Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Hahaha Mandota wafa nayooo kkkkk actor wafa...50 pin yavaya kkkkk big up Doc.
Nice anyamata km naneso ndi chisukulu cha hemandota apa ndayamba km siku Lina ndisakuna ndi gogo
Mandota 🙏 kemesi yanu imanama pa chiphwanya Kulakalaka bola munkadakongoza straight
Ndanenatu ine last week kt aliyense ndiofunika kwa nzake lerotu izi akuikani mbama kudyetsanso 50pin ija kkkkkkkkk
Ching'aning'ani wachita bwino kumubwera 50 pin che mandota anakupanga cholipongwe nd mkazi wake
😂😂asimu akufuna kutuluka, ehhhh Koma sing`anga waketu Nde wabozaso
You can get more views if it were either in English or at least with English subtitles
nooooo this is enough
Babawo naweni kujipa moto🤗🤗🤗
Tayamba ku ndipeza ine lelo😋❤️❤️
Azing'anga enawa kumaona kae 😂😂😂🤣🤣🤣🤣😜 50 zauzande yapita🏃♂️🏃♂️
Sing'anga kuopa kubeledwa 😂😂Che mandota ndi Elizabeth😅😂
Koma gyz muzatipha ndikuseka ulemu wanu bas mumaitha 🇲🇼❤️
Hahaha nakuuzani Inu kuti Chiphwanya kamagwero ndi galu wakuba kkkkkkkkkmm
Zoona chiphwanya ishiii
May Allah keep you strengthen
Kkkkkklll akuomba
Mandota wabeledwa kkkk, komanso ndinawona news ati ukufuna thandizo chifukwa cha depression, koma ndizoona??? Tiuzen chilungamo
Che mandota, wa khemisi amapita Kwa asing'anga? Ndakomoka🤣🤣🤣🤣
Nice one, iweyo unabwera kuzakhala.
I said it that Che Mendota will help Chiphwanya in one way or the other 🤣🤣🤣😘
Kkkkkkkkkkk koma nanga amathira chochi kkkkkkkkklk. Koma guys kkkkkkkk
Mandota bwera kuno ndikuperekeze kwa Sing'anga ku Mbanganda 😆😆😆😆
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Chemandota kukonda akazi until they steal your money aaaaa ulemu wanu guys much love you all mumatiyimilila
Komatu kuona akufuna 50pin pomwe amabisara🤣🤣🙌🙌
😂😂😂😂, aise ndafa, mbama plus kupemenerera kwakeko
😂😂komatu zina umangoona wazimba nawe mandota kukopeka Iiiiih😆
Wati zakanika koma zithu zake aaaa chibwana bwanji tenga zako #mandota 🤣🤣
😂😂😂😂😂 aise video iyiyii eeeee ndikanafa ndi phwetee
Ndikuphunzira chichewa ndikufuna subtitles
Chonde chemandota ndikufuna subtitles pleaseeee
Koma ndasekaaa🤣🤣🤣🤣 more 🔥 fire😂😂😂😂 good job
😂 😂 😂 Aelisabefi adya bazi zimunadye.
