Thanks for your encouraging comments guys,we're still working on the other tracks,we have completed 2 tracks MOYO NDI MA KIYI AND ZOBANDUKA once they are done,shortly you shall have them here
Kumwamba ndikobeba kumangonkhalira kuvina basi..choir yanga yokondedwa since when iwas young at amponela ..More fire ntchawale ..Ambuye akupatseni mavumbulutso ochuluka
Imeneyo sitinajambule bwana km tinajambula ziwiri zina "Moyo ndi Ma kiyi kmso Zobanduka " zinamalizika ma editing chinatsala ndikuti tithane ku studio ....
Kwaya yakwathu Kee it up
People sing Gospel songs but this is the singing of God's Engels
Thanks for your encouraging comments guys,we're still working on the other tracks,we have completed 2 tracks MOYO NDI MA KIYI AND ZOBANDUKA once they are done,shortly you shall have them here
Tumizan zambili please ...timaikonda choir ya Chennyanga
Choir yi ili ndi luso komanso uthenga okoma zedi keep it up 🛐
I love you ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Kumwamba ndikobeba kumangonkhalira kuvina basi..choir yanga yokondedwa since when iwas young at amponela ..More fire ntchawale ..Ambuye akupatseni mavumbulutso ochuluka
Used to listen and like this truck way back
Tikudikilatu😂😂
❤❤🎉 Jesus is a Lord
Tumankoni zina pls nkati nkotheka ❤️
Great move keep it up muchiteso zinazija
🔥🔥🔥🔥
Nyimbo zamphamvu taikonda zedi keep it up
I miss ❤❤❤
ZIMACHEDWA KUTI SEND MORE
Anali asanamalize makobili ku studio bwana zatsala ziwiri akamaliza tiponyanso
This is amazing singing. Keep it up.
Congrats Mr. Thomas, send more from this group pliz if available
Nyimbo ziwiri zina tinamaliza ma editing koma ndalama zomalizira ku studio nde akusaka kaye bwana ....
Zilipo zinazi ndithu bwana wanga tamaliza dzulo anytime tiponya tipeze chilolezo kwa anuwakeo
Kumwamba tikanjoya
Amen 🙏 Nyimbo zathu izi
@@EstherManda-ex3bc hahaha inu ndia chamnyanga??
@@thomasnkhomarangopicturesp8944Eya takhalako Kwa Chimungu
Nice song,ngati zilipo zochuluka tiponyeren monga ija amati Ena anafa December sikuti nkufuna
Imeneyo sitinajambule bwana km tinajambula ziwiri zina "Moyo ndi Ma kiyi kmso Zobanduka " zinamalizika ma editing chinatsala ndikuti tithane ku studio ....
Amen
Nyimbo zabwino zija zayamba kutuluiira 🔥🔥🔥
Aaaah nnadziwa
Thanks ....nyimbo zamphanvu
Well appreciate
Tikudikila
Kukhala ngati drama koma mkatimo muli uthenga olama.
😂😂😂😂😂
Mshangano
Nyimbo za chimalawi
Nyimbo ya bwino uthenga wa bwino
Zinali kuti izi? yasala Moyo ndi makiyi ikufunika.🙏🙏🙏
Ndiponya mawali Moyo ndi Makiyi bwana
@@thomasnkhomarangopicturesp8944 ok abwana tapangani choncho
❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndizomwe timadikila
4:07
Amen
Amen