FINAL Greciam Nyambo ABISALOMU Official Music Video 1
Вставка
- Опубліковано 4 жов 2024
- Hello my Fans out there
Thanks for the support you always give since i started this music journey
its close to 20 years now i do not take this for granted tank you very much
in this year 2021 i have bring you another new Video titled Abisalomu
The massage
the song is an appeal to the general public not to make decisions out of anger or frustration
Kumafatsa koma
Kumadekha koma
osafulumila kupanga Chisankho Mwachipyera Mtima
hope you will enjoy it
May good God bless you
Umuliro bwingi Mr Nyambo ,tutakwivya
Humble musician, God grant you more blessings encluding wisdom
Umakwana bwana
Big ulemu wanu mumatha kuimba big tikudalisika heavy
Probably the best song, mkulu wanga ndiwe dolo, nyimbo iyi muli uthenga wabwino kwambiri
Abwana Grecium'nyambo mulungu akudalitseni kwambiri ndi uthenga omwe mumatipatsa ife anthu ineyo ndimadalitsika nawo kwambiri
Nice music
He's too good 🔥🔥💯 underrated musician ...
His songs touches me a lot, this is never luckson
Ukuswa sound Greee 💥💥💥💥💥💥💥
Am absalom and I love the message In this song
+265999453453
Yonse bho, ija ya udzimusangalatsa mulungu ngati Loti bwanji
Ilibwino kwambiri man
Ndiwe Big man pa nyimbo zako
Wometa m'baliwa😂❤
Afana awa mulungu anawadalitsa ndi mawu abhooo
Well crafted music...
I like his songs kwambiri
Your songs are wonderful and educative.
Nice song , but sound track , ikumveka ngat ya Gift Fumulani -ndiyimbira
He is so unique and original. I love his music
Big inumumatha pitilizani nyimbozi zilibho
This is the best song keep it up iam listening it again and again
2420 one of the best songs ever
Mumatha bwanji kuyimba Chichewa ndi chizungu nthawi yimozi nyadilani chilankhulo chani monga anthu aku Tz
Kkkkkkk ufulu
My son's favourite song
Nyimbo zodzara ndi unthenga wamphamvu
Fantastic song
Love it
Receive your flowers champ
great
This song is 100% perfect, audio, lyrics and video i like everything!
Abwana taponyani ya Mapeto Ake Tikaika Inuyo Please sikupezeka pa Internet pano
Am in love with this song, ndazikonda
Hit but concept is not matching brother....
I need your music Grecium, how can I buy?
Halla me on WhatsApp bro this is Greciam Nyambo +265999453453
Nice song