

    APM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥boma watenga ndithu

  • @LindaChikwawa
    @LindaChikwawa 15 днів тому +3

    Ndirande osazaiderera apm my vote 🔥 🔥🔥

  • @RobertNkhomanyamuka
    @RobertNkhomanyamuka 15 днів тому

    Great job brother

  • @SuperBuild-k9s
    @SuperBuild-k9s 15 днів тому

    Koma uyu kumwamba kudyele nyama ❤❤❤❤

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 15 днів тому +2

    Boma ndila Dadi basi🎉🎉🎉❤❤❤

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 15 днів тому +4

    Kuno ku state house tili busy kuonera zomwezi ndipo ma bp athu akwera 😂😂😂😂😂

  • @DicksonEvance-h6g
    @DicksonEvance-h6g 15 днів тому

    My vote

  • @AndrewChampionKapyola
    @AndrewChampionKapyola 15 днів тому

    Ati kaya nfitiyo ndi ndani kaya🙌

  • @JosephMakatha
    @JosephMakatha 15 днів тому

    #chakwera akhe madzi basi ...blue love in the air 💙💙💙💙

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 15 днів тому

    Mtumbidwa simayendetsa boma kkkk❤❤

  • @EnifaJoseph
    @EnifaJoseph 15 днів тому

    Ndpo chikangawa ili madzi❤❤❤❤

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 15 днів тому +2

    Ndipo.ndizoona boma lolanda lawakanika. Adad litengen tavutikatu

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba 15 днів тому +2

    Mau mpakana akupitatu,ayankhulitsa adad

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 15 днів тому

    My president a dad I athu awo😀😀😀

  • @BrianMbedza-iz2nd
    @BrianMbedza-iz2nd 15 днів тому

    🎉🎉🎉🎉🎉🌽🌽🌽🌽💐🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Tikavota adade.

  • @NyengoMalili
    @NyengoMalili 15 днів тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @PriscaMussah
    @PriscaMussah 15 днів тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @christophermapenzi3813
    @christophermapenzi3813 15 днів тому

    adadi👏

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 15 днів тому

    ❤❤❤❤

  • @RobertSamuel-p7g
    @RobertSamuel-p7g 15 днів тому

    Livr🎉

  • @JumahBatumeyo
    @JumahBatumeyo 15 днів тому

    Iweyo akutumao machende anu APM my voter

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 15 днів тому

    APM more fire ,,,,, DPP woyee

  • @ChuzyBoy-u1c
    @ChuzyBoy-u1c 15 днів тому +1

    Ulemu wanu adadi ndi Sameer Sulaiman

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 15 днів тому

    Apa kubera ahhh zizayenda ngat mujamutu

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 15 днів тому

    Inuyo amene mukuti peter wakula, mudziwe izi kut moyo wa munthu amausunga ndi Mulungu komanso amapeleka mphamvu ndi Mulungu.

  • @DoreenChiwanda-xv8nm
    @DoreenChiwanda-xv8nm 15 днів тому

    Boma ilooo dpp woyeee

  • @AlexanderBilliat
    @AlexanderBilliat 15 днів тому +1

    Koma nde kuzazatu

  • @Patrickasima
    @Patrickasima 15 днів тому

    I ndimakukondani

  • @RuthKakathera
    @RuthKakathera 15 днів тому

    Pompooooo😂😂😂😂

  • @SOLDIERLOVE-e1q
    @SOLDIERLOVE-e1q 15 днів тому

    Chakwela ndi Mfiti😂😂

  • @rajabkjumbe954
    @rajabkjumbe954 15 днів тому

    Koma ndirande

  • @neemakwagwanjichilalika8274
    @neemakwagwanjichilalika8274 15 днів тому

    President otukwana, it's a pity

    • @chachaamoah3592
      @chachaamoah3592 15 днів тому

      Watukwana ndani apa.zakutuvani kamwereni panadol ngati zakuwawani😂

  • @ChiyembekezoJohn-v8o
    @ChiyembekezoJohn-v8o 15 днів тому

    Anali akuchokera kwanthu ku bangwe

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 15 днів тому

    Koma attraction iyiyi eish

  • @RuthSignal
    @RuthSignal 15 днів тому

    Zukunyasawe manyazi bwanji

  • @georgeohms7692
    @georgeohms7692 15 днів тому

    Tawinaso apaa

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 15 днів тому

    Chikangawa Chakwera akulira matsiku amuthera.

