Ku utm mukut kunali ufulu opikisana nawo pa mpando wa president coz chinali chamasiye and kukanakhala kut Chilima aliko sipakanapezekaso opiksana nawo akanayendaso yekha pa u president tiuzanepo apa
Ku Mw ndale anthu tlinazo kutali kwambiri...we dont know chomwe DK analandiridwa ku UTM,and omuloreza kuimiliranso u President...and ndi gulu la Kaliyati omweo anavomereza kutero...tikamayankhula,kumanyoza tizikumbukira kuti kuli mawa nso
Atolankhani aku Malawi, mukuonjeza ndinu amene mukusonkhezela moto, asiyeni anthu apange okha maganizo awo, you're fuelling fire on political matters, check your ethics
Let's think twice as much about what late Goodall Gondwe said 6 yrs ago Kuti NDALE SIZIFUNIKA ANA , AMAKULILANA MITIMA , look achina USI, .. Kabambe failing to stop Usi using nsalu Za UTM
Ukamalimbana ndi chitsilu,anthu owonawo amangoti nonse ndizitsilu...don't think DK have that time to stop Manganya...chizereza chioneka bwino bwino 2025Sept
Mumapangisa ndinu antora nkhani osamapanga Chocho amene aja anachisunga chipani kuti akabambeo achipeze
Azimayi a UTM ine. Ndimawadziwa ndi osamba awa akuyenda ndi usi ndi osasamba a MCP kaye. Kununkha isiyeni. Nsalu yathu musaveke nyawu.
Kabambe my vote. Amene aluza asataye mtima agwirane manja ndi Kabambe. Inu atolankhani musasemphanitse anthu
Atolankhani inuyo mulibe umunthu, tchito satero ayi,kagwireni tchito yanu mubwereko muzapitilize tchito yanu, osati zomwe mukunenazo
Amayi akulu DR PATRICIA KALIATI musamvere zimene akunena anthu khalani olimba mtima, komanso gwiranani manja ndi akabambe ndi nonse pamodzi ndife akumudzi tichotse boma lamanyili
Mayi Kaliati alibwino tuuuu sanayamibile pano kuluza inu sinkhani yomukweza mtima iyi ayi
Ndiponso
Ndikabambe ekha amene akatenge mpando 2025 azachotse ma Bez onse aasilikali Aku America kuno kumalawi Ife tamudalila kabambe monga Ife amalawi kut it's our traore
Ku utm mukut kunali ufulu opikisana nawo pa mpando wa president coz chinali chamasiye and kukanakhala kut Chilima aliko sipakanapezekaso opiksana nawo akanayendaso yekha pa u president tiuzanepo apa
Ku Mw ndale anthu tlinazo kutali kwambiri...we dont know chomwe DK analandiridwa ku UTM,and omuloreza kuimiliranso u President...and ndi gulu la Kaliyati omweo anavomereza kutero...tikamayankhula,kumanyoza tizikumbukira kuti kuli mawa nso
Atolankhani aku Malawi, mukuonjeza ndinu amene mukusonkhezela moto, asiyeni anthu apange okha maganizo awo, you're fuelling fire on political matters, check your ethics
Ukayishosha ndeuyo imakukanika amkawona Ngati ndewuyo ayiwina kuchenjera mopusa uyuuu
Apa a usi zomwe akupanga. Nde. Kuthundukwa ndiyemwe anapha Chilima galu ameneyu azimayi akuyenda nawo ndi a odya zake alibe mulandu asatinyanse usi
Selina ndi zakoyo uku sikunkhala😮😮😢
Hule anapwa chilima kuti akhale president wa UTM, wanyanayo kaliati. Wagwa ndi first failure hule kaliati
Ukuyankhulira kusaziwa...Ambuye yekha ndiamene angakukhululukire
Atolankhani awawa ndiosathandiza ndiponso oyambanitsa m'malo momawerenga nkhani zothandiza mumaterotu mukachotsedwa m'boma mukaba inuyo kuyamba kumanyitsa anzanu osayiwala mawatu ,awatu ndi inu
Kumeneko simukupanga bwino chifukwa Inu ndinu omanga chipani nanga mukamatero mukusokoneza anthu
Zitsiru za atola nkhani kulibwino kusiya agaru inu.
😂😂😂😂😂 koma OBanda ndi wamwano mpaka mwat kukamwa yasaa
Later fight each other 🤜👨🤛😒😒😒
Ngakhale makosana Inu muchiture kampeni utm, koma ulendo unu Chakwera akutengaso boma molapitsa. Kabambe ndi mlendo, mcp boma
Koma amalawi sazatheka
Malawi sažatheka
Kodi aChakwera mumawaderanji anthuni anthuni Kabambe katangale
Ayi Inu ndiinu athu osokoneza atola khani
😂😂😂koma nyimbo zinazi 😂😂😂😅
UTM yatha
Akaliyati anayakhulisa kkkkkkkkk 20 mm
Chipan cha masiye ichi nanu
Kkkkk nyimbo zinazi 😂😂😂is

Usi ndi kape😵💫