BON KALINDO LERO PA 5 SEPTEMBER 2024 | ZA BLACK BOX | MARY CHILIMA NDI JOKER WA ZIPANI ZOTSUTSA |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 142

  • @mikesangano6624
    @mikesangano6624 10 днів тому +11

    The DC, I'm your fan. Mumatiimilira ndipo umanena zoona zokhazokha. Keep the fire burning.

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 10 днів тому +2

    Tiyeni....Amalawi tigwilane maja ....tigwese Bomali tipage Chimozi.... Amalawi plz... Mcp yakwanatu

  • @AgathaChidatha
    @AgathaChidatha 10 днів тому +7

    Mr. Bon kalindo mumalankhula bwino kwambiri Marry is a good leader

  • @rennieyoublessmewiththisso4981
    @rennieyoublessmewiththisso4981 10 днів тому +4

    Mary Chilima ndi mkazi wa masiye musiyeni allele ana ake, kodi mulibe chisoni??? Mukufuna kuti Mary awasiye ana ake pa dzuwa?? Mary usapange ndale ino ndi nthawi yolira mwamuna wako komaso kulera ako osati kupanga ndale chonde chonde Mary usayambe Ndale

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 10 днів тому +3

    Kuti MCP ichoke pakufunika opposition yonse ipange alliance bas

  • @user-co6sc8om5n
    @user-co6sc8om5n 10 днів тому +3

    AMALAWI IFE KUGONA KWAMBIRI CHILUNGAMO NDICHOTI AMALAWI SITIMAKONDANA NDIFE AMANTHA

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 10 днів тому +6

    Nkhani iyi akalindo ife abthu wamba sitingamufikile presidentiyo anthu ofunika kutero ndi ma mp kumufunsa presidentiyo mu parliamentimo ngati julongosora kwake ndi kumeneko angomuwuza kuti turapasi udindo immediately

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa 10 днів тому +5

    Anthuwa akubelatu chifukwa akuziwa Kuti kusogoloku chawo kulibe akapanda kuba pano kumagula manyumba kunja kumanga ma Hotel ndima lodge ku malawi asiyeni basi,nawo a UTM alole mary chilima akhale president wa chipani osati manga kaya kwinako mumati chani

  • @agnesKachikunji
    @agnesKachikunji 10 днів тому +3

    ❤inde we need our mum Mary to be strong and agree to take UTM please we beg you mama Inthe name of Jesus

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 10 днів тому +3

    Malawians let’s wake up!!! This is straight forward issue President is supposed to do something on the matter basic on report but he is quite busy traveling, thats why we are suspect him to be involved on the issue.

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 10 днів тому +1

    More 🔥 the DC Booooooni Kalindo!! Mary Chilima ndi number one kuichotsa mcp ng'ona party no more in Malawi 2025.

  • @JonathanChimwaza
    @JonathanChimwaza 10 днів тому +3

    Mu nyengo yong'alura
    Dr chikangawa

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 10 днів тому +1

    Vuto amalawife tinapusa chifukwa amakhala ngati Maiko ena Maliro Achilima sanakaikidwa kufikira atafufu kuti chinachitika ndi chani Apo AI osaika Maliro mpaka Chakwera ature pansi udindo ndithu izi zinakatheka

  • @user-kb6ed1fq3s
    @user-kb6ed1fq3s 10 днів тому +1

    Born kalindo the DC mwan oopsa kwambiri ng'alulani paliponse the DC 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @augustMag
    @augustMag 10 днів тому

    You're the one voice of the justice speech 🔥🔥🔥🔥 the DC Boooon Kalindo never give up

  • @innobashirbernard7853
    @innobashirbernard7853 10 днів тому +2

    Mr DC our president ❤❤❤❤❤❤

  • @user-gk4nu4xr8r
    @user-gk4nu4xr8r 10 днів тому +4

    Pa Mary ndiye ayi

    • @AngelaMphinji
      @AngelaMphinji 10 днів тому

      Zoona.. Mpaka. Mary!!! Amalawi. Musamangolankhulapo. Kumawonanso. Kutsogolo.... Olo. Uja. Akumuti. Mtumbuka. Uja. Mmmm. Ndi. Zero!!!