Mandota uli ndi chibwana 😁😁😁😁😁😁nice kkkkkkkkkkk
Apa ndiye actor wapusa 🤣🤣🤣🤣
Achimphwanyaaaaaaaa.....😂😂😂😂😂Amuswa khofi mandota
Mwakumana nazo kkkkkkkk Mesa mumakaniza
Kkkkkkkkkkk km ndaseka mwina ndathila apang’ono kkkkkk mpakana wakumbuka chiphwanya 😂😂😂😂😂😂😂
Ipitilile mpaka ponthela Po mandota 💯💯💯💯💯💯💯
Umakwan ase iweyo❤
Kod muli moyo et kkkkkkk koma yanga munalandira et😂😂😂We loves u chemandota squad much love from machinga t/a nyambi malundani
Nice
Mandota wabetsa ndalama 😂😂 ati ku headquarters ya makhwala kkk
Ilibwino kwambiri muyao iwe, iweyo unabwera basi
Kod iweyo eti ndiwakutiko komaso umakhala kuti, sorry tu ndafusa coz timatsutsana ndi ma guyz kunoku
Keep going on man great video
Amafunika kwambili ndi Elizabeth 🤣🤣🤣🤣
Mmm kkkk
We lafuzi yu too..... Keep up the good work
Mandota chitumbuwa kudya ngati unasala kkkkk
Hahahahhah madota ayindithu zikomo mpakana palirime 🤣🤣🤣
Kumagwira ngat mwanyamula mazira ankhwali🤣🤣🤣
Nthawi koma I'm proud you all guy's
😂😂😂nice collaboration,, kanthawi koma kakumachepa💔
Che mandota mumakwana
Aaaaaa ndikupita konko kwa shiphwanya
Kkkkk akut munthu sumangodyera chigwada chokh chokha komano nthaw zina umadyako bodya
😂😂
Koma akulu akulu nutikomola kunja nkwadzuwa uku😂😂😂😂😂😂😂
😂🤣🤣nde mwathawatu Che Mandota, keep the good work ✨🥰
wabetsa Mandota kwa Chiphwanya kkkkkkkk
You makes us happy always my bro ❤😂
Keep up the good work chemandota 😎😎😎
😂😂😂😂😂😂 Akita akungovatu maziku ano
Mwana wamwini Mpaka kwa ng'anga hahahahahhah
Akuomba mandota 😅😅😅
This guy is talented
Okuba waberedwa 🤣🤣🤣🤣
Kkkkk very impressive Chemandota
Kma chiphwanyayu kumapeto kwake ayambana
Its `kapena ndapepelera ochepa` for me🤣🤣🤣🤣
Osamangokhala Pali ponse mukhalila ndondocha kkkkk
Nkhonya yobwenzera kuwawa lol 🤣🤣
Chigwada Kma iweyo 🤣🤣🤣
Wapepera baba wanga🤣😂🙌
Safuta
Wafa Akita 😂😂😂😂😂 mandota and Chimphwanya ❤
Kod zoika subtitle ya English munasiya bwanji??
Zimatenga nthawi
Wagwa nayo mandota😀🤣 zandinyazatu
Welcome back che mandota I lafusi you
Tabwera mochedwa lero....💥💥💥my favorite 😍
Big man,apatseni ndalama amzanu
Kkkkkkk pa ground patereradi ndalama yavutadi 😂😂😂😂😂😂😂
Actor ndi actor basi go konko kwa asing'angako
🤣 🤣 biggy azanu apasen ndalama Corona virus zugwilizana bwanji
Mesawapereka 50 yo
I never laugh like this...koma lero ai zikomo big man
Mmmm suuzatheka uyelekeze uone anyamata anga akupondeni
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Kma mandota ukuzembera ndan zakwang'angazo
Iyinso ndiyabwino kwambiri
Kkkkkkkk akuombani a bwana
Nsangalasi wathu wa thawi nzose
Kkkkkkk mandota unabwera kuzakhala
ati mwina ndathila apang,ono kkkkkkk
Akita wapasidwa umbama😂
Kkkkkk kma nde akuhenda pansitu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😅😅😅Mandota Athamanga ekha
Nc boss
Well Done ✅🤗
🤣🤣🤣 iih nambo yindu yakwe yakusyausyatu🙌🙌💪
Ili BHO bo kwambiri 😊
Nice one
🤣🤣🤣
Koma madolo awa sazatheka 😂😂😂😂
Love you bro mandota
Include subtitles please
Mwaswa chair
Kkkkkkkk koma akupasa chimbama 😂😂😂
Kkkkkkkkkk mumakwana
Kkkkkkkk nanga mangwarawo amatero? Kkkkkkk
Hahaha Mandota wafa nayooo kkkkk actor wafa...50 pin yavaya kkkkk big up Doc.
