Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Mandota iweyo ..... umakwana bg mn keep it up 🤣🤣🤣🤣🤣 wauleperetsa mwambo otunga madzi uja etiiii
Komatu koma anthu azakuluma😀😀😀😀😂😂za ndeu basi
iweyo umatha ase keep up the good work
🤣 🤣 🤣 Ine ndikanamuuza chilungamo kt ndili be dola, nde ndikwela PF, mumata nsanga iweyo
Mandota mandota udzathera mmanja mwa anthu iwe😂😂😂
Bas mzangomvesesa poti ndi che mandota koma wina ndimukhapa😆😆😆😆😆
🤣🤣🤣 yapezeka basi Mandota akunthidwe basi
Inetu mpaka nditakubilibinyani Che mandota or kukuwisani kuti wakuba uyo wandibela ndalama 😂😂anyway keep it up che mandota 🔥🔥
Kaitana kavula kkkkk ndiye kabasayo mumapepha kapena kulamula inuyo simuzatheka bas🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Eee l can't go, how are you going to enjoy with your love, Mandota keep the fire burning, (aju ngisakomboleka kkkkk)
Koma kukhala satero simaths choncho Oo 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂
Munthu umakwela bandu opanda ndalama kulakwa,cholinga mukaonane ndi mkazi wamwini Kkkkk lavuzi yu tu
Mukanafika koma komwe kuli kayitana kavulako kamakudikiranitu 😂😂😂
Hahaha mandota umakwana soona mungakwele kabasa musanakambilane olo kupemba amapemba mutabwela
1Nditaona kut ndilibe ndalama nditha osapita cz utha kuyenda wapasi koma tsoka lake mkaz yo osakumana nayeso .2kundipatsa map abodza cholinga akafike komwe akupitako nditha kupanga zoti asiye khalidwe lakelo
Akulu mpaka madzi otunga kale mukutaya? koma inuyo anakonza kkkk
Kayitana kavula mukachedwa mukapeza kavala 😹😹😹🙌🏻🙌🏻 udeh mumu oo
Panalibe kuchitira mwina pamenepo. Ndy funso mkumat plan ya pobwerera kunyumbano mabweredwe ake
Ndikapange just like you did Mr
Munthu ngati wakuuza map olakwika akufunika kumuomba makofi
Kkkkkkk koma mjomba uyu eeh akukhwana🤣🤣🤣
Kkkkkk mkazi anandiyitana koma ndinalibe transport kkkkkk muzamenyedwa nazo
Muzathera manja mwa anthu inu 😂 🤣🤣🤣🤣 simulapa
Kkkkkkkk Mandota ndi more wachiyao wangalusa
Kufusamesa nakhakumangopita 😂😂😅
Kkkkkkk koma yeah Zatichitikirapo kutipatsa map olakwika man koma kungovomeleza basi
Sono ngati ukukanika kupeleka yakabanza kwa mkazi ukapeleka chani azakuchotsa mano kkkkkk
Basi kungomuwuza chilungamo kuti ulibe transport
alindota mundu wamkulu always amakhala ndi ma plan oloko apuse kumapeto kwakeko
kkkkkk nditha kuuza kt ndalama ndlibe ya transport
Basi kumapita kaitana kavula actor ukachedwa kapisiratu kkkk
Kaitana kavula ukachedwa ukapeza kavar 😄😃😃😃😃😄🔥🔥🌟💧💦
Ukupita ku chibwemzi olo ya kabaza ulibe aise
Kuchita kumuimetsa bwino wanjingayotu kkkkkkkk Ngati zinezin
Team mandota 😂😂😂mpak kukwer kabaza
Ine kundiuza Mapu ofoila choncho ndakubanduraso
Mpaka mwambi zakubazo 😂😂
Koma lifidiyoli linavupikatu Malindota chivukwa limasuna mwachuga kwambiri
Inetu zindingapitetu kwa mkasi ameneyu. Nanga atakafuna sodyera ndiye kuti ine ndikamupasa chani?
