Dr Lazarus Chakwera Kuyankhula ku Mtundu wa Amalawi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 29 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 228

  • @MastonWatson-g7g
    @MastonWatson-g7g 3 дні тому +9

    Nanga bwanji ukuba,ndalama mmalo mugula chimanga kuthandiza anthu?

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 дні тому +1

    Asala achimwen akulu Bakili Muluzi TV icant wait

  • @WezzieChisi-e1g
    @WezzieChisi-e1g 2 дні тому +4

    Ndimayesa kuti ayankhulapo za anyamata azikwanje kuti agwidwe onse amene anasokoneza mademo koma uyu chakwela atiphesa ndithu palibe chanzelu wayankhulapo munthu woyipa wakupha anapha chilima one day iyeso azamusata chilimayo 🇲🇼🇲🇼

  • @JohnKandodo
    @JohnKandodo 2 дні тому +11

    Ufumu wanu wayesedwa ndipo wagawidwa pakati pa DPP FORD UTM ndi UDF

  • @Abdul-u4r
    @Abdul-u4r 3 дні тому +7

    Nanga za zikwanje ukut bwanji?

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa 2 дні тому +4

    Tsiku ndi limodzi mulungu adzatibweletsera mtsogoleri wamzeru. Uyu ndi yona wadziko lathu .ubwelere ku mpingo otherwise utibvutitsa ndi mkwiyo wa mulugu.

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 2 дні тому +2

    Mkuluyu ngwa bodza koopya Mulungu anachotsa wisdom mmutu mwanu bwana

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 2 дні тому +1

    Vuto akulu awa maboza amaoneka ngt chilungamo koma ndifiti iyi😢😢

  • @ChimwemweJuwao
    @ChimwemweJuwao 2 дні тому +1

    Ayise ndiwe Muthu ofuna kumpangisa Muthu kuti achikwe bwererani ku mpingo konkuja musafune kutitora nkakwa apa zivayani

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 2 дні тому +2

    Akulu awa anati tikawapasa, office,tidzawayang'anile,2 years.ndipo,akalephela,pa zaka zimenezo,azachita resin.ifetu,timadikila,kuti asiya pasi udindo wa u president.one njala yabvuta two katundu wakwela mitengo.3, security mulibe muno.mr president musatibowe, just resin as you promised.

  • @MastonWatson-g7g
    @MastonWatson-g7g 2 дні тому +8

    Chindele cha pulezidenti ichi.

    • @fannyzimba149
      @fannyzimba149 2 дні тому

      😂😂😂chizeleza chaicho tchewe yakubwentha

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u День тому

    Aaaasa..!
    Iweyo ndi ndi chitsilu kwambiri padzana umkati chiani galu iwe kwambiri.... ndalama zosezi ukupanga nazo chiani.... manyazi mulibe achakwela Inu..... kuthawa tchito ya MULUNGU kumadzazuza amalawi 😢😢😢why why why... mtima wasanje ndi azako omwe amalamurila dzikori mbuyomu 😢😢😢

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm 2 дні тому +7

    Kodi akuti chani uyu guys

  • @DouglasDimingu
    @DouglasDimingu 2 дні тому +1

    Apa phindu palibe koma kumangoyankhu no actions

  • @MelnisaMaretho
    @MelnisaMaretho 3 дні тому +11

    Ambuye chonde tibwelesereni mtsogoleri mu dziko lathu la Malawi 😭😭😭😭😭😭😭

  • @DanielGeorge-l4h
    @DanielGeorge-l4h 2 дні тому +2

    Ingotigairani ndalama basi zinazo tikambiranabe😢😢

  • @IdrissahKampango
    @IdrissahKampango 2 дні тому +1

    Uyu ndiye ndi panja pa president weni weni kuyankhula ngt Ali ndi munthu koma Ali kape weniweni

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 2 дні тому

    A chakwera alibiletu mzelu zoyendesera Dziko mamina okhaokha mutu mwa achakwera komakani ndi kuba ndalama

  • @DavieZidana
    @DavieZidana 2 дні тому

    Nangabwanji mukuseweletsa ndalama mukuti mukamangila chiliza cha Gwanda Chakuwamba Mmalo mothana kaye ndimavuto anjalawa 2 billion plus ,zibwana zimenezo tayambani kaye mwapanga zanjalazi kampeni mupanga kutsogoloku