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 15 днів тому

    Chikangawa part ali mmadzi zake zada basi

  • @ibrahimedson1145
    @ibrahimedson1145 15 днів тому

    Ife kuno a mcp pamozi ndi chakwela mitima ili mmalele iwe utipweteka😢

  • @HendrixChaputa
    @HendrixChaputa 15 днів тому +1

    Ati Chakwera ndi ndani??😢😂

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 15 днів тому

    garu chikangawa avotera dpp 😂

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 15 днів тому

    Inu wamisala sangayendetse boma (chikangawa)

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 15 днів тому

    Chakwera ndi mfiti

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 15 днів тому

    Chakwera uzayese kuyenda utsiku chonchi

  • @rajabkjumbe954
    @rajabkjumbe954 15 днів тому

    Chakwela ndi mfiti!!!!!

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul 15 днів тому

    Ati Boma simafunika nthumbidwa

  • @RichardAlick-o8k
    @RichardAlick-o8k 15 днів тому

    Moses kunkuyu ukuti bwanji komwe uliko 😂😂😂😂

  • @LevsonChikalema
    @LevsonChikalema 15 днів тому

    Boma ndilimeneri bas

  • @NgomaRaheem-k2t
    @NgomaRaheem-k2t 15 днів тому

    Ndilande mbambande

  • @InnocentChinseu
    @InnocentChinseu 15 днів тому

    😂😂😂😂😂😂 mwati chani nyimbo yooo chakwera watiii😏😜

  • @MacdonaldMajohn
    @MacdonaldMajohn 15 днів тому +1

    Koma achakwera tavomeredzani kuti dzakukanikani ufumuwu unali wolanda mmdalitso subedwa lero siidzi munaba koma simunabe kayendetsedwe . kake

  • @AndrewChimpikizo
    @AndrewChimpikizo 15 днів тому

    Adad ndi boma ndipo wina azathawa nthawi imeneyo

  • @GiftMajawa-v1k
    @GiftMajawa-v1k 15 днів тому

    Proff akapanda kuwina azakhala amubera

  • @DeborahMmango
    @DeborahMmango 15 днів тому

    Kkkk osusa manyazi bwa paanthu onsewa osusa mukakhale 2 people ziveleni chisoni pomwe mwakhalapo bolanso mukanangokhala chete hahahahahahahahaha

  • @IdianMpindeni
    @IdianMpindeni 15 днів тому

    😂😂😂 koma chikangawa angamudikire anthu mpaka mdima chonchi??

    • @AndySymon
      @AndySymon 15 днів тому

      Ndukaika 😂

    • @AndySymon
      @AndySymon 15 днів тому

      Ndukaika 😂

    • @paulpaseli6310
      @paulpaseli6310 15 днів тому

      Loko chikangawawa sangalole kt kude 😂😂😂. Kugondela angaziwe akufuna amuphese

    • @ChaonekaSande
      @ChaonekaSande 15 днів тому

      Aaaa mayazi blue ndi one ❤❤❤

    • @RachealHarawa-xc9gs
      @RachealHarawa-xc9gs 15 днів тому

      Kumudikira kungotaya nthawi

  • @poemlounge
    @poemlounge 15 днів тому

    Awa azatikomokera akulamulira awa😂 voice yokhayo

    • @symoldicky
      @symoldicky 15 днів тому

      ndiwe kape kusasa mawu kamba kakulankhula kwanthawi yaitali sudziwa ndiwe khanda kod , masala osewo wakhala akuyenda nkumalankhula nde Umat mawu asapite or ukafuse chakwera

    • @poemlounge
      @poemlounge 15 днів тому

      @symoldicky ine zandale sindimakhulupilira aliyense. Even Chakwera or peter or kabambe , onsewa ndizigawenga koma zosamba zija man, eetu cheers basi

  • @BERNARDSIKWESE
    @BERNARDSIKWESE 15 днів тому

    DPP not again, we are moving forward

  • @DanielMbingwani
    @DanielMbingwani 15 днів тому

    Kkkkkkkkk nthumbidwa?

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 15 днів тому

    Boma koma ili

  • @martintivalenji320
    @martintivalenji320 15 днів тому

    MCP yagwa basi

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 15 днів тому

    Kodi nkhalamba yanuni izingopita Ku Blantyre? Ndinu agalu Boma simungatengeso ili

    • @ChristinaLigomeka
      @ChristinaLigomeka 15 днів тому

      Kamwe makhwala a BP usanagwe iweee😂😂😂

    • @ChristinaLigomeka
      @ChristinaLigomeka 15 днів тому

      Olo mtamwa ambuye mtengeni kileti mkudzuka mamawa okavota tingachonge chakwera never!!!!!!!!