Ndingkhale osapita kwa nkaziko
Mandota yine koma ndikufuna malowo man
Che Mandota kaitana kavula mumayitha❤❤
Mozichepesa ndmuuza traspot ndlibe n ngat wandpasa map olakwikwa for ur on benefits...eee ndngakubandule bas🤣🤣
Mwejo chitchituputikasya
tsiku silingathe ndisanaonele che mandota
Anthu osokoneza m'mudzi ndiinu
Koma nde kuiwelenga tu ai inuyo munabwera burasa
Kwa sing'anga ndingo mulosa
Cheh ndipase number yanu chonde ndimafuna tigwilisane zot timenye sewe
Umakwana ndiwed dolo
Kumusa mkasiyo kuti Ndilibe ndalama ya talasipot kkkkkk
Nditha kungoyenda pasi Kom eeeee
Kukwera njinga osalipila basi kwinako zioneka
Umatha kwambiri nkulu wanga
kumuuza kut transport ndilibe bas
Kadapangazomwe wapanga iwe
Ndibwino kusapitako
Osamunamiza koma kumuuza chilungamo
Actor we uhule ndi 1 kkkkkkkk
Ndibwere mwa kamin'gi 🤣🤣
Kkkkkkk imeneyo nde nkhani mumatha man
Ine sindipiteko kwa mkaziyo
Umakwana ndota 😂😂😂😂😂😂
Hahaa Ankolo muli bhoo....koma Ka sound kamasintha sintha kamamveka low Pena
Sindingapite chfukwa drama palibe
Aaah iweyo adhaaaa. Mmakunyadira aisy...i need ur wap contact privately, i am ur big fan Bro. U lafuzi me tumachi
Bwanji osavaya ukakumane ndi nkaziyo aaaaaaaaaa.....imapitiliraka
Mumaitha mundu wamkulu😂😂😂
Sono akulu 499 yo mukuiona kuchepaeti a nzanu Tikukanika olo malate 10 kkk
Hahaha umakwana mandota😂😂😂
Wachiyawo wangalusa bulasa
Kaitana kamvulaUkachedwa ukapeza kavala 😂😂
Keep fire burning proud of u che mandota
😂😂😂😂😂 Mandota sazatheka
Hahaha kma yah kabaza yemweyu
Wakabaza wa njinga yamoto uj akanakhala kakhani ndikanayipasa 100% kakhani nd mandota nd fire for now 80%
Akita wafa koma iweyo sudzatseka
Achiyao kukonda kudya zakuba
Mmene ulilimo madota opanda ndalama
ili bho koma panopa tifuna ma episodes more than 15 minutes atleast not za less than 10mns kaa
umakwana ayinse mandota
Umakwana,kom mpaka 400 za srs
I cant 😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮mmmmh che mandota suzatheka
urine ndarama kudziwinbotsa kungo kuthawa ukana kukuvuraza
Mandota umakwana
Dina kazi wa kondindanino
Wamupusitsa wakabaza
Kukonda zinthu mandotaAdzakuphwasamula anthu
Kkkkkkkkkkkkkk ku 6 miles wafika kukawale
Che Mandota simulibwino 😂😂😂
Nzovuta
Sabhotu mandota nditunditu😂
Koma mandota iweyo umakwana
Ndip zilibwin
Kumulanda phone ndi magalasi
Mwabwela biggy
Ndikufuna malo
Inuyo mumakwana blasa
nambo wawo hahahahha akusaka kulongola eti?
Kkkkk mandota koma suzatheka
Umakwane Ase
Mandota iweyo ..... umakwana bg mn keep it up 🤣🤣🤣🤣🤣 wauleperetsa mwambo otunga madzi uja etiiii
Komatu koma anthu azakuluma😀😀😀😀😂😂za ndeu basi
iweyo umatha ase keep up the good work
🤣 🤣 🤣 Ine ndikanamuuza
chilungamo kt ndili be dola, nde ndikwela PF, mumata nsanga iweyo
Mandota mandota udzathera mmanja mwa anthu iwe😂😂😂
Bas mzangomvesesa poti ndi che mandota koma wina ndimukhapa😆😆😆😆😆
🤣🤣🤣 yapezeka basi Mandota akunthidwe basi
Inetu mpaka nditakubilibinyani Che mandota or kukuwisani kuti wakuba uyo wandibela ndalama 😂😂anyway keep it up che mandota 🔥🔥
Kaitana kavula kkkkk ndiye kabasayo mumapepha kapena kulamula inuyo simuzatheka bas🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Eee l can't go, how are you going to enjoy with your love, Mandota keep the fire burning, (aju ngisakomboleka kkkkk)
Koma kukhala satero simaths choncho Oo 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂 😂
Munthu umakwela bandu opanda ndalama kulakwa,cholinga mukaonane ndi mkazi wamwini Kkkkk lavuzi yu tu
Mukanafika koma komwe kuli kayitana kavulako kamakudikiranitu 😂😂😂
Hahaha mandota umakwana soona mungakwele kabasa musanakambilane olo kupemba amapemba mutabwela
1Nditaona kut ndilibe ndalama nditha osapita cz utha kuyenda wapasi koma tsoka lake mkaz yo osakumana nayeso .