  • @LovelyAcorn-xi4bo
    @LovelyAcorn-xi4bo 2 дні тому

    Uyu sitsogoleli ndithu aaaa. Ndebolasoti amalawiwambafetu sitidalila zayeni koma awa nde aaaa pambali penipeni pawutsogoleli

  • @StanleyShadreck
    @StanleyShadreck 3 дні тому +4

    In ndie sinamve kalikonse😮

  • @JoannaNAMA
    @JoannaNAMA 2 дні тому

    APule wa penapake ndikawayang'anisitsa ndimaona kuti mutu wawo sumaseweza bwino. Apopo amazatiziwitsa kuti akuchoka.

  • @MAsd-r8s
    @MAsd-r8s 2 дні тому

    God help pls help Malawi, haaa this is nonsense 😭😭😭😭😭

  • @MathewsChitambe-m6o
    @MathewsChitambe-m6o 2 дні тому

    Nanga thandizoyo ikuperewera bwanji panopa popeza chithandizo chomwe mwalandira ndi chomwe chatsala chambirindi chomwe mealandilacho,mmalo mot chakudyacho chiyambe kupelewera miyezi yakumapeto yomwe munaiyelekezerayo monga February n March.nafensotu masamu timawatha.

  • @FaithSteve-t6h
    @FaithSteve-t6h 3 дні тому +5

    Bankha uyu kutidikilitsa koseku nkhani yopanda mutui

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 2 дні тому

    Koma chakwela ndiye bolanso munakamupepha the D.C. anakakulembelani likasa labwino apa ndiye wamuputa boni kalindo ndipo angowona kichedwa kucha akung'alule mawa pano chakwela usazapezekenso pa national address nanga zalipoti zili pati?

  • @AthonyChibwe
    @AthonyChibwe 2 дні тому

    Koma akuluakulu plz ichichi ndiye ayi tiganize bwino ndinthu nanga fundo zitatu zija ndizimenezi?

  • @KhadijaMsosa-d7z
    @KhadijaMsosa-d7z 2 дні тому

    Zomwe ndimafuna ayankhule sanayankhule...guys muganiza zomwe ndimaganiza ine?😂😂😂😂

  • @FelixWiskesi-d7w
    @FelixWiskesi-d7w 2 дні тому

    I thought he called us to resign

  • @ThumbikoChipofya-p8i
    @ThumbikoChipofya-p8i 2 дні тому

    Kod mavuto amafuta , fuel shortage, high inflation sakuwadziwa ?

  • @ShabaanKanyenda
    @ShabaanKanyenda 2 дні тому

    Kuteloku galu ameneyuyu zimene amafuna kulankhula leloli ndizimenezizi??

  • @Chafikanaomega-v4e
    @Chafikanaomega-v4e 2 дні тому

    Bolanso mwanawanga amayankhula ine ndikumva. Koma izi😢😢😢😢😢

  • @MuhammadWiness-i7h
    @MuhammadWiness-i7h 2 дні тому

    Feteleza wamakoponi chaka chino kulibe which means or mvula itagwa yochuluka kukhalanso njala yanyoo ngat alindimzeru akanagawa makoponi ochuluka kuthani ndinjala yachaka chamawa akamayakhula ngat kut akunva chisoni mmmm koma chakwera iweyoo ooohooo

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 дні тому

    Kodimwati zimenezi ndimfundo za President 😂😂😂kalanga ine malawi wanga😂😂😂

  • @GranceChirhwa
    @GranceChirhwa 2 дні тому

    Palibepo chazelu Mr Chakwera malawi limba ntima

  • @BlessingsBanda-ol9kc
    @BlessingsBanda-ol9kc 3 дні тому +3

    Useless speech ukanangosiya u mean head of state alibe mphavu yolamula a police kt amange axikwanje very stupid. President

  • @neemahkapatamoyo9563
    @neemahkapatamoyo9563 3 дні тому +2

    Ndipo palibe chanzelu chomwe walankhula uyu ukapita kunjako umabwera ndi Chani? Zaziiii uko munthu olephera iwe basi BZ kumatenga ndalama Za anthu osauka kumapitila kunjako

