MEC YATEMESA NKHWANGWA PAMWALA KUTI OPANDA NATIONAL ID CHAKO PALIBE ZIIMVERE NTOLO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 26

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 години тому +2

    Akawina usi tonse tikupita ku dpp ndi afford cz udf idatha mcp ikatipha😢

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 6 годин тому +2

    Akufuna kuba chipani uyu usi i don't trust him

  • @officialturfrican_ent
    @officialturfrican_ent 6 годин тому +1

    AKupanga zonyanyalitsa anthu osalakwa kuti okhao a mcp azakhale ndi mphamvu yolawila kuzaponya voti 😢

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 3 години тому

    Annabel akudalila Chan Kodi Mesa adachita kusakhidwa zothekanso kumuchosapo kuikapo ena

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 6 годин тому +1

    Musalore ndiye chakwela achokela madem

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 години тому

    Ndili ndi maganizo ena oti tizapange lisanafike tsiku loponya voti ,
    Ndaonazoti pakufuna pachitike zibwana zofuna kutipusisa ngati ndife masaizi awo .
    Ndiye tidikile kaye

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 6 годин тому +1

    Koma mcp why koma a opposition please musalore zimene kapena kugonjela amcp please musalore 🧎🧎🧎please please guy's amec apasidwa ndalama musalore. Chuma chamalawi sichikuyenda bwino athu kudya kopelewela. No economics mcp wy.

  • @CharlesBande-yr1yb
    @CharlesBande-yr1yb 5 годин тому

    Musadandaule ai ndili momuno ndibulitsa mec yo ine akunama amenewo ,tangotini ziii.

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 5 годин тому

    Osaopa osafooka osatopa chilungamo chioneke sitikufuna Smartmatic ayi

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv 2 години тому

    Nrb ikulemba amcp okhawokhakodi mantha bwanji anthu inu

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p 6 годин тому

    Malawi is now hell on earth

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 6 годин тому

    Kodi palibe anthu ena
    Ndiye tisankhe anthu ena ogwira ntchito
    Chifukwa ndalama zimene akagwile ntchitozo ndi za Malawi

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 5 годин тому

    Anamalomba palibe kudekhanso apa nde kulibwino dziko alitenge asilikali tisazakhalenso ndi president ochoka ku ma parties

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 4 години тому

    .mwambo not mambo

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 6 годин тому

    Apapa pakufunika ma dhemo iyiyi osatekhe because ambili tilibe ma id

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 34 хвилини тому

    Dpp utm afod bomah

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 6 годин тому

    Komatu wonani zomwe zikuchitika ku Mozambique light now

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 4 години тому

    ADAKAIMIKIDWA KAYE .not adainikidwa

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa 5 годин тому

    Kom uyu akufuna kutula udindo ndimademo kom kusanvaku ndalama kapena chan

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 6 годин тому

    Kalemberayu.adakainikidwa kaye.chifukwa andale zonse sakubvomereza .ndipo dzikoli.ndilatonse osati mcp yokha

    • @WisikiBlack-gj4gu
      @WisikiBlack-gj4gu 6 годин тому

      Kodi mukufuna kuti uza kuti mcp nde ndiyomwe ili ndiphamvu kuposa ife a malawi

    • @WisikiBlack-gj4gu
      @WisikiBlack-gj4gu 6 годин тому

      Pakufunika ma dhemo apapa because mcp ikutionatu kupusa

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 3 години тому

    Mai anabel bambo wake anali wankhanza nayenso walozera zomwezo