2kundipatsa map abodza cholinga akafike komwe akupitako nditha kupanga zoti asiye khalidwe lakelo
Akulu mpaka madzi otunga kale mukutaya? koma inuyo anakonza kkkk
Kayitana kavula mukachedwa mukapeza kavala 😹😹😹🙌🏻🙌🏻 udeh mumu oo
Panalibe kuchitira mwina pamenepo. Ndy funso mkumat plan ya pobwerera kunyumbano mabweredwe ake
Ndikapange just like you did Mr
Munthu ngati wakuuza map olakwika akufunika kumuomba makofi
Kkkkkkk koma mjomba uyu eeh akukhwana🤣🤣🤣
Kkkkkk mkazi anandiyitana koma ndinalibe transport kkkkkk muzamenyedwa nazo
Muzathera manja mwa anthu inu 😂 🤣🤣🤣🤣 simulapa
Kkkkkkkk Mandota ndi more wachiyao wangalusa
Kufusamesa nakhakumangopita 😂😂😅
Kkkkkkk koma yeah Zatichitikirapo kutipatsa map olakwika man koma kungovomeleza basi
Sono ngati ukukanika kupeleka yakabanza kwa mkazi ukapeleka chani azakuchotsa mano kkkkkk
Basi kungomuwuza chilungamo kuti ulibe transport
alindota mundu wamkulu always amakhala ndi ma plan oloko apuse kumapeto kwakeko
kkkkkk nditha kuuza kt ndalama ndlibe ya transport
Basi kumapita kaitana kavula actor ukachedwa kapisiratu kkkk
Kaitana kavula ukachedwa ukapeza kavar 😄😃😃😃😃😄🔥🔥🌟💧💦
Ukupita ku chibwemzi olo ya kabaza ulibe aise
Kuchita kumuimetsa bwino wanjingayotu kkkkkkkk Ngati zinezin
Team mandota 😂😂😂mpak kukwer kabaza
Ine kundiuza Mapu ofoila choncho ndakubanduraso
Mpaka mwambi zakubazo 😂😂
Koma lifidiyoli linavupikatu Malindota chivukwa limasuna mwachuga kwambiri
Inetu zindingapitetu kwa mkasi ameneyu. Nanga atakafuna sodyera ndiye kuti ine ndikamupasa chani?
Ndingkhale osapita kwa nkaziko
Mandota yine koma ndikufuna malowo man
Che Mandota kaitana kavula mumayitha❤❤
Mozichepesa ndmuuza traspot ndlibe n ngat wandpasa map olakwikwa for ur on benefits...eee ndngakubandule bas🤣🤣
Mwejo chitchituputikasya
tsiku silingathe ndisanaonele che mandota
Anthu osokoneza m'mudzi ndiinu
Koma nde kuiwelenga tu ai inuyo munabwera burasa
Kwa sing'anga ndingo mulosa
Cheh ndipase number yanu chonde ndimafuna tigwilisane zot timenye sewe
Umakwana ndiwed dolo
Kumusa mkasiyo kuti Ndilibe ndalama ya talasipot kkkkkk
Nditha kungoyenda pasi Kom eeeee
Kukwera njinga osalipila basi kwinako zioneka
Umatha kwambiri nkulu wanga
kumuuza kut transport ndilibe bas
Kadapangazomwe wapanga iwe
Ndibwino kusapitako
Osamunamiza koma kumuuza chilungamo
Actor we uhule ndi 1 kkkkkkkk
Ndibwere mwa kamin'gi 🤣🤣
Kkkkkkk imeneyo nde nkhani mumatha man
Ine sindipiteko kwa mkaziyo
Umakwana ndota 😂😂😂😂😂😂
Hahaa Ankolo muli bhoo....koma Ka sound kamasintha sintha kamamveka low Pena
Sindingapite chfukwa drama palibe
Aaah iweyo adhaaaa. Mmakunyadira aisy...i need ur wap contact privately, i am ur big fan Bro. U lafuzi me tumachi
Bwanji osavaya ukakumane ndi nkaziyo aaaaaaaaaa.....imapitiliraka
Mumaitha mundu wamkulu😂😂😂
Sono akulu 499 yo mukuiona kuchepaeti a nzanu Tikukanika olo malate 10 kkk
Hahaha umakwana mandota😂😂😂
Wachiyawo wangalusa bulasa
Kaitana kamvula
Ukachedwa ukapeza kavala 😂😂
Keep fire burning proud of u che mandota
😂😂😂😂😂 Mandota sazatheka
Hahaha kma yah kabaza yemweyu
Wakabaza wa njinga yamoto uj akanakhala kakhani ndikanayipasa 100% kakhani nd mandota nd fire for now 80%
Akita wafa koma iweyo sudzatseka
Achiyao kukonda kudya zakuba
Mmene ulilimo madota opanda ndalama
ili bho koma panopa tifuna ma episodes more than 15 minutes atleast not za less than 10mns kaa
umakwana ayinse mandota
Umakwana,kom mpaka 400 za srs
I cant 😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮mmmmh che mandota suzatheka
urine ndarama kudziwinbotsa kungo kuthawa ukana kukuvuraza
Mandota umakwana
Dina kazi wa kondindanino
Wamupusitsa wakabaza
Kukonda zinthu mandota
Adzakuphwasamula anthu