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 дні тому

    Kkkkkkkk akupengatu uyu 😂kapena ziwanda, kodi iwe chakwera ndikakupatsa vote yanga chimanga uzatingulitsa bwanji😂

  • @GiftChalunda-ss9qu
    @GiftChalunda-ss9qu 2 дні тому

    Pathako pake inu Uyu zoona fertilizer anamupeza pa 20 000 after 4years akamufikise pa 100 chakuti zimenezo ndizoona

  • @HandEllah
    @HandEllah 3 дні тому +3

    Diso linalo latupa bwanji 😂😂😂😂

  • @DeeHMugonya
    @DeeHMugonya 2 дні тому

    Anyamata zikwanje aja bwanji akuwatuma ndani?.

  • @MkandawireKennedy
    @MkandawireKennedy 2 дні тому +1

    Nde mwat zazikwanje mkuti bwanji apule pena kumaganiza zofunika kumaganizila anthu osapanga zachibwana

  • @MikasHsiwwh
    @MikasHsiwwh 2 дні тому

    Kkkkkkkkkkkkk wa yesu yemweyo komano mutimamo mulisatana ndinukapena ndiwina aaaaaaaa nakhano nyau zija ndizandani nakhano azikwajeaja ndiandani😂😂😂😂 you good Bros you today

  • @JamesonKayuni
    @JamesonKayuni 2 дні тому

    Plz plz azakhalenso pompho tizaimbe ma fon azitiyankha pwala lako pat

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 3 дні тому +1

    Ngati mumadziwa kuti mudziko muli njala chifukwa chiyani mulibe nthawi yokhala ndi a Malawi
    Pa kucjepetsa kuyendayenda

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 2 дні тому +2

    Amalawi zachisoni tsogoleri uyu palibe iiiii nkhani yake ya ziiiii

  • @AmisiDytoni
    @AmisiDytoni 3 дні тому +3

    Mundilakwisa kumalankhulidwe

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 2 дні тому

    Inu mkanena kuti nkhondo ya ku Ukraine ndi imene ikusokoneza zinthu malawi muno,, zitheka bwanji anu ake a nkhondo kutithandizaso ife anthu tilibe ndi nkhondo yomwe 😢😢😢

  • @AbdulazizWyson-dq3ce
    @AbdulazizWyson-dq3ce 2 дні тому +1

    Chakweratu
    galu
    nyani
    mphaka
    nyalubwe
    mfiti
    nkwhezure
    kazizi
    pusi
    chigananga
    kapolo
    Galu wachiwewe
    machende ake nyamako
    opanda mfundo
    Olephera
    iweyo ndioluzaluza pita uzikaseta ndalama wabazo

  • @mosewallace9717
    @mosewallace9717 2 дні тому

    May God bless Malawi 😭😭

  • @User_n6-8n
    @User_n6-8n 2 дні тому +1

    2 king 8 :35 verse limeneli likutsimikizira kuti ngati mvura isakugwa nde kuti tachimwira mulungu wakumwamba ,in short Mulungu sakukondwera ndimomwe mukuyendetsera dziko Mr president God bless Ambuye akumbukile malawi

  • @John-e2v4l
    @John-e2v4l 2 дні тому

    Mene chakwela amayamba kuyakhula...........chindege chimayenda bwino🛩️🛩️
    Ndadyatu kuno...........mawa ndilipila lent........
    Chakwela akuchedwesani

  • @user-nt5yn2im6t
    @user-nt5yn2im6t 2 дні тому

    Zonama izi chakudyacho umapereka kuti?

  • @binalisaidi7617
    @binalisaidi7617 2 дні тому

    For 4 years kumangoti zokhoma zokhoma 😂😂😂😂😂 Mr

  • @DeavncKapesi
    @DeavncKapesi 2 дні тому +1

    Unatembereredwa iwe sukuziwa zimene ukupanga😢😢😢

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 дні тому

    Zaziiii olo ana oti sanamadwe akuopa kumadwira ku Malawi,

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 2 дні тому

    Ku Malawi kulibe President chonde boni kalindo mwezi yasalayi alandileni akuwa

  • @IshmaelKhonje
    @IshmaelKhonje 2 дні тому

    Kod ndindani amene Ali ndi number ya achakwela NDA tandize kulangula

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 2 дні тому

    Ameneyu ndiochimwitsa mulungu amukhululukire sakudziwa chomwe akuchitsa

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 дні тому

    Chitsiru chamunthu galu wachabechabe koma mutu mwake muli uzimu kapena misala futsek chikangawa Belezebulu gulukunyinda iwe za chabedi nanga anthu a kudya chitedze iwe kunyamula ma team kumapita kunja ,galu iwe ndiye mafuta alikuti nanga chilikuti chimangacho usatichimwitsepo

