A prayer worth praying to God. Precise and direct. A mere person seems more spiritual and moral than Reverends. Let GOD arise and His enemies be scattered.
Its very shocking to hear that moderators from Nkhoma ccap were invited and blessed with mk10 million each only to continue troubling the innocent people of God,keep my words God is watching and ready to serve his poor people and for those planning evil they will perish in red sea as the Egyptians were still this government is going
Komanso azibusa inuyo mumapemphera mu chooona? Ndinudi atumuki a Mulungu? Koma mukudziwa kt Mukadzafa muzaweruzidwa? Oky ndi pemphere nanenso. Kwa ife ayi kwa ife ayi koma kwa zibusa onse amene asakufunira Malawi zabwino zabwino. Muwakathe azibusa amenewa ndi mabanja awo ndipo muwachotsere mwai wao. Achite manyazi pa September pano Amen
Abusa mwalandira ndizoona be reminded that God is above everything if you wont repent you have welcomed the evil spirits into your ministrial work from the darkness underneath the waters finally you are finished
Azibusa Yesu wake uti amene mumkutumikira? Yesu mwini wake adaletsa malonda mchalichi nanga ichi ndi chiyani? Ambuyee tilandilen chakwerayu eeeee km Ambuye mumasunga mivivi kunjaku mukutenga Abwino km zilipozi ndiye kaya
Mwene musadabwenazo zimenezi Padzikolose ndichipembedzo chimodzichokha bas chomwe sichilowerera za ndare zinazi ndi mahure kusakaniza za mulungu ndi za kudziko chibvumbulutso 17ves5
Mulungu wava mapemphelo anu atanyiwa ndipo mulungu tipembedza ndi wa moyo atimenyela nkhondo sizintheka amen and amen💪🙏🙏
A prayer worth praying to God. Precise and direct. A mere person seems more spiritual and moral than Reverends. Let GOD arise and His enemies be scattered.
Mu mdzina la Yesu nkhristu Amen
Its very shocking to hear that moderators from Nkhoma ccap were invited and blessed with mk10 million each only to continue troubling the innocent people of God,keep my words God is watching and ready to serve his poor people and for those planning evil they will perish in red sea as the Egyptians were still this government is going
Zisantheke indeed ,mutiyendere ife Malawi Ambuye wathu wakumwamba🙏powerful Ntanyiwa🙏
Amen and amen Isaiah 32 vs 17 :27
Amen comrade
Azibusa adyela a ACCP asiyana ndi azibusa a Catholic ku Catholic kuli azibusa adzelu not ngati CCAP,
Amen Amen and Amen comrade
Eeeeeee abusa mwawonjeza......siwonse akuti ambuye ambuye akalowe kumwamba but there is God in heaven
Ambuye Mulungu olenga kumwamba ndi pansi pano amene muli mwini wa zonse atate tikuku pemphani kuti landilani kulira kwa Malawi ndipo azibusa a ccap muwalange koposa nsinkhu wawo 🙏
Amen !!!!! Please God help Malawian
MULUNGU AMAONA,comrade ntanyiwa pemphero lili lonse MULUNGU AMAMVA ndipo lero MULUNGU WAMVA kulira kwanu,MULUNGU AkHALE KUMBALI YANU NTHAWI ZONSE 🙏🙏♥️♥️♥️♥️
We need u more comrade ntanyiwa ❤❤❤
Komanso azibusa inuyo mumapemphera mu chooona? Ndinudi atumuki a Mulungu? Koma mukudziwa kt Mukadzafa muzaweruzidwa? Oky ndi pemphere nanenso. Kwa ife ayi kwa ife ayi koma kwa zibusa onse amene asakufunira Malawi zabwino zabwino. Muwakathe azibusa amenewa ndi mabanja awo ndipo muwachotsere mwai wao. Achite manyazi pa September pano Amen
Si ONSE OTCHEDWA AZIBUSA AMAKHALA OZOZEDWA 😊😊
Azibutsa a CCAP amakomedwa ndi ndalama onse koma anya anthu awo sangapange zoputsazo
Mmmm Malawi wathu watani!!!!!!!!!!!!!
Amen,Ambuye ife ana anu tichotsereni satana oipayi
Abusa mwalandira ndizoona be reminded that God is above everything if you wont repent you have welcomed the evil spirits into your ministrial work from the darkness underneath the waters finally you are finished
Azibusa adyela chiujeni chanu
Azibusa Yesu wake uti amene mumkutumikira? Yesu mwini wake adaletsa malonda mchalichi nanga ichi ndi chiyani? Ambuyee tilandilen chakwerayu eeeee km Ambuye mumasunga mivivi kunjaku mukutenga Abwino km zilipozi ndiye kaya
Fire in Jesus name fire in Jesus name 🙏🙏🙏🙏
Chauta, imvani kulira kwa a Malawi....😢😢😢 Amen.
