This is one of the Malawian songs that we need to export. Great creativity and very very artistic loved everything about it. Receive your flowers 🌹 🌷 guys. Mumatha kwambiri we want more songs like these to reach above and beyond the diaspora. 100% Malawian art
Ndiye mwati kumadya 🎉🎉🎉bweletsakoni tiichite chipweteko koma phwedo umu mwamuonetsa akulilila kuuna ati bola school days 😂😂😂😂😂😂mphatso ali kuti aone izi Leticia muuze mphatso kuno 😅😅😅😢😢😢ndinaiwala paja adafa moment of silent T shirt ya Mphatso phwedo akabweze madolo ake tituma inuyo mwamuonetsa😂😂😂😂😂 on repeat here
Kod kufikikira kutaya koma kumadya kkkkkk kudya kudya olo kamodzi kkk mwakazinga iyiiii more fire 🔥🔥🔥 sy & ke 2025 uzichokera ku parliament ukukazinga dzina kumadya 😂😂😂
An insane shot where the green carpet of uneven grass introduces the scene to a young boy, dancing solo, with the subtle sunset giving a general warm effect to the shot, real talent there cameraman and director! 🎉
I'm the only zambian who understands this audio from our lovely brother from our new capital city or province which is malawi.... From now own lilongwe and blantyre they are part of 🇿🇲 district. Kumadya anyamata mu zambia osango taya basi 😂😂😂😂 Olo ndiwa soya piece tiyeni tizidya mosafulumila modeka mtima
Anyone to like my comment so that I comeback here and listen to this masterpiece😊osayiwalatu kumadya kumeneko ka😂
😂😂😂😂Indee kumadya
Ife tikudya katatu
i hope nanunso mukudya bwino kumeneko
Come and listen 😂😂😂 hope mwadya kumeneko
Ife tikudya zofunika kudya
Zitengera nzeru zako kuti umve nawo nyimboyi 😂🤗 Only for legends
Ndipo only legends can understand the song
Kikkkkkkkkkk kumadya azibambo Kikkkkkkkkk iyi ndi hit kwanga sindikuziwa kwa enanu
Eee ndudabwa nazo 😂😂😂😂🙌
Kkkkkkkk kukhalila kutayaa😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂🤣
Munthu sakhala dolo moyo wake onse ndaonera Phwedo🤣🤣🤣 Nice tune guys!!💥💥
Azibambo kungofikira kutaya ndikut kutaya chakudya koma maguyz awawa Kikkkkkkkkk
Iyi mwakazinga 🤸🤸🤸🤸🤸💯💯💯💯 , brothers and sisters gather here to support our own celebrities.... 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Tikufuna yina guys
Tadya takhuta
Iyi indithera ndalama iyi
Kkkkk Koma yaaa
Muli boo anyamata aku 25
Sure u r ryt❤❤our very own🇲🇼
Zambia here we approve this song 🌹🌹🌹🌹🌹🌹🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Ayitu mukafuna Ina munena amene tikufuna Ina let's gather here ❤️
My favorite crew ❤ keep it up guys inuo mumakwana kuposa pa 40 and nyimbo zainu mmafatsa when shooting the vdz .Mmatiyimilira
Komatu phwedo simunamcheze bwino makosana 😂🙌🙌
amuenda pansi
Komatu phwedo yu munamulakwira aaaash 🙆 Nice one from our very own legengs...Onyamata Onyemba-nyemba 🔥
I like your union: you have survived for all this time since you started -PLEASE CONTINUE
Dzanyamata dzakudya💥💥
Mwapha, kupekulira shovelo nsima
Big up 🥳 kma uncle Phwedo mwawalakwira😂😂
Mposo etinu Kkkkkk kumangomutuma
Phwedo apa wagwanayo alibe makani kkkkkkkkk
Kulakwadi😂😂
Phwedo phwedo😂😂😂
Brother Symon ofunika kuyamba workout tu achimwene akulu wo bola tinawazolowera.......lots of love from this side......Ina ikufunika
The Symon n Kendall Style we know 🔥🔥🔥
Mmatimvesa kukoma
This is 🔥🔥🔥 much love I can see my favorite phwedo 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Komatu food yake ndiyomwe kapena inayi kkkkk, zikundivekela mwaaa.... Nice tune
Iyiyi ndiinado
@@EstherZintambira-sq3yy ndipo inu ayi zikomo
Nice tune.Komabe uthengawo siukundimvekera bwinoyi,kudya kwake sichakudyachiyi😁🏃
Akendal nda symon ambuye azikudalisani pa ubwezi wanu continue guys mukuitha muvingeso film ija mudapanga zakazpitazo
This is one of the Malawian songs that we need to export. Great creativity and very very artistic loved everything about it. Receive your flowers 🌹 🌷 guys. Mumatha kwambiri we want more songs like these to reach above and beyond the diaspora. 100% Malawian art