  • @AndileyaMkandawire-x8r
    @AndileyaMkandawire-x8r 10 днів тому +1

    Kom thawi ya Peter kunali mademo ayooooo paka kuchoka kom apa kuliziiiiii

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 10 днів тому +2

    Dangerous Child a.k.a DC Boooooon Kalindooooooooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪

  • @RajabuAkibu-td8lf
    @RajabuAkibu-td8lf 10 днів тому

    Bon kalindo ndi wa malawi keep up my president we love you

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 10 днів тому +8

    Mulimbitseni mtima Mary Chilima The DC tikuonamo kuthekera.

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 10 днів тому

    Maliro aja ndi akulu kudziko laMalawi, sizingakhale zoona kuti mkazi Chilima pompanopompano apitirire kupanga zandale, timakuvetsani bwana DC and mumatiimira koma zankazi Chilima musiyeni kaye abaphwa misozi😢

  • @PraiseDuweh
    @PraiseDuweh 10 днів тому +1

    The Diiiiiii ciiiiii

  • @VioletMbale
    @VioletMbale 10 днів тому +1

    Am going back to Malawi if Mary agreed to stand as a president of utm you have my vote

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 10 днів тому +1

    The Dc Bon kalindo good message

  • @yohanekipandula5197
    @yohanekipandula5197 10 днів тому

    Our own DC

  • @Maxcarcare-g1d
    @Maxcarcare-g1d 10 днів тому

    The DC💪

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 10 днів тому

    The DC, business as usual imeneyi ikukhudza ambiri, ogwira ntchito ma department a Boma, ma Ambulance ambiri sakuyenda nkhani yake negligence ma bwana. Otsutsa Boma nawo Tulo , negligence, kudikira 2025 anthu azawavotere ..moti agwilizane alipane Boma la MCP to resign and form an interim government and change constitution. Azipani zotsutsa nao ndi okulilana mitima koma asazinamize kuti without coalition angatenge Boma pa okha.

  • @CassimWasotso
    @CassimWasotso 10 днів тому +2

    😂😂😂 Kodi Mesa akuti ndegeyi inanyamulmra maliro akasamphara Ulendo ku mzuzu nthawi imene imanyamura maliroyi zinthu Zimenezo munalibemo kapena zinachoka nthawi imene ikamanyamura vp

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd 10 днів тому

    The DC ❤❤❤❤❤

  • @johnmalefula1487
    @johnmalefula1487 10 днів тому +1

    This president must step down😢

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft 10 днів тому +2

    Mary my vote

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 10 днів тому

    The DC president waife amphawi

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 10 днів тому

    More respect big man!!

  • @MalanNzima
    @MalanNzima 10 днів тому +1

    Malawi yaonongeka umphawi watipweteka tasiya kufwila ntchito timangolandila ziphuphu ngakhale azibutsa alowerera kusiya chilungamo bola alandila ndalama tikuyendera ndalama osati malamulo adziko

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 10 днів тому

    Asirikali ndi apolice akumalawi ndi mbuzi za anthu...they only protect few thieves

  • @OsimanIbnAkim
    @OsimanIbnAkim 10 днів тому +1

    The DC HEAD OF SPEECH

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 10 днів тому +1

    Chitini zopanda madzi ndiye kalindo kod nthawi batile linatha nthawi yanji ndiye lelo mkunyoza chakwela osaphatikiza wosewo bwa galu ndipo ndipo ndiwe kambwee chikalindo kuchikamwa ngati wadya nyasi

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 10 днів тому

      Iweso chikamwa chakocho ngt dzenje la chimbuzi chokumba , mwana wa pedegu

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 10 днів тому

      Chikangawa son, ngt mukudya nawo ndalama zamagazizo thawi ikubwela Mulungu aku kwapulani limodzi. Kumaoneka ngt mashasha mukama commenta zoduka mutu muziona Malawi Mulungu amaikonda satisiya tokha

  • @LuciusScott-h7b
    @LuciusScott-h7b 10 днів тому

    Nice mbwiyanga

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 10 днів тому +1

    zosaveka anthu awa ndiwakumpha ndipo marawi sazatheka ndipo mukunena zowona from DC

  • @vynasvc
    @vynasvc 10 днів тому

    Mary for life

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 10 днів тому +1

    Ngati malawi first , tiuzeni tsiku lama demostration , tisangokhala chete,
    Sizingatheke kuti wina aliyense angozipangila payekha payekha

