Thank u so much Bon , Indeed we've witnessed today kutidi MALAWI FIRST GROUP PREASURE ,, Ndi chida chokhacho chomwe Mulungu watipatsa .Mulungu akudalitseni Bon pamodzi ndi anthu nonse ku Malawi first . Wa MRA Kapoloma ndiye palibepo chomwe wakamba chomveka bwino apa", M'malo moti apite to the Straight Point nkunena kuti ,ma Stamp pakali pano tawayimitsa kaye :
Komanso gwirizano wa anthuwa apusisana!! Chifukwa mmene kuyakhulira wa MRA a mwautabwali.. amene amalowesa katundu wambiri opanda nsonkho ndi a ndalewa
Kalindo is positively impacting Malawi and bigger than chakwera and Michael usi combined..
Man of the moment 🔥🔥
Without born kalindo we're nothing ❤❤❤
Steven Kapoloma my brother in-law MRA spoken person inuyo ndi katundu Mulamu
Viva Born Kalindo🔥
❤bon kalindo ndiwe Muthu olikonda ziko lamawi
Bon Kalindo machine opangira machine machine anzake,mwana wachabe!🔥🙋 salute
Thank u so much Bon , Indeed we've witnessed today kutidi MALAWI FIRST GROUP PREASURE ,, Ndi chida chokhacho chomwe Mulungu watipatsa .Mulungu akudalitseni Bon pamodzi ndi anthu nonse ku Malawi first .
Wa MRA Kapoloma ndiye palibepo chomwe wakamba chomveka bwino apa", M'malo moti apite to the Straight Point nkunena kuti ,ma Stamp pakali pano tawayimitsa kaye :
Thanks bwana born kalindo mwaonetsa ukulu that's freedom fighting ndale zitichedwetsa big up let's change Malawi our country
Komanso gwirizano wa anthuwa apusisana!! Chifukwa mmene kuyakhulira wa MRA a mwautabwali.. amene amalowesa katundu wambiri opanda nsonkho ndi a ndalewa
Mr kalindo ambuye azikusamalilani ❤
I am a member of Malawi first since 1964 now I appreciate Mr president Bon Kalindo
😂😂😂😂 Owo
❤❤❤❤❤ Bon Kalindoooooooooooo is a one man Standing Happy to have you
Ulemu wanu president A wanthu wosauka
Thanks you always updating ❤
DC 💯💯💯💯💯
Mr kalindo God bless u and keep you safe. One Malawi one nation.
Dolo kalindo,receive your flower b4 u sleep🎉🎉
Boooon kalindo the DC we nothing without bon karindo in Malawi wether you like it or not ❤
The most respected man ,in Malawi🔥🔥
Viva Born Kalindo Viva Malawi first mumatiimilila Amalawi
Mr Dc u deserve to be leader of opposition mwana wachabe kwambiri
Ambuye akhale nanu Mr Born kalindo
Keep it up Bon Kalindo oooooh
Born kalindo ❤ndiwe number one respect
The DC 🔥🔥🔥true definition of a freedom fighter
Anathaw ku south Africa aja awuzen ajawon zomwe bon kalind akupanga osat manyi ake aj chal chamulung chikaloz chaloz panop chaloz pa bon kalind
One man standing man of GOD Bon kalindo
This is indeed Mr Born Kalindo
Mumatiimilira Mr mwainu mulungu azikusamaliran❤
May God bless you mr kalindo
Bon kalindo may God bless you and protects you
Bon kupanda iweyo zambiri sizkanaenda popanda iwe🎉🎉
All the best Bon kalindo
Mulungu akudaliseni bwana Kalindo chifukwa kuzera mwa inu ambuye akuwonesa ukulu wawoo nthawi ikubwela ndithu
The DC's is number one viva Born K 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
The DC president wa anthu osawuka 💪✊ we are nothing without you Mr president
Man of Reality 🔥🔥🔥
Bon kalindo your the one Mr DC
Born kalindo akukwanira zikumvveka bwino ndithu zimene akuyankhula
We need Malawi like this ❤❤❤
NDIYE WINA AZITI KALINDO NDI WOSOKONEZA ,NDIXAPHA MUNTHU DAY 1.