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga 2 дні тому +2

    Manyaka iwe

  • @SkabhuKabhu
    @SkabhuKabhu 2 дні тому

    Agendedwe ameneyo akangoyenda ngani ya zikwanje wayisiya bwanji ameneyu

  • @JumahIssah-d2n
    @JumahIssah-d2n 2 дні тому

    💔💔💔mbuzi iyi singapulumutse amalaw

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 2 дні тому

    Aaaaaa chakwera ndi alibedi mzelu matope okhaokha mmuumu

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 дні тому

    Mukafuna kuphwisa chitulutseni ndithu chifukwa kupana chiphwisi mpweya umene uja ngwachabe umathamangira ku ubongo kukachotsa nzeru za munthu mkumachita zopepera ngati chakwera phwisani musachite manyazi kuopa kudzakhala ngati mkuluyi chifukwa mmutu mwake mzeru mulibe 😮😮

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 2 дні тому

    Ine ndabwereza kunvera Ka 1000 koma palibe chimene ndanva nde inu mnyamata wa Malawians camera ndimasuliren chonde ndagwira mwendo wanu😂😂😂

  • @ManzuzoMbawa
    @ManzuzoMbawa 3 дні тому +2

    Ndangotayapo nthawi koma palibe chomwe tayankhula po cha nzelu

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 дні тому

    Usafotokoze udati suziwa za boma tangokamba za kuchipiku, kodi uti chani zinyau bwanji monga mkulu wa dabwe munthu ochititsa manyazi😢

  • @CharlesMatope-xg6ln
    @CharlesMatope-xg6ln 2 дні тому

    Aaa cha nzeru palibe apa nditukwana

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 2 дні тому

    Palibepo chanzelu walankhula kodi thanzizolo wapatsandani

  • @AustinNkhula-j6y
    @AustinNkhula-j6y 2 дні тому

    Koma ndiye mathandizo mwalandilatu koma nanga zilikuti kapena ndizimene mwaunjika mmanyumba mwanu

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi 2 дні тому

    Ine ndimaona ngat akufuna kudziwitsa anthu kuti wapanga resign

  • @ChilindaJustin
    @ChilindaJustin 2 дні тому

    Ulichindere iwe chakudya chipezeka bwanji mtengo wa fetereza mmene ukudulilamu chisilu chamunthu

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr День тому

    Atembeleledwa awa mizimu ya anthu 9 aja ikuyenda ndi achakwera mutu sungagwire bwino ntchito

  • @D.RJALLI-qo6yd
    @D.RJALLI-qo6yd 2 дні тому

    Kodi amakulembela ndani dzoyangulazo zanuzo koma akukuyu iwe ndiwe mbatata kobasi galu wamuthu mbudzi yeniyeni ndiye anthu akufelanji wose akutandidzawo dzili kuti galu iwe chakwela😂😂😂😂😂

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 дні тому

    Aaaaaaaa.. ...clueless!......... dziko lino lili pa njala yoopsa....panopo, za ndalamazo mukudziwa ku office kwanuko..koma mmalawi sizinamufikire....kaya mwina kwanuko!

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward 2 дні тому

    Ndimadikilirila kuva kulankhula kwa pule koma dakakozekera palibe fundo yazelu yomwe alakhulapo yazelu

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l 2 дні тому

    Wamanyi ameneyo maphazi Ake achoke ameneyu wawusili

  • @FundoNdeketeya
    @FundoNdeketeya 2 дні тому

    Ndiye iweyo ndi president koma you think like a child pano Malawi azivutika iwe ukudya batile basi Kumati bola anakuvotera 😂😂😂😂

  • @DoniAliha
    @DoniAliha 2 дні тому +2

    Koma.xina inu tayakhulana xazeru 😂😂😂😂😂

  • @AbdulNyambi
    @AbdulNyambi 2 дні тому

    Chakwera machendiyako mpaka muyaya iweyo unalanda boma ulibe plan yoyendesela ziko utule pasi udindo wakanika chisilu