Nice anyamata km naneso ndi chisukulu cha hemandota apa ndayamba km siku Lina ndisakuna ndi gogo
Mandota 🙏 kemesi yanu imanama pa chiphwanya
Kulakalaka bola munkadakongoza straight
Ndanenatu ine last week kt aliyense ndiofunika kwa nzake lerotu izi akuikani mbama kudyetsanso 50pin ija kkkkkkkkk
Ching'aning'ani wachita bwino kumubwera 50 pin che mandota anakupanga cholipongwe nd mkazi wake
😂😂asimu akufuna kutuluka, ehhhh Koma sing`anga waketu Nde wabozaso
You can get more views if it were either in English or at least with English subtitles
nooooo this is enough
Babawo naweni kujipa moto🤗🤗🤗
Tayamba ku ndipeza ine lelo😋❤️❤️
Azing'anga enawa kumaona kae 😂😂😂🤣🤣🤣🤣😜 50 zauzande yapita🏃♂️🏃♂️
Sing'anga kuopa kubeledwa 😂😂
Che mandota ndi Elizabeth😅😂
Koma gyz muzatipha ndikuseka ulemu wanu bas mumaitha 🇲🇼❤️
Hahaha nakuuzani Inu kuti Chiphwanya kamagwero ndi galu wakuba kkkkkkkkkmm
Zoona chiphwanya ishiii
May Allah keep you strengthen
Kkkkkklll akuomba
Mandota wabeledwa kkkk, komanso ndinawona news ati ukufuna thandizo chifukwa cha depression, koma ndizoona??? Tiuzen chilungamo
Che mandota, wa khemisi amapita Kwa asing'anga? Ndakomoka🤣🤣🤣🤣
Nice one, iweyo unabwera kuzakhala.
I said it that Che Mendota will help Chiphwanya in one way or the other 🤣🤣🤣😘
Kkkkkkkkkkk koma nanga amathira chochi kkkkkkkkklk. Koma guys kkkkkkkk
Mandota bwera kuno ndikuperekeze kwa Sing'anga ku Mbanganda 😆😆😆😆
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Chemandota kukonda akazi until they steal your money aaaaa ulemu wanu guys much love you all mumatiyimilila
Komatu kuona akufuna 50pin pomwe amabisara🤣🤣🙌🙌
😂😂😂😂, aise ndafa, mbama plus kupemenerera kwakeko
😂😂komatu zina umangoona wazimba nawe mandota kukopeka Iiiiih😆
Wati zakanika koma zithu zake aaaa chibwana bwanji tenga zako #mandota 🤣🤣
😂😂😂😂😂 aise video iyiyii eeeee ndikanafa ndi phwetee
Ndikuphunzira chichewa ndikufuna subtitles
Chonde chemandota ndikufuna subtitles pleaseeee
Koma ndasekaaa🤣🤣🤣🤣 more 🔥 fire😂😂😂😂 good job
😂 😂 😂 Aelisabefi adya bazi zimunadye.
Mandota uli ndi chibwana 😁😁😁😁😁😁nice kkkkkkkkkkk
Apa ndiye actor wapusa 🤣🤣🤣🤣
Achimphwanyaaaaaaaa.....😂😂😂😂😂
Amuswa khofi mandota
Mwakumana nazo kkkkkkkk Mesa mumakaniza
Kkkkkkkkkkk km ndaseka mwina ndathila apang’ono kkkkkk mpakana wakumbuka chiphwanya 😂😂😂😂😂😂😂
Ipitilile mpaka ponthela Po mandota 💯💯💯💯💯💯💯
Umakwan ase iweyo❤
Kod muli moyo et kkkkkkk koma yanga munalandira et😂😂😂
We loves u chemandota squad much love from machinga t/a nyambi malundani