Keep it up mr Dc
I'll join him when i come back home putting Malawi First
Malawi first and born kalindo❤
Kalindo ndi 1 big up
Our good leader born kalindo munthu wamasophenya chonde mulungu akudalitsen ndipo mulungu akutalikitsiren kuzoip ndipo mulungu akakusungen Malo Abwn
The DC Bon kalindo good Message ❤
Well done Malawi First 👏🥳
We're nothing without born kalindo the DC
Mulungu wadzusa kalindo ngati mose pa Malawi ndipo amene atamusiye kalindo akwiyisa mulungu
Dc kalindo ❤ ulemu wanu boss
The Dcccc number one The world 🌎 ❤❤❤❤❤
We 💕 you the DC and the entire Malawi first ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Kalindo anadza kuzakhala ndip Mulungu Wathu wa zatheka bwanji kapena kut wamoyo osatha apitilize kukupasa nzelu zochuluka, kulimba mtima, ndi moyo wamphavu 💪 God bless you Mr Kalindo 🙏
Zoona amupatse moyo wautali bon kalindo
Ambuye mulu mtikukyluoemphani kuti mumupatse bon kalindo moyo wautali komaso mudzimutetedzera kwa anthu oipa omwe akufuna kuononga moyo wake mulimbikitseni lotifungatila poti iyeyu ndi mpulumutsi wathu ife osauka mumupase nzeru zambiri chifukwa akumuposa ladzalo cakwera
Big kalindo mulungu akudalinseni
Umakwana kalindo ❤❤
More fire the DC mwana ooopsaa kwambiri
The DC BORN KALINDO❤❤❤❤❤
Ulemu wanu akalindo❤
The DC Bon kalindo good Message number one ❤
Mwene kalindo you're super star
takuvani big man abon kalindo koma ife akulilongwe tandaura kwambili cz mademo kulibe kkk
Ndipo mfundo akukamba wa MRA za ziiii, zaboza zokha zokha
Viva! Kalindo Viva!❤
Tili pambuyopo Mr kalindo
Congratulations mr plesdent aife akandapatuwe
The pangolin Mulungu akusungeni ndi moyo wautali bwana wathu president wa anthu osawuka
Bon kalindo Mokonda ❤
Mr Bon Kalindo ❤
Proud malawi
Mbambande Mr born kalindo
Bon kalindo, akatundu
Born Kalindo ndi akatundu brother
Umayitha kalindo ❤❤❤
Kalindo he's standing throuth
Big up Mr kalindo
DC is a big fighter
Amuna muna Kalindo
Timamfuna ma FactsBon mukuchita bwino kumalitsamwitsa Boma coz we. Have we have no opposition 😅😅😅
Born kalindo worldwide ❤
Muzitumiza a kalondolondo pafupipafupi owona tax stamp ndi mitengo yabwino pa msika
Tsono wa MRA akuyankhura bwanji
The D C mwana owoopsa kwa mbili?
Akuti osaopa amalawi dzikoli ndila democracy chocho ku kabura tituluke ambiri mawa popita kumademo muumodzi muliphavu osafooka amalawi
Wa fewa etiiii kalikoti
Viva Malawi first viva Born K
Mumatikonda God bless you
The dc ndiakatundu from lusaka
More fire Born
Koma Bon Kalindo is a Hero
Booon kalindo the dc🎉🎉❤
Koma2 sikuti zingokhala zapakamwa kuti apusitse anthu. Okay ndie akakhala kuti akupitiliza za ma stamp monga inu Mr DC zizankhala bwanji??
Mumakwana beans born kalindo
Koma mavuto tili nawo ambili osati zama sitaphu okha, chikangawa chilima anafa bwanji, feteleza mudziko muno mulibe, ulamulilo wachakwela ife sitikusangalala nawo achoke, ma dhemo akufunika kwambili ndioti chakwela atule udindo phasi, sitikufuna chakwela achoke , ma dhemo akufunikabe a born kalindo musaizizilitse ,tikumvatu kuwawa ife,
You have also right to hold demonstrations! Inu pitani musampanikize kalindo yekha
This is nice
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥
Km atolankhani enawa mafunso awo akut kodi pomwe simumamvana ndi Pati??? aaaaaaa
Mwana wa chabe kwambiri 😂..the DC
Bon kalindo machine
Kalindo timadalila inu
The Boldness in a man
Kalindo we love you
Following mr kalindo
Awe bozza Kalindo
The dc ife tikuthokoza mulungu akhale nanu