КОМЕНТАРІ •

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 5 годин тому +3

    Keeping pushing mphwanga

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 години тому +1

    Zamphambvu fredo long live❤❤❤

  • @berlz12k
    @berlz12k 2 години тому +1

    Utm woyeeeeee + dpp woyeeeee ng’onayo pansana pake zitsiru zaanthu😡 ipase motsoooo iwee 🥳🥳

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 15 хвилин тому +1

    ❤❤ good guy

  • @JaneBanda-ht4ve
    @JaneBanda-ht4ve 16 хвилин тому +1

    Ngati mwina anavota ndi Chilima yekha koma nonse a UTM palibe anavotela MCP. MCP inawina yokha ndipo kuti ukhulupilire uwona mmene iwinile chaka cha mawa chino kuti Mulungu akuchitisani manyazi ndi kupeka nkhani kwanuko

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 години тому +1

    Za power💪

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 3 години тому +1

    Mizimu ya onse anafera Ku chikangawa iwuse mtendere

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g 2 години тому +1

    Ndipo mavutika kulipila school fees koma mwana no ntchito iiii kumalawi mmm

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 4 години тому +1

    ❤❤❤

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 4 години тому +1

    Fana iweyo unapanga chisakho chabwino kwambiri iweyo sitizakuyiwala ife mafana

  • @BrazioNtondo
    @BrazioNtondo 2 години тому +1

    No band festival. Chikoka basi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 4 години тому

    Awuze zigawenga za mcp zakupha zankhaza chipani chamwazi chang'ona .

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 5 годин тому

    AUZEN FREEDO

  • @FidesChandama
    @FidesChandama 5 годин тому

    Mcp ipite yatikwana guys

  • @MathewsMynus-v9u
    @MathewsMynus-v9u 3 години тому

    Ntchana omweyo

  • @DominicYohane
    @DominicYohane 4 години тому

    Umakwana

  • @GustinoKamanga
    @GustinoKamanga 4 години тому

    Umakwan iweyo

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 5 годин тому

    Mtchana usazaphwekese

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 5 годин тому

    Kwachematu 🤣

  • @SojahBashilu-w6y
    @SojahBashilu-w6y 5 годин тому +1

    Zowon ndipo mcp ndichipani chokhacho sichitha kukumbukila komwe wachokela

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 5 годин тому

    Aku anthu mukumayankha ndimphanvu mukuzitenga kut

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 4 години тому +1

      Chipani chokondedwa mesa🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RazackjKabadwe
    @RazackjKabadwe 5 годин тому +1

    ❤❤❤❤❤