This is the true meaning of being courageous. The flow goes very well. If all Malawian public figures were like Danlu we shouldn’t be suffering now. Chakwera it’s your time to go down bro.
Thanks Dan for speaking on our behalf 🔥🔥🔥🔥🔥I like this tune imagine cooking oil 2 litters nine thousand the cheapest are seven point something. This is too much!!!!
Iyi ndiye message yoyenera ....ndipo munapha ..osati Choir mwaimbayi
Wachiyawo wangalusa mukufunikila mujambule dzimene dzakwera mtengodzo nyimbo yii ndiye ili bwino kwambiri 🔥🔥🔥
Who is here with me today 😂
I'm here my friend 😂😂😂😂the song is on repeat 😂😂😂
😃🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣
Ife pano😂
😂😂😂😂😂
Tikumverabe iyi ife😂😂 Zomenya kugwesazo nzanu😂😂😅
Zake zimenezo
Pesi Nyasa🙌🙌 indeed you are voice of voiceless.ambuye akudalitsen
Well said Mr Dan Lu analonjeza kuti mtundu wanthu ukazaona kuti sunkhutusidwa nawo azatula pansi udindo
Kuyipatsa motooo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥kwende wachiyawo wangalusa💪💪💪
So tisatire zitizo apa this was so amazing song koma eish ndi chani dan lu
For sure atuledi iweyo dan lu ndi one wachiyawoooooo♥️♥️♥️♥️♥️
Kuyimba kwamwana wa mkango dan lu teceve your flower 🌼 🌸 ♥
This is the true meaning of being courageous. The flow goes very well. If all Malawian public figures were like Danlu we shouldn’t be suffering now.
Chakwera it’s your time to go down bro.
P
Wachiyao wangalusa blasa big up Mr dan lu keep up the good work we expect alot from you
Sindipanga zachipani komano kukamba zoonadi nyimboyi yafika munthawi kaye akutukwanawo angosowa chilungamo basi pitilizani kutimenyera ufulu Dan🔥💪....
atule pansi bas zatikwana ife
On point bro... the song wt a meanings.. and I salute u🎶👌💥💥🇲🇼
Ilibwino nyimbo dan lu, atuledi amenewo zinthu sizilibwino malawi ali pamoto
Gotta give it up when the truth is spoken. And done in the best way 👏🏽👏🏽 the video shot nicely with a vibrant minimalism 🔥🔥 Shout out brother 🇲🇼🇲🇼
Imeneyo yili muche
2023 Ambuye alanga kale nd Futali apa nde Plus ma guy wa atiphatu 🤣🤣🤣
Thanks Dan for speaking on our behalf 🔥🔥🔥🔥🔥I like this tune imagine cooking oil 2 litters nine thousand the cheapest are seven point something. This is too much!!!!
Chimanga chakwera kkkkk koma simwano umenewu kkkk
Yoooo bro big up this song mwapha end Muli uthenga Tura
Naweni brasaa
Big Up! 😅🤣😅😅.. Ameneyu atuledi pansi udindo walephera wabodza
Chilungamo kuwawa more fire Dan 🔥🔥🔥🔥🔥
Truth Hurts wangalusa Wabwela ndi Mottoo apaa
Nkhani ndya straight Tulani pasi
Ndine chief mponda kuno kujoz nyimbo ili bho 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 auze
Straight forward, atule pansi bas usogoleri wakanika
Hit ili mwala 🔥🔥🔥
mwanena zilungamo zokha zokha ...ndipo asakuopsyeze
Ine misonzi m'maso mwanga .....nyimboyi yaimbidwa zenizeni ...kwa m'malawi okonda dziko lake kumvera nyimboyi akhonza kuona kuti chilichonse chonenedwa mu nyimboyi nchoona ndithu
Good work, kumadzudzula pomwe zikulakwika
inuyo nd Big man bro ubwino wake nd dzoona zokhazokha sured thats reality
Brother its true kwasalira chilungamo ichindu ngaikwenda chenene
Gud vibe bru...u rock🎤🎤salute
Yomweyo galu iwe 🙌🤣🔥🔥
Though am Zambian but you talking the Truth, and remember those who talk the Truth are always on the run Dan lu ndiwe chikali keep it up
Umakwana Dan lu iwe unapha nyimboyi
Kumenya kugwetsa 😂🔥🤜🤸♂️🤸♂️🤸♂️
Ipase moto🔥🔥
Kachilungamo kobaya moyo. Tulani🙌
Mwayimba man zoona zenizeni ngankhale Lozani zanu zinali zenizeni
Tulani ili best 🔥🔥🔥🔥🔥
Uthenga wapita ngati ali wakunva wanva.
