MPAKA ZAFIKA APA?? VP MICