*Zonse zomwe mukuyembekezera,zichitike mwachangu ndipo Mulungu azuzule zotchinga zonse pa ma plan ako onse mu dzina la Yesu!* Prophet galimoto at Tete Mozambique for Jesus 🙏🏾
Beautiful voice...God's true servants. Favoured Martha you unique. Very Power songs women of God. Good collaboration. Lankhulani komaliza za tsogolo langa Yahwe!!
*Zonse zomwe mukuyembekezera,zichitike mwachangu ndipo Mulungu azuzule zotchinga zonse pa ma plan ako onse mu dzina la Yesu!*
Prophet galimoto at Tete Mozambique for Jesus 🙏🏾
Mmmm nyimbo iyi ikusuntha nyengo zanga ndipo ili pa repeat ❤❤❤❤
Thanks to the studio and both of you best singers! Yamenyedwa bwino ! God bless you! My inspirers
Indeed muli ndi mau omaliza ndinu yawe.only God has the final say ❤❤❤
Ndavesala mokwanila zomwe ziko likuyakhula 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 yakhulani komaliza ndinu yehova osalemphela 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
First day kuimvera nyimboi was on play me a song program koma nde ndinalira, this song is powerful
❤️
Nyimbo ikuyakhula ndi nyengo zanga yakhulani komaliza Yahweh
Ndikudikila mau omaliza yawee chitonzo kuwawa eeeee😢😢😢😢
Amen🙏🙏yankhulani koma Liza ndinu yahwe taweruzidwa kwakwana ndinu amene mmadziwa za moyo wanga🙌🙌🙌🔥🔥🔥
Amen
Amen chikhulupirilo changa chili pamawu amaliza so touching 😢
Mhuuuuu am speechless nsaname zitonzo kuwawa, Yankhulani komaliza Yahweh.
Anthufe timakumana ndi ziphinjo zimenezi koma mulungu ndinu final destination no one can paint black if he put white❤❤❤❤
Eish this song eee mau ndilibe yandililitsa ine
This is complete, may the good lord continue blessing u and give the desire of your heart ❤️ 💙 💜 💖
I lyk these song koopsa ndipo ndimainvera dairy olo la 20 pasiku ndipo myimbo imeneyii imangogwilizana ndi nyengo zomwe ndikudusamo
Powerful song everyday I play this song ❤❤❤❤
People can sing eeee, in love with the voice mmmm nyc song
Nyimbo yomwe yanyamula vumbulutso pa moyo wanga ndinso pa banja langa. Yankhulani mau omaliza Yahweh.
Very powerful song! Speaking to me
Yakhulani komaliza.. anthu atidulira maliro yakhulani komaliza Yahweh
Yankhulani komaliza Yahweh... Muli ndi mawu omaliza ndinu Yahweh 👏👏👏👏
Love this one so much, yankhulani komaliza baba
Yankhulani komaliza YAHWEH 😢😢😢😢😢😢ohhhh God
Ndipempho nd pembedzelo langa kt mulankhule komaliza pa banja lomaliza ambuye chitozo chakula ku banja lakwathu😭🙌🏼
Powerful song God bless listening in from Zambia
Yankhulani komaliza ambuye n yakhani mapemphero anga😢😢
Indeed God has the final say to me....musalole Adani anga andiseke...banja ndili nao mwana ai yakhulani komaliza baba😢😢😢
Beautiful voice...God's true servants. Favoured Martha you unique. Very Power songs women of God. Good collaboration. Lankhulani komaliza za tsogolo langa Yahwe!!
ndine nsilamu koma uthenga uwu aaa ineyo ndikungoyimvela koma ndikulila ndi nyengo zanga
Nyimbo anayimba bwino iyi❤
Beautiful gospel ambuye ndinubnokha muli ndi mawu omaliza 🙏
Nyimbo yabwino kwambiri. Dziko lapansi limalankhura potengeradi nzeru zake zokha koma inu nokha ndiye mumadziwa munthu chiyambi ndimapeto ake.
Powerful message Rachel, i like the song
Osintha nyengo ndinu nokha Yahweh
Mau omaliza ndinundi Yahweh
Amen.
So powerful massage mmmm muli uthenga Wanga yankhuleni komaliza ine Yahweh
This song leaves my heart at peace, muli ndi mau omaliza ndinu YAHWE
Nice song ndaikonda ayankhuledi komaliza yahwee zamoyo wanga😢
Oh yes, may a Mulungu ndi mau okhawo a moyo ndi ochita Chita pa nyengo za omudalira iye. Mau enawa asatisunthe, koma a Yahweh.
This is what we call gospel with great messages
Mmmmm koma zoonad my national anthem, every day prayer God has a final say 🙏 ❤❤❤
Amen mlungu wanga yankhulani komalizadi pa moyo wanga
😢😢😢😢
God bless u. My ccter alakhure komalidza wakumwamba Amen
Nice song ndipo ikundisutha kwambili moyo mwanga very nice ❤
Powerful song lhave been searching it for along tym ndipo ndizingoimvera tsiku lonse yankhulani komaliza Yahwe
Amen yankhulan komaliza ndimoyo wanga
Apowerful message, He has a final say Indeed🙏
Mmmmm koma mwandifikapo. Bravo only yawe can conclude
Ndinu muli ndimau omalizadi yaweh ❤❤❤ I love this song
Amen yankhulani komalidza ambuye pa banja langa mulindi mau omalidza pa moyo wanga
Nyimbo yabwino yankhulani komaliza Yahweh zikomo pa nyimbo yabwinoyi amen
Ulemu upite kwawambamwamba JEHOVAH. I salute Him.
Muli ndi mawu Omaliza ndinu yaweh😢😢
What a touching gospel song ,,❤,,ndipo this song it's very touching
This indeed touched my heart. Encouraging song.
Thank you our artist for more things you sing to me nyengo zanga ndamusiyira yahwe
Only Jehovah who has the final say ,,, waiting for God's time father
Only God has the final say
Yankhulan komaliza ndinu yaweh eshhhhh ikundisuntha hvy
Nice song.... Muli ndi Mai omaliza ndinu yaweh
Amen ambuye yankhulani komaliza pamoyo wanga Yahweh
Nyimbo iri bwino kwambiri. Ambuye alemekezeke kopambana
Revelation to several am here. Speak my Yahweh sakundiva ine anthu
Muyankhula liti komalidza Yhawe panyengo zanga😭😭😭😭😭
Yankhulani komaliza yehova pa moyo wanga, pa mwana wanga ku banja langa komaso zatsogolo langa yahwe🙏🙏
Fantastic vocalist you both great job
Yankhulani komalidza Yahweh 😭😭🙏
Nyimbo iyi imandisuntha and imakamba zanyengo zanga bt i believe kt kuseli kwa nyimboyi kuli umboni wanga tsiku lilikuzali❤❤
Yankhulani komaliza Yahmweh😭😭🙏🙏🙏
Eshhhhhhhh kunyozedwa kosalekeza yakhulan komaliza Yahweh😢😢😢
amen mau omaliza nd ateta kumwamba bas
Amen yankhulani kommaliza yahwew
Yankhulan komaliza Yahweh nd moyo wanga
😢😢😢😢😢yakhulani komaliza yahweh
Muli ndi mawu omaliza Yahweh
Ndinu nokha yaweh muli ndi mawu omaliza palibeso wina💪💪🙏🙏
So powerful God has Final word thanks aunt martha nda Rachel keep it up❤
Eshi, thoa song raises my spirit and feeds my soul God bless
Yakhulani komaliza yehovah pamimba yanga imasulidwe mudzina layesu ❤
He has a final say🙏
Muli ndi mau omaliza ndinu Yahweh
This is what we call gospel
Amen!!! indeed only God has a final say...
what a msg ? Stay blessed dear
God bless you for reviving many souls to him
It is only God who has final say😭😭powerful song
Only you load ndiyangure yehova pamoyo wanga 😭😭
Thank you for the songs
Final wards come from God amen
This is the last days indeed, Glory be to our God
yankhulani komaliza ndinu Ambuye 🙏🙏🙏
Ndinyimbo yabwino kuonetsa mene umakhulupilila mulungu
It is very good song, keep up
Ooh yes Lord final word from you❤
Powerful song ❤
Congratulations guys ndayikonda kwambili❤
Powerful message. Ndaikonda
Jesus has final say uplifting song ndipo ndadalisika Ambuye ayakhure komalizadi
Ambuye yankhulani nane komaliza nyimbo iyi yikumasuntha moyo wanga
Amen nyimbo muli uthenga
Powerful mam....I love Yu my dearest
Koma mai uyuu nyimbo iyiii ayiii ikundililitsa etii
Yakhulani komaliza , beautiful song