Why A Malawi Timasiya Utsogoleri Wabwino Ku UDF Kumatenga Anthu Otibela? - Sam Muyao

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 16

  • @Suwedie
    @Suwedie 13 днів тому +1

    Chifukwa cha mtundu ndi chipembezo, am telling u if could be he was not a Muslim and yawo bwenzi akupangidwa praise
    Chomvetsa chisoni ndi choti anthu atundu ndi chipembezo chakewo sapatsa support yokwana
    My fellow Malawian if we really need change for better we might vote for Atupele Muluzi

  • @KhaifaMdala
    @KhaifaMdala 13 днів тому

    ❤❤❤

  • @LimbaniSamueli
    @LimbaniSamueli 14 днів тому +1

    Maganizo anga ali ku Dpp 💙

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 14 днів тому +1

    Atupele uja osazamuphwekesa UDF my vote

  • @ZANLUSQUARE
    @ZANLUSQUARE 15 днів тому +1

    Inshallah Chakachino ikulowa boma💪🔥

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 13 днів тому

    Ok maganizo ndikuti Atupele sikuti ndimamuda ai koma pakali pano abadikila nkhani ndi nthawi, Anthu tilibe nae chifukwa timamukondanso kwambiri ndi nyamata okongola, wamphamvu zake koma adikile nthawi asadandaule 💙💙💙💙💙💙💙💙boma la caka cino ndilimeneli Atupele adikile nthawi.

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 15 днів тому +1

    UDF ndi chipani chachitukuko chopnda jelasi zoona

  • @MonjeziShaban
    @MonjeziShaban 15 днів тому

    Malawi sungavetse

  • @HusseinAubrey
    @HusseinAubrey 13 днів тому

    km mwa tupele muli utsogoleli wabwino

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 15 днів тому

    Uyuyu timaopa bambo ake, tikuwadziwa bwino bwino

  • @Ertyvhk
    @Ertyvhk 14 днів тому

    Koma uchifamba time ya a chair unakula azimai amaduridwa mabere maka kuchirazulu mmmm

  • @DeMu-t2v
    @DeMu-t2v 14 днів тому

    Ineyo mmmmm kunena zathawi ya UDF singayifuneso nkakumbuka njjala komaso anthu ankakhala mwamatha kumakolowedwa maso kubalaka,ku chiladzulu,kumayamwidwa magazi ,afisi mene ankadyera anthu mmmmm,bodza lomwe linkakambidwa ndi Bakili aaa munthu sangandiuze za udf,ndiwe wabodza Sam

    • @Suwedie
      @Suwedie 13 днів тому

      Inde bola nthawi ya kamuzu yomwe anthu amkaponyedya ku ng'ono mix njala ya 1980s ija

  • @PaulNkhokwe-e1x
    @PaulNkhokwe-e1x 15 днів тому +1

    Iwe udf inatha kalekale