Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Wow i know this choir since iwas 12 years old.. ndipo Muli unthenga wamphamvu ndipo unthenga wawo umandidalitsa ndiku ndi tsitsimutsa kwabansi
Send more of chamnyanga choir pliz
Waiting to upload full
Taponyani ya full please please please.
❤
Do we still have to wait, moyo ndi makiyi taponyani apa
Dzibwere nyimbo izi plz
Ponyani nyimbo yose please
Ponyani nyimbo izi anthu tikuzifuna
Nditukwanatu mapeto ake, ife tikuzifuna nyimbozo ka
Hahahaha ankolo
Taponyani zambiri
Am ready to support them, send me the songz please
I have link you with the Choir,what ever they tell me I will do sir ....thanks so much for that heart
@@thomasnkhomarangopicturesp89440:23
Very shortly guys we will be producing them all,we have 3 videos of these guys...
Taponyani ya full chamnyangayo
When are you uploading the songs?
Ndikudziwa guys zikuoneka kuti sitikuchita bwino posakuponyerani nyimbo ya full kapena nyimbo zonse,ndilumukizane ndi akwaya this week,ndawauza za pempha lanu .....
Its now a month
Titumizileni number yawo bwana
guys tumizani timvere
Tikudikilatu ma video mwangotilawitsa apa
Akubwera month end ino bwana atatu onse tiponya tikungofuna awatulutse natipatsa chilolezo kuti tiwaponye pano
@@thomasnkhomarangopicturesp8944 its now 10 months above the line