Dan Lu walowa MCP ... Koma why?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 38

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 4 години тому +2

    Kodi olo mugule dan luu mukuona ngati mungawine ziko agalu inu .......mpaka kugula munthu pa mtengo wa 5000000000 ....kuononga misonkho ya anthu .....chakwera ndi mbuzi yeniyeni

  • @RABSONSIKELO
    @RABSONSIKELO 3 години тому +2

    Amalawi nsanje inu...let him go....pezan musician wina azikuimbiran kuchipan kwanuko..khalan pansi nde muzifunse kut mu dpp mwatuluka zipan zingat?

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 години тому

    Dun lu ndichisilu kwambili wazinyozetsa monyasa, komabe MPC singawine olo atangula oyimba ose

  • @MajidKasim-pn8kt
    @MajidKasim-pn8kt 6 годин тому

    Machende Ake mpaka 2025 akufunakufela mundale cz kunyumba Samantha vutolake ukamapangachiganizo ulibendalama umazitenga Ngati munthu olwphela Apapa olo atamwalila lelo sitinga Mada ndaule😢😢😢😢😢😢

  • @hassanrasheed1379
    @hassanrasheed1379 2 години тому

    ayende bho ife sitimadya music Dan lu ndiwe wofoyila kape heavy Agalatiya 😏

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 6 годин тому +1

    Oyimbawa alibe phindu pakutukula ziko awa amangoyang,ana ndalama ineso ndamutulika 😅😅

  • @Robertmkango
    @Robertmkango 6 годин тому

    Ndipake ayimba Aku Malawi samapita patali sananame Namadigo nyapako Dan Lu

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 години тому

    Ubwino ndi oti mukulowa mwa tendele koma potuluka khomo lotulukila simuzaliwona chifukwa tu ife zogwesa misozi tatopa nazo

  • @jayries35
    @jayries35 7 годин тому

    Let's gather here and make UA-cam money together ❤️

  • @SamNkhomo
    @SamNkhomo 4 години тому

    Apite ameneyu sathaso kuimba ku DPP titenga kell Kelly

  • @McloudGondwe-x5e
    @McloudGondwe-x5e Годину тому

    Musaiwale ulosi wa malemu Grace Chinga

  • @robertMangochi
    @robertMangochi 6 годин тому

    😂😂😂😂 kima ma Nyssa tijasafa tizakumanenso kumwambako kukaipasa moto nyasaland😂😂😂😂

  • @MilosAdam-h8s
    @MilosAdam-h8s Годину тому

    Chisilu chamuthu osagwilao 😂😂😂😂😂😂😂😂 azalima kusogolo kuno

  • @ChikuMega
    @ChikuMega 7 годин тому

    Inu munava kt chipan cha wina chifukwa cha muthu woymba atakavote ndi iyeyo apite wadyela amneyo ife tamutuluka

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 2 години тому

    Nsanje zanji zomwe muli nazo amalawi iiii musiyeni ndichisankho chake kah aaa. Inu chikukunyasani ndichani

  • @SamuelTchomza
    @SamuelTchomza 7 годин тому

    Kuyimba santha galu uyuu akuona ngati akhoza kulemera ukunama iweyo panyapako unyaa

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 6 годин тому

    Anthu amva kale inu mukuchedwa pati ?

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 6 годин тому

    Adadi uyu wosamurandilapo chisilu ish alibe ntchito

  • @HamuzahMatola
    @HamuzahMatola 4 години тому

    Siyeni akafa ife sitizadandaula

  • @SAMARTEDWART-b1j
    @SAMARTEDWART-b1j 7 годин тому

    Uyu ngwadyela ndipo ndiopoila bwampinuyu

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge Годину тому

    Danluu ndi mbuzi ndimkani anthu anamutuluka

  • @SumayaOsman-de2dn
    @SumayaOsman-de2dn 7 годин тому

    Umbawi wamumvutha dan

  • @BesterWilliam-y3y
    @BesterWilliam-y3y 6 годин тому

    Ine nsatukwanike apa odi ndichokepo

  • @ThokoKanyenga
    @ThokoKanyenga 5 годин тому

    Kma za ndale😂😂😂😂😂😂

  • @VincentKadzinja-q3b
    @VincentKadzinja-q3b Годину тому

    Kape panyapako galu iwe

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 7 годин тому

    Ndiwopanda ntchito uyu

  • @user-JoyNgondoma03
    @user-JoyNgondoma03 6 годин тому

    😂😂😂😂 simungazimvese

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 6 годин тому

    😂😂😂😂😂arozani zanu kkkk

  • @TDalo
    @TDalo 6 годин тому

    Koma naye uyu aaaa

  • @justicechizala8651
    @justicechizala8651 3 години тому

    Adatha awa

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 49 хвилин тому

    Ndkape uyu

  • @GeraldMangani
    @GeraldMangani 24 хвилини тому

    Ndalamatu basi

  • @Djmsakama-kj3ne
    @Djmsakama-kj3ne 7 годин тому

    Chisilu chamundu

  • @malawimuahmmed5941
    @malawimuahmmed5941 7 годин тому

    Mmmmm

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk 6 годин тому

    ❤️🎉

  • @SoftChampion
    @SoftChampion 3 години тому

    Eya

  • @FelisterBenedicto
    @FelisterBenedicto 6 годин тому

    𝐎𝐩𝐮𝐬𝐚 𝐚𝐦𝐞𝐧𝐞𝐲𝐨 𝐚𝐲𝐞𝐧𝐝𝐞 𝐛𝐰𝐧𝐨...𝐧𝐝𝐢𝐞 𝐚𝐤𝐮𝐨𝐧𝐚 𝐧𝐠𝐚𝐭 𝐤𝐚 𝐯𝐨𝐭𝐞 𝐤𝐚𝐤𝐞 𝐤𝐚𝐧𝐠𝐚𝐥𝐞𝐩𝐡𝐞𝐥𝐞𝐬𝐞 𝐤𝐮𝐭 𝐝𝐩𝐩 𝐢𝐳𝐚𝐰𝐢𝐧𝐞.