Kudya ukuku mkomweku koma anyamata Inu,mmmmm pena nduona ngati mwatikuluwika azimayi....big up our own artist.....iyiyi mwaswa eeeee
You're still entertaining us for 2 decades now... We're proud these guys
Ndiye mwati kumadya 🎉🎉🎉bweletsakoni tiichite chipweteko koma phwedo umu mwamuonetsa akulilila kuuna ati bola school days 😂😂😂😂😂😂mphatso ali kuti aone izi Leticia muuze mphatso kuno 😅😅😅😢😢😢ndinaiwala paja adafa moment of silent T shirt ya Mphatso phwedo akabweze madolo ake tituma inuyo mwamuonetsa😂😂😂😂😂 on repeat here
Yomweyo galu iwe kumadya bas on repeat here😂😂 ❤❤❤❤
Only legends will understand
Phwedo amuonetsa. Wakumana ndi man Chaksy ndi mfumu mzake pachakudya. Amaona ngati ndi mphatso machira. Nyimbo ilibwino iyi 🔥🔥🔥
No one will compete with you guys❤️❤️💃💃
I like the drum 🥁 very massive, Man Phwedo ayipatsa moto. This has been cooked, yapsa! 🔥 🔥
What a masterpiece...... Anthu muli ndi luso
Ndipo lusotu
😂😂😂 phwedo mwamulakwira zoona kumaliza wilibara yonse iye olo mbamu. Nice song guys. Ur ID intact big up
Ine awawa since day one ....... kumadya or kamudzi kokha... bambo a Juu😅😅😅😅🤣
Kod kufikikira kutaya koma kumadya kkkkkk kudya kudya olo kamodzi kkk mwakazinga iyiiii more fire 🔥🔥🔥 sy & ke 2025 uzichokera ku parliament ukukazinga dzina kumadya 😂😂😂
Apapa nde mwabweratu zakale zja 🔥🔥🔥
Kumaphakadi mamuna mpamimba 🔥🔥🔥🔥.Nyimbo yih soh ili bho angoidyera kumodzi 💥💥💥🔥🔥
Malawi let's gather here Malawi let's go ya China phwedo mono kumadya
The song is deep😂😂😂only legends will understand
Only legends 😂
Koma ndipo😂
U hav gone beyond critical listening 😂
Nanga mpaka kutenthesa mbwanda pakati pa usiku
Nyimbo iyi ikukamba za nsima yomweyi??????😂😂😂😂😂😂😂
Azimayi mzitimvetsaaa 😂😂😂😂🎉🎉🎉 nzinziri olo muli inu mkadatanii
Kudya uku sikwasima, akukamba zogagada pa home,
Symon & Kendall, back at it again with another amazing banger! Love these guys. Every song is always a hit! 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼
Phwedotu waziona apa kkkkk
Nice track guys, you always entertain
Phwedo kkkkk sanakupase mbali yako ayi 😅😅😅😅 next time uzacgenjele😂😂😂🎉🎉
Big up to you my brother's.. You really represent south africa music listening from Zimbabwe
😂😂 Anyamata inu simuzatheka kkkkk Big up .,.. more 🔥
Awesome video 👍👏🏼👏🏼🤣🤣🤣🤣, you guys making laugh, Watching from America 🇺🇸
Symon and Kendall my favourites. Mumatha guyz. Big up!!!
Mr Phwedo nkudzalowa chamutu pamene paja😂
Koma mukumadya?😂
Apa nde mwabwer faddest with pwedo mkat 🎤💪🔥🔥🔥🔥
Iwe ndi dolo aise, osachimvela chitsilu chimwendo banda wa mutu ngati bus 🚍 mbuzi yeni yeni
An insane shot where the green carpet of uneven grass introduces the scene to a young boy, dancing solo, with the subtle sunset giving a general warm effect to the shot, real talent there cameraman and director! 🎉
Classic one boys. Message tamva ndithu. Tiyesesa osamadya kamodzi
I like the creativity in the song and kumudzi simuiwalako ponjambulitsa
Tikufuna ina ndipo tizidya mwachinakodwa
Koma phwedoyo anamupanga chipongwe anabwelela kutumidwa osayitema 😂 munamuwonjeza over wise it's hit song congratulations brothers
Welcome back brothers mwatiimila a symon takusowani ku honeydue kuno
Absolutely😂 funy .kkkkkkk phwedo achose mbale😂😂😂😂😂😂😂
Nyimbo iyi Ayi mwaiphika ine ndimaona Ngati mudadanatu ambuye alemekezeke muli uthengatu umadya nthupi samanga ndilidya nyimbo ili bwino iyii
Beautiful and local song "kumadya thupi sitimanga ndi linya 👉❤❤❤❤❤❤
Kma athu Inu munavana😜😜😜😜🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo mwamenya iyi🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 video nde eeeeeee mwala
Mphwedo sanadyetu.nde.mutilimbikisa bwanji kuday wina mutamana
One of the reasons I love being Malawian 🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️❤️ culture ...odi ndikaiteleke 😂😂😂😂
This is Greatness on a different level.
