Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo Fm "Ma Demo Ankozedwa Kuti Akane Za Smartmatic Agulitsidwa"

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 9 лют 2025

КОМЕНТАРІ •

  • @NeliaGlaciano
    @NeliaGlaciano День тому

    ❤Mumati imilila boss

  • @PhillipChisanu-k3r
    @PhillipChisanu-k3r 2 дні тому +3

    Mu boma ili kulibe kuzapanga ma Demo,the reason is that they avoid kuchita manyazi fukwa maiko amzao akaona or kumva kut ku Malawi kuli ma Demo amadziwa kut muli mavuto or kut boma lalephera,ma Demo tizapanga tikazasitha mtsogoleri.Paja boma ndilomweli la Malawili koma tingosintha mtsogoleritu

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i День тому

    Comrade the one

  • @RobertBanda-m1m
    @RobertBanda-m1m 2 дні тому +2

    Vuto amalawi kutengeka ndi ndalama too much kungokufumbatisa Kena kake basi ma demo osachitika pomwe zithu zikuonongeka no mutu achewa

  • @dianachipondeponde2797
    @dianachipondeponde2797 2 дні тому +1

    Game ya activist it's not for broke people indeed mwamuona Bakili muluzi TV?😂😂

  • @ThomasJohn-j8x
    @ThomasJohn-j8x 2 дні тому +2

    Ife tipanga anthu mademo alindimamwana agwilitse apa ndi wafa wafa

  • @AnyuxyJulias
    @AnyuxyJulias 2 дні тому +1

    Kod mesa mukut smartmatic inapangidwa format apa mukut akufuna kupanga ma demo ot azasiye kugwilitsa tchito kwen kwen tinve zit

  • @kingSoko-wf4pe
    @kingSoko-wf4pe 2 дні тому +1

    Ma demo amenewo amafunika atsogoleredwe ndi a zipani zosusa osati amabungwe ayi achulukiridwa dyera ndi ndalama

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 2 дні тому +1

    Ngati zabooka adyereni.ovota ndiife

  • @joebonface4443
    @joebonface4443 2 дні тому +1

    Kodi ndye kuti opangitsa ma Demowo cholinga chimakhala chosaka makobiri eti? I wonder how come inu muli ndi cholinga chofuna kupulumutsa Malawi kapena kupulumutsa mimba zanu?

  • @HassanMawila-h5f
    @HassanMawila-h5f 2 дні тому +1

    Ntanyiwa ndiwe katundu wamalawi

  • @MapataMohammed
    @MapataMohammed 2 дні тому +1

    Just tell as

  • @CollinsEkhamunu-g2g
    @CollinsEkhamunu-g2g 2 дні тому +1

    More fire