  • @sydemsamude190
    @sydemsamude190 10 днів тому

    team the dc❤

  • @AngelaMphinji
    @AngelaMphinji 10 днів тому

    Ayi. Mary chilima. Ndiye. Ayi. Aaaa. Amalawi. Mwatani. Kodi. Mumangotchulapo. Olo. Mtumbuka. Uja. Aaaa. Zero

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 10 днів тому

    More fire Bon Kalindo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

  • @timothymphwina
    @timothymphwina 10 днів тому

    ❤ bwana Born kalindo

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 10 днів тому +1

    DC 🔥🔥 amakwana

  • @sothinimwale3405
    @sothinimwale3405 10 днів тому +1

    Lero ndiye ndakumva bwino wanena zinthu zogwira ntima

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo 10 днів тому

    Mawu ❤❤

  • @user-pv2xx3lu8b
    @user-pv2xx3lu8b 10 днів тому

    Chinga khale chi alliance cha mphavu bwanji ❤️‍🔥❤️‍🔥

  • @LazarusWidsonChima
    @LazarusWidsonChima 10 днів тому +1

    Awo asaphatikizane ndi DpP adzaona mbwadza

  • @ErnestAllex
    @ErnestAllex 10 днів тому

    Mfundo ya Marry Chilima ndi #1 kma andale kukonda mipanda sizingatheke

  • @MayamikoMwale
    @MayamikoMwale 10 днів тому

    A born kalindo timakunyadilan nthawiwi zonse

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 10 днів тому +1

    Merry akukwanila

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 10 днів тому

      Gentlemen, let’s think like the new generation. What makes Mary Chilima a good leader? You can’t put Mary at the forefront of this battle. Politics is serious business; don’t joke about it. Why are you choosing her over all the men available? You’re confusing the followers. We don’t understand what you’re aiming for. Are you being bribed? Are you suggesting that Mary is more courageous and brave than Kabambe, Kasambala, or Mtumbuka? Be realistic, guys. Corruption is everywhere. You must be corrupt to campaign for her. Do you want to harm her the same way you harmed her husband? What do you mean by saying Mary Chilima can turn things around? Please elaborate.

  • @Penior265
    @Penior265 10 днів тому +1

    I caught the words Kaya ndikuso nkhondo

  • @lizzymotika3895
    @lizzymotika3895 10 днів тому

    MR DC kulankhula ndiye mwalankhala koma anthuwa Samantha ali ngati mbuzi

  • @KazembeSemion
    @KazembeSemion 10 днів тому +1

    ❤❤❤

  • @DoraMtegha
    @DoraMtegha 10 днів тому +1

    We need our mum Mary Chilima

  • @DicksonMacheso-lr7oy
    @DicksonMacheso-lr7oy 10 днів тому

    Amalawi olimba mtima tilipo koma bvuto mabwana ngati achina non kalindo mumatsowa kuti tilumikidzane,timangobuula basi

  • @FaithTricia-q5d
    @FaithTricia-q5d 10 днів тому

    Joker nd mery kod chikuvuta ndichan? Dpp Udf afrod utm nd ambewe please

  • @FrankWaresi
    @FrankWaresi 10 днів тому +1

    THE DC ❤❤❤❤❤❤

  • @80yami
    @80yami 10 днів тому +3

    Joker ndi Mary kumene❤️

    • @matiasphungwako
      @matiasphungwako 10 днів тому

      how special is Mary kuti DPP, UDF, pp,asiye zawo ndiye azikapanga za Mary ways bwanj iyeyo kalindo mmatimirira kima apa pokha simunayankhula za nzeru

  • @DoraMtegha
    @DoraMtegha 10 днів тому

    Pitilizani kutiyimilira....the DC🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z 10 днів тому

    More 🔥

  • @KhooNyoni-r1h
    @KhooNyoni-r1h 10 днів тому

    Big man

  • @godrick-s6w
    @godrick-s6w 10 днів тому +2

    The DC , go and meet her in person, the country needs her and she is the only person who can truthfully investigate what happened on 10 June 2024 to his husband and 8 others. Please Mary , take the mantle . It will be a compensation from God for the loss.

  • @ZioneMkangadzula
    @ZioneMkangadzula 10 днів тому

    akulu aku army ingonenani madeal omwe munauzidwa kuchita chifukwa zikukhalirani awa ngochenjera milandu ikhara mmanja mwamu

  • @DippedJob
    @DippedJob 10 днів тому

    Musiyeni Mary chonde asapangeso zandale

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula 10 днів тому

    100% love it.

  • @stuartsangaloti8461
    @stuartsangaloti8461 10 днів тому

    I support you bwanawe someone must resign sure panafunika mademo anyooo

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 10 днів тому

    Minister of homeland security ndi mbuzi yamunthu...i wonder whats gonna happen to this thieves when their time is up

  • @lizzymotika3895
    @lizzymotika3895 10 днів тому

    Morning

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 10 днів тому

    Mr boon kalindo the DC president wathu izi mukuyakhula mosabitsa Apatu amalawi mademo pamafunika ndithu

  • @JosephFulayi
    @JosephFulayi 10 днів тому +1

    Live

  • @blessingsmasina9254
    @blessingsmasina9254 10 днів тому

    Facts

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 10 днів тому +1

    Mary kungoimira atha kuwinilatu or osapanga alliance nd aliyense

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 10 днів тому

    Ndizooona chipani kuti chiyende ndindalama Sono Mai wo ndi jokadi mbali zonse komaso asakaike chitha kuwina kuzela pangwilizanowu

  • @MosesCaswell-f4h
    @MosesCaswell-f4h 9 днів тому

    Rodriguez Elizabeth Davis Anthony Taylor Lisa

  • @BonifaceNamakhwa
    @BonifaceNamakhwa 10 днів тому +1

    Kuswa kuswa

  • @patrickkapalamula2109
    @patrickkapalamula2109 10 днів тому

    The DC umakwana

  • @user-qp5rc5bk8p
    @user-qp5rc5bk8p 10 днів тому

    The DC 🎉🎉mary emweyooo ifee monga amaiii tili pambuyo pake

  • @AllanBinali
    @AllanBinali 10 днів тому +1

    Nkhani ndi ya Mademo

  • @SumatiFrecha
    @SumatiFrecha 10 днів тому +1

    Tinamufunakarekare ameneuja

  • @davieabel5631
    @davieabel5631 10 днів тому

    The DC

  • @LemsonManyowa
    @LemsonManyowa 10 днів тому +1

    Awa ndi akatundu ndimakunyadilani

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 10 днів тому +1

    Mary my vote 🎉🎉🎉

  • @cossaphyxo
    @cossaphyxo 10 днів тому +1

    Kung'alura kung'alura the DC

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 10 днів тому

    yes nkhani ndiyomweyo ya mary basi nkhani ndiyomweyo akufuna kubisa nkhani zambiri zukani mayi chirima anthu akufuna inu osaopa osafooka osatopa ambuye ati tsogorera

  • @SparrowBanda
    @SparrowBanda 10 днів тому

    Koma combination imeneyo ikhala yovutatu osati masewera

  • @FaithTricia-q5d
    @FaithTricia-q5d 10 днів тому

    Matha malawi

  • @MulinianiStenas
    @MulinianiStenas 10 днів тому

    Kd ngati munalibe zipangizo zolumikizana kuma airport nanga atanyamula maliro a kasambala amalumikizana bwanji? 15:03

  • @mikekambwiri5234
    @mikekambwiri5234 10 днів тому +1

    Uthenga wamphamvu kwambiri ndizoona mai chilima alsongolere chipani

  • @OupaGololo-l5f
    @OupaGololo-l5f 10 днів тому

    Osaopa panga comment bas the Dc

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 10 днів тому +1

    Kkkkkkkkkkk koma Dccccc umakwana

  • @BintonDzuwa
    @BintonDzuwa 10 днів тому

    Mukufuna kumuphanso mariya

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 10 днів тому

    Komaso akazi achakwera anati olo aluze iwo adalemera kare adaya khulapo izi akucheza ndiadzawo zinayenda pashosho npopa tinanva

  • @MercyMfune-dc3rq
    @MercyMfune-dc3rq 10 днів тому

    Ask them mr Dc

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf 10 днів тому +1

    Zoonadi

  • @LazarusWidsonChima
    @LazarusWidsonChima 10 днів тому

    Asiyeni anawo ayendepaokha UTM,AFORD ,UDF. ndiPDP

  • @PatrickBreak-l9v
    @PatrickBreak-l9v 10 днів тому

    Bon Kalindo, you are the man. How can I meet you?