Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
😂😂😂😂wi lafusi yu tu machi mandota mpaka akolole watching from durban
😂😂😂😂Tamaliza ya ma paper amalo yija, mwina anapita basi 🏃♂️🏃♂️🏃♂️🏃♂️🏃♂️
Kkkkkkk Mandota ndiwe dolo😂😂😂😂
😂😂😂😂 Azibambo nd mutu wabanja
Kupanda kubwera inuyo bwezi ndikutan kaya,,, ❤❤❤mumakwana
😂😂😂😂 Ma Maili abwera mwa emergency agwire okha
Talented man!!! Komanso kankhani uja munagwilana
😂😂😂agwida ndi kamwana
Ili sharp ase keep it up ❤😂😂
😂😂😂 mandota ndiwe achalume
Kkkkk ati uyu nde wanutu uyu 🤣🤣🤣
😅😅😅😅😅 koma mandota waonjeza m'pakana kamwana kazaka 14 koma abale akumangani kangani paja ndiwapolissi
Mandota mkanjo umenewu uzauike pa auction,usanathe😂😂😂😂
Mandota umandiwaza gee😂🎉😂😂😂😂
Am watching from Lilongwe
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 mutu wabanja uja wagwidwa
Uwe baba matonda tusanyadraga ❤❤❤❤❤😊😊😊😊😊
Titugolele kwa sapoti jawo
Mandota akalowe ndithu kundendeko kenako akapange zachinyengo nkutulukako. Real life situation😊😊
Kkkkkkk koma ma amayili mukanawabisa kkkkkk big up Che Mandota
Wawojo achalume 💪💪
Akuti asisi uyu ndiye ndiwanutu. Pepani azimai
Nice one che mandota
😂😂😂 Umatha iwe. Big up
Nice one indeed!I salute you Mandota
😂😂😂Mandota ndikatundu
Kangotola masilipasi koma liwiro lokhalo😂😂😂😂🎉
Ziri bho izi
Kankhani akuti akachedwa eish ndakayika ngati atabweretse chenje ameneyo😂😂😂
Kkkkk eesh apa ndedi actor wafa basi big up chemandota
Odala mumatatu mwakomesha😂
Ati angooneka kuchepa😂😂❤
Kkkkk km iweyo ndilib mawwawuandota
hahahahahahahahahaha eeee ayayaayyaa koma Mandotaaaa......keep the fire burning
Akita wavadi🤣🤣🤣🤣🤣Big up Che mandota💪💪💪💪💪
We love you mandota here from zambia ......but I could love to have juz of you brand
Km guys sometimes at ndiganyu😂😂😂😂😂😂
Mandota lowani mkasiyo mukusiwa 😂😂
Kkkkk bwana mandota ngaŵa kamulwa soni kane kere, ngaŵa chine kusokonasya mlope
🎉😂😂😂 don't give up Mr Mandota you are teaching us how to respect our families
Mandota emweyo 🎉
Kodi ku inbuild Malo alipobe takatenga ma plot awiri nduona ngati muzipanga daily mumangepo popangira.
😂😂😂koma yah wagwidwa
Akumbwandira😅😅
Mamayili amandiwadza kwambiri serious 😂😂
😂😂😂 kubafa sinakose
akita wagwila ka nthete 😂😂😂😂 apapa waswa malamulo a boma wakumaula basi
Iwe unadza mandota 🙏🙏
😂😂😂😂 Che mandota suzatheka..nice one
Kkkk akita wagwidwa akadzidzimukila ku Central basi😂😂😂
Eeh koma ndasekaaa😂😂😂😂
Inuo ndi chi~vibe😂😂😂😂
Apapa sindinabese data yanga kkkkkkk koma mandota ndi wani bas
80k subs ..malawi to dih world🔥🔥🔥
Malawi to the world 💪🔥🤗🕺
che mumadya kasaizi yangat😂😂😂😂
Vidioyo ikumveka bwino I'm asomuli malangizo kwa akulu ogwidwa
Iweyo aseh 🔥🔥😂
mumakwana big brother
I'm the 1st one to comment, receive my respect Mandota🔥🔥🔥
Tipanga comment koma mwagwidwa inu ❤❤❤❤❤❤
Kubafako sinakoseko 😂😂 koma ndoxy
Mandto very nice video
Koma Chenji wabweletsa Uja??🤣🤣🤣
Eeee bola ma mayili abwera, ndinawasowa
🤣🤣🤣🤣🤣 kuwamenya basi kkkķkķ
Osamamenya asibambo,asibambo ndi mutu wabantchaa,
Iweyo sukhumudwsa aseh😅eeeeish km ndaseka🤣🤣🤣
🤣🤣Mandota unabwera
Iweyo nda dolo 😅😅😅😅😅
Wachiyo wangalusa ulemu wao adala
Sikuti dzuwa lilowa asanapepere kkkkk
Cholera watan mwati😂🤣
Big up bro nice
Mumatiimilila bro mandota
Iwe ndie watha basi
Keep it up ur doing great job
Akufupika akita sachedwa kufa kkkk
Koma actor wafadi kkkkkk
Mandota never disappoint 🔥🤟
😂😂😂😂😂mutu wabanja usamenyedwe😅😅😅
Best comedian of a decade
Kikikiikiki Chemandota mwamptsa ma sweet angati?
Mandota ❤
This is nice. Keep it up 🥳🥳🥳
Nice brother
Wagwidwa mandota 😀😀😀😀
😂😂😂 mandota sazatheka
Chemandota apa mwatisokoneza, malizisani ya malo ija aaaaaa. Amologoni anakuendani pasi, pokupasani mapepala aboza. Inatha bwanji?
Timasiya kuti muzimaliza nokha mmaganizo😂
Moto unandi 🔥🔥🔥
Mumakwana sala
Wow ❤nice cha
Inadyambulidwa lit shimangachi
Mandota mwana wa zaka 14 ukakhalaso kundende zaka 14
Siinathe bwino 😭😭😭😭😭
Akanalowa km
Good video
U just made my night😁😁😁
abwana mumaita OK one
Wava ndi imosi yoneco bas
Madhala Mandota 🎉
Apa nde UNECO imutenga mandota
Nice one
Big up bro

Nice one indeed!
I salute you Mandota
😂😂😂Mandota ndikatundu
Kangotola masilipasi koma liwiro lokhalo😂😂😂😂🎉
Ziri bho izi
Kankhani akuti akachedwa eish ndakayika ngati atabweretse chenje ameneyo😂😂😂
Kkkkk eesh apa ndedi actor wafa basi big up chemandota
Odala mumatatu mwakomesha😂
Ati angooneka kuchepa😂😂❤
Kkkkk km iweyo ndilib mawwawuandota
hahahahahahahahahaha eeee ayayaayyaa koma Mandotaaaa......keep the fire burning
Akita wavadi🤣🤣🤣🤣🤣
Big up Che mandota💪💪💪💪💪