Mumakwana big wachiyao wangalusa bulasa
Ulibho Dan lu big up wachiyao wangalutsa
this is true bro, atule pansi udindo kwantere ameneyo
kma kma iyiiiii
Respected to you big man you will never end all ways coming with 🔥🔥🔥 love you so much watching from Johannesburg 🇿🇦
Atule basis alephera!
Nice song ! Big up dan up 🔥🔥💪💪
BIG UP YOA KING, Mwina utheka kukafika nawo kubomako 💪💪
blead unja wakwera ,sugar unja wakwera 🎼🎼🎶🎶🎶
You said it all man Lu, on the point with his fake promises
Nice tune & perfect timing too 🔥🔥🔥🔥
The most powerful message big up boss
Tula kwantele udindo 🔥🔥🔥
My favourite artist Dan.... me loves you .
We just dance & fill the vibe MR! These song is nice, muli othenga okhudza ndipo omveka bho, keep it up Mr Lufan
Video of the year akulu mwapha
Straight forward amwene kkkkkk fire 🔥
Iweyo ndi dolo kwambili 🙏🌹🌹🕊️
Umakwana wachiyawo...!!!
I like your courage man. Keep it up. From Zambia
I can see mr chakwela mwasithadi dzithu ndithu
Ehhhh am sure this message is goes straight Tula🎶🎙🤝
Koma apapa kutchaya kugwesako zikumanveka bwanji koma timva zithu ndithu kumalawi ndikobanda ndithu 😂😂😂😂😂😂😂
Yomweyo galu iwe 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Wazimvela enkha chakwela yoo
Ine ndathamanga kuzaonela ndikuonela exclusive inteeview pa zodiak after atamufusa za nyimbo imeneyi ayi zikomo
Mbuzi zaanthu zimenezi.... Kumangothoka basi amaona ngati kulamula dziko ndimasanje eti
Akanatuladi mwaulemu wawo eish
Tafika ife 😂😂😂😂❤
Wachiyawo wangalusa brazaa
Ukutaniko kuno
@@harriekandiero9037 iyayi malume
Chilungamo
Boss nice
You never disappoint brother man,you have said it all🔥🔥🔥🤸
everything on point and the song carries a very strong message
Akanatuladi atipha awa.
Dan u have just for our fellow Malawian keep it up brother
Atikanika mr chikangawa
Salute big
Wamupweteka Chakwera aise 😃
Fire burning everywhere 🔥
Annah achepa 💥💥💥
My personal person.
I salute you.see you on the other side🔥❤❤
You really good to remind him what he was say Dan u very super on this
Am happy 🎉🎉🎉
Chirungamo nyimbo iyi kwazisiru chakwera ndi chilima ikuwakhara
Game ndiye inawavutadi koma dyela lakula sangatule awa.
😂😂😂 choyamba ndikunthozeni big zikomo apo mwayiphula dan lu mukutimenyera khondo
Aise Dan Lu iyi yokha wapha!! Kudos bro!! Telling the tricksters nothing but the truth. Mumakwana biggy
Strong message braz Man
Dan lu umatha ndakuvulirani chipewa inu ndi azibambo
Wakumbusye
Salute bro listen song from zambia
More love Dan lu
Kwende nayo
On da point Dan 🔥✊
More fireeeee
# 1 Dan Lu
Wise artist fighting for our freedom