Keep the 🔥🔥 burning
Phwedo yo moti akanadya nawo naeso anenepe,😂iyi nde yabwera ngati coming ❤
CAN WE PLEASE HIT 1 MILLION IN JUST 5DAYS PLEASE PLEASE PLEASE...WELL DONE TEAM..ONLY .CREATIVITY THAT DAZZLES....CONGRATS TEAM
Always i respect you guys I'm here in south Africa binoni cloverdene moto kuti buuuu mofaya
Hahaha I didn't expect kuti phwedo angapuse chonchi 😂😂 you got a fan guy keep it up
Fertiliser mpaka k100000 mkumayimba nyimbo zautsiruzo chibwana eti Dpp my vote
😂😂😂
phwdo waphika km osadyko kkkk😍😍😍😍🔥🔥🔥
This is super super i like audio, video as well as actions...keep it up pliz
Guys mpaka kum'mana phwedo😂....nice tune 🔥
Kumadya amwene kkkkkk inu anakonza keep up the good work achakulungwa
Hahaha phwado waipeza itatha koma Guys aah inuyo anakonza watching all the way from South Africa 😂😂❤
Mnyamata wakochimeza ndi komasumba nkhunda 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼
❤❤❤ ayoooo kwereko kutaunaga akutitu .. km azibambo awa ayi zikom...
Production ya audio so massive nde kubweraso video mbambande respect guys 🙌
Muzik mwapha ma guy,, local hit 🔥🔥🔥
Big music concert wth powerful meaningful ......l love the song
Absolutely Beautiful! only 4 the Legendz!!!!!!!!
kuli ntchito chaka ichi
super guys back on the field.
Since day 1 I realized that there is this dual ,,,never disappointed
A touch of class. Well crafted , the concept is just well done. 🎉
Mwaikwaupa heavy 🪨🪨🪨 congratulations 🎉🎉🎉🎉👏👏👏👏👏👏
Wow, ndaikonda iyi😂😂😂😂guyz....sons of the soil😂
Zilibwino ma boss munatiyiwalitsatu mulipobe Kodi 😎
Beautiful sounds. The concept is just dope
Malawian jams, kkk keep it up you guys ❤
Kumadya kanayi patsiku ok kkkkk love from Zambia
To say fuct inuyo ndiwoyimba guys keep it up
Eeeeeeeee km mwapha guys big 👆 tinakusowani
Ayiiii ine ndamvera manyokomintooooo😂😂😂😂😂😂 Nice tune
Ma guys I don't disappoint. Message and creativity top class
iiiih koma guys mpaka kuphika thumba lonse and nkuika mmemo mu wheelbarrow. Phwedo kuipatsa moto 🤣🤣🤣🤣🤣🙌
It's Phwedo's move when he was walking away for me. 😂😂😂
I'm the only zambian who understands this audio from our lovely brother from our new capital city or province which is malawi.... From now own lilongwe and blantyre they are part of 🇿🇲 district. Kumadya anyamata mu zambia osango taya basi 😂😂😂😂 Olo ndiwa soya piece tiyeni tizidya mosafulumila modeka mtima
Ichichi ndichi hit 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kumadya zikumveka bwino ndie kungondimana upakila❤❤❤❤❤
Ehe nsima kudzadza wilibala,eheee kunachematu 🤣🤣🤣🤣nyc song
Iyiso nde ndi Bomba 🔥🔥🔥
This has made my night🤣🤣🤣 mpaka nsima kumaliza wilibala anthu awiri🤣🤣🤣🤣🤣
Masterpiece of all your video songs 🔥🔥🔥🔥❤
kumadya soya osalira mafuta............................thats goldness
Aah inetu kudya mukamba apaku sindikugwilizana Nako😅😅😅😅😅😅😅si nsima iyii...si nsima
Kkkkkkkk Phwedo wazionatu nice content
U are the best guys keep de fire burning