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga 2 дні тому +3

    Mbuzi ya munthu

  • @PaulSymonch
    @PaulSymonch 2 дні тому

    Nzodabwisa kuti a president sanatchule boma kan nkhata-bay ndiye kuno kulibe njala...
    Izi nzodabwisa kwambiri
    Nkhata- bay
    Mzimba osatchulidwapo kut kuli njala

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 дні тому

    Amalawi tiyen tilimbe mtima tilibe ntsogoleri, ndmayembekezera kumva zanzaru km apa palibe ndamva ine walankhura nyaupe ameneyu

  • @peterthawi
    @peterthawi 2 дні тому

    mmmmmhhh koma apapa nde ku malawi zativutatu...dziko kungokhalira kupemphetsa,ndikuubweleka ndalama...eeeehhh

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 2 дні тому

    Koma apul mutuwanu panokha umagwila ntchito zimenezi ndizinthu zouza amalawi mukulankhulazi ndizoenera kumauza azikwanje waja osati dziko panyapako boloyako pantumbopako nyini yamako chakwera

  • @cuthbertjafali6059
    @cuthbertjafali6059 2 дні тому

    Yona adali mtulo anthu akuvutika kutaya katundu namondwe atavuta, Yona adali wachilungamo adadziwa kut mavuto onse achitika chifukwa cha Iye that's the exactly thing zuchitika mmalawi muno, once he steps down mtendere ubwera pamalawi

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 дні тому

    Za ziiiii ine ndimawona ngati mukamba za zikwanje mwina za smart Matic machine njara imene tilinayo inu munachita kukoza Kuti ife amalawi tizikugwadirani chiti

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 2 дні тому

    Zopanda nzeru zimene ukuyakhura iwe

  • @HajieMusitafa
    @HajieMusitafa 2 дні тому

    Kkkkk koma zinadzi koma uyu ndi sogoleli wa dziko dzamanyadzi pali chazelu wayangulapa 😂😊

  • @PeterJames-i8y
    @PeterJames-i8y 2 дні тому

    Mbwerera zokhazokha palibe cha nzeru wanena

  • @Atheeeefire
    @Atheeeefire 3 дні тому +2

    Zero over ten ndy kumati boma ndi lomweli zopoilazi

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 дні тому

    Nde jalayo feteleza alikuti wavula ikubwelayi, zimene ukuyankhula sukuziziwa mbololi Yoko bola ukanangokhala osati putila mkwiyo wathu.

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 2 дні тому

    Mr president chonde chonde Kodi kumudzi kwanu muli ndi mbumba koma inuyo bwana kwayine ndakukayikira kwambiri pa zochita zanu simungakwanise kumanga mudzi anthu amayambatu bwana ndinthu zikomo kwambiri Kuti muli Ku boma lathu la Malawi eeeesh mulungu salakwitsadi eti palibepo ndamvapo ine eeeesh

  • @JohnSanudi-p9f
    @JohnSanudi-p9f 2 дні тому

    Ndalama zonsezo mutela nahule ku state house bas

  • @ElijahTheprophet-y9m
    @ElijahTheprophet-y9m 2 дні тому

    Plz plz plz ine sindikufuna kutukwana achewa ai koma bulutu uyu akufuna anyozetse mtundu wawo

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 дні тому

    No no no! zikomo amenewo , you would have made some phone call to them not on air!

  • @ChrissyWanda
    @ChrissyWanda 2 дні тому

    Zumuudza mwanatu izi otsati nkulu ngati ife,kodi akuti Chiyani chikangawayu apa Ambuye tumidzani mtsogoleri yemwe sananyamulepo matumba ku chipiku ndi kudyera anthu ndalama ya cha khumi kwa anthu Osauka.

  • @JamesLidson
    @JamesLidson 2 дні тому

    Mwina ineyo umbuli wanga ndwaukulu kwambli pliz wina andiuzeko mfundo zitatu zokha zmene wayankhula

  • @FundoNdeketeya
    @FundoNdeketeya 2 дні тому

    Kodi uyuyu alinawo ndithu makolo 😂😂😂😂 I never see this in my life this worse