Adah Awa Azawamanga

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 17 жов 2024
  • #malawi #cyberlaw #trending

КОМЕНТАРІ • 32

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 місяці тому +8

    Kumangokhalira kupanga blame anthu ,come with your solutions, blame games won't work

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +3

    Wanzeru ku Malawi ndi Dalitso Kabambe; Napoleon Dzombe; Thom Mpinganjira; etc. Nzeru zawo zinawalemeretsa osati izi zachambazi ayi.

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 2 місяці тому +7

    Inu mumangodana naye Kabambeyo.Chilichonse angapange kumunena basi....muchila koma.sikuti akuyankhani

  • @AngelinaMzowa
    @AngelinaMzowa 2 місяці тому +4

    Basi kumangolongolora, no construction but blaming game,,
    Tulutsani zanuzo tizione,,

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 2 місяці тому +2

    In Malawi people have Degrees,Phds Doctorate to Receive more money in their positions not to Come at the ground and use there knowledge.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +2

    Let Kabambe become president and you shall be ashamed.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +1

    Mfiti iyi yatinyozera Kabambe eti? Ayi ndithu agalu alipo.

  • @MissHazel442
    @MissHazel442 2 місяці тому +3

    Chokani, nanga osabwela ku Malawi muzachite implement mzeru zanuzo? Ndipo Dr D Kabambe sakumvatu. Muimbireni phonetu mupeleke mfundo zanu.

    • @FosterChakanga
      @FosterChakanga 2 місяці тому +1

      @@MissHazel442 ngati alibe number yake nditha kumupatsa.Foolish

  • @beakab2378
    @beakab2378 2 місяці тому +1

    Awanso, kungdzadza nsanje thooooo! Muchira koma mochedwa.

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому +2

    Noone can arrest him coz he's talking de truth, umangomva kumanga gologolo iwe eti, no wonder mzika zamalawi likungobeledwa ndalama zikuona kuwopa kumangidwa eish!,

  • @AnthonyGondwe-b1t
    @AnthonyGondwe-b1t 2 місяці тому

    Seconded

  • @nkhwaziaeros1845
    @nkhwaziaeros1845 2 місяці тому

    I was also confused when he suggested that malawi needs ministers in every district lol . He might have knowledge of economics but i doubt if he lives or functions as an economist. During his time at reserve bank we all heard about how extravagant he was , that lives some of us professional to ponder his political ideologies

  • @charlessulumba2521
    @charlessulumba2521 2 місяці тому

    Genius

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +1

    There was no inflation when Kabambe was director. I correct you.

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 місяці тому

    Wise man

  • @FridayMilaji
    @FridayMilaji 2 місяці тому

    Vutho ku Malawi tinazamva zeni zeni pokapoka titawona zovuta, ndikugwilizana nanu 200% Munthu wa mkulu,umphwawi unatitseka makhutu komanso sitiwoma za mutsogolo unless atapezeka anthu ngati inuyo

  • @KennyTchapo
    @KennyTchapo 2 місяці тому +2

    Nzeru zapamwamba

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 2 місяці тому

    Abolish of tenders ,
    President and Minister s shouldn't have tenders of the government only indigenous people call Malawian should have tenders, but lecturing is needed both sides Village and in Our cities.

  • @MissHazel442
    @MissHazel442 2 місяці тому

    Dzina lanu ndani Baba

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 2 місяці тому +4

    Achimwene siyani kudya cocaine, bwerani kuno kumudzi mudzapange zomwe mukunenazo

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 2 місяці тому

    Power to that 👊

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 2 місяці тому

    Ndiponso kwambili kwakwe vut limene lili kumalawi kuno we just cross our eyes that's why

  • @rexnyalugwe4910
    @rexnyalugwe4910 2 місяці тому

    "Everyone thinks he has solutions for this country"

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому +3

    Lelo walakhulako zazelu ndithu koma bvuto ku malawi ndi umbuli ndi umphawi

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 місяці тому +2

    Yes he suppose to go to parliament that's it

  • @henrykadzuwa6018
    @henrykadzuwa6018 2 місяці тому +4

    I hate your articles, how can you attack God and good people. Your master, the devil won't save you from the wrath of God

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 2 місяці тому +5

    Ukungosokosa ndi mlomo wako opotokawo.Ngati uli ndi solution osabwera kuzapanga zomwe ukunenazo bwanji.Stupid!!!

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz 2 місяці тому +1

      Iweyo bwa😂

    • @FosterChakanga
      @FosterChakanga 2 місяці тому

      @@AchinaKellz sindingakambe zoti singakwanitse😎😎😎

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Frankly speaking bro and I agree with you ❤