Amen mulungu atimenyela khondo sawina amenewo
Amen. God knows and he will act accordingly.
Very powerful comrade ❤
Kodi osadabwa bwanji MCP ndi Chakwela akugawa ndalama Kwa Azibusa ziwilatuni kuti ameneyu ndi nyenga akudziwa kuti MCP yathapo.
A Yassin Gama monga alandila nawo?a Kambiliso alandila?ndakayika
Amen amen God will help us all malawians
Ndipo azibusa anenew akakhalaanzeru angodya ndalamazo koma mudziwe kuti azibusa alowa corruption😊😊
Komano ndalamazo pomwe amatengapo ndiye zilipotu. Momwe anayambira kupereka muja?
Amen and Amen powerful prayer
Okamoto ndife osati azibutsa akunama ameneo akata okay ife ayi
Amen..mulungu akyona zonse
army inali kale disciplined osalowerera za politics
Ambuye mudalitse azitsogoleri a mpingo wakatolika umene sulemekeza chuma Cha dziko lapansi osati azibusa adyera a CCAP ku Malawi kuno sapembeza mulungu koma amalemekeza chuma mulungu muwakhululukire azibusa adyera osasamala mavuto ankhosa zawo shame on you CCAP pastors tipereke ulemu kwa ma bishop akatolika ambuye akudaliseni
Very powerful, Amen 🙏
Chakwera wafka pondiwawisa mutu ...mwati ndimwana Wana wandani 😂😂
Yehova timenyere nkhondo tipulumusenidi ife abale anga akugona ndinjala chifukwa chaulamulilowu
Amen Powerful 👏
Antanyiwa Kodi inu ndimtolakhani kapena mmbusa mumatha
AMEN 🙏🏻 🙏🏻
Immunity ndiyoopsa kwambiri imawonongetsa dziko.
Chakwera akachoka zikufunika adzalandidwe chuma chomwe amabisa ku mayiko akunja
Amen amen amen 🙏
Amen, Amen
Mulungu wa Abraham, wa Yakobo musalore mcp ndi chakwera kuti abwerera kulamula uyutu suzawinaso azibusa agalu a ccap kumangoononga kodi chakwera ukuluziranji ndalama suzawinaso chakwera ukungooononga ndalama
Palije kuluta kuchanya imwe
Obey these CCAP clergies BUT please donot follow them.They are hypocrites MATTHEW 23 .
Pephelo limenelo tikupephela dairy tilipo gulu ndithu ndipo mulungu wayakha kale muzina la yesu
pemphero la mphamvu
Ameen 🙏
Mulungu awadzudzu azibusa amenewa
Kkkk 😂😂😂 Amen
Azibusa a fake awa
Kadyeni ndalama ya magaziyo
Well come Mr Ntanyiwa
Adyelatu ukumutora chakwera mcp ndalama zapweka akumudyera azazira zimenezo bwanji ubulutu chakwerayuuuu chiani nanga
Mulungu atithandize ndithu kukantha anthu iyipawa
Amen🙏
Nkhoma synod oyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeereeee
Mulungu omwe timuphera ndiwa moyo wosatha chakwera uzafa uli chilili
Abusa a CCAP alibe chikondi pa anthu awo. How can they do this? Iwo sakuona kukwera zinthu
Mulungu akumva mapemphero athu ndipo akuona
Amen
Koma achakwerawo mavuto adziko lino akuwawonadi?
Dziko lavunda Lazarus ndi azibusa a ccap apasana ndalama za magazi, akaseka okha maso Sunday likubwelali. Zovuta ziwaonekera okha olandira ndalama za satanic, malandila landira zikusolosani nonse munya
The love of money is the root of all evil.
Amithenga asatana anakumana ndi mbuye wawo satanayo ku state house.
Zawulele olo ine simdingakane,, Akakhala ovota aliyese adzavota yekha ndipo akasankha yemwe akumufuna
Mazibusa anthu lakula ndidyera ndipo amatichisa manyazi
Mwene musadabwenazo zimenezi Padzikolose ndichipembedzo chimodzichokha bas chomwe sichilowerera za ndare zinazi ndi mahure kusakaniza za mulungu ndi za kudziko chibvumbulutso 17ves5
Azibusa a nkhoma ccap alibe ngakhale panti angaleke kukapemphesa ku sanic?
Azibusa a nkhoma synod adyera
Agalu awa achoke basi
Mulungu azikusogolelan
Abusa verses azibusa
Masiku womaliza
Emen and emen
Amen
Amen 🙏🙏🙏🙏
Ameen🙏
Amen 🙏
Amen Amen
Amen amen amen
AMEN 🙏🙏🙏🙏
AMEN
Amen 🙏
Amen amen
Amen
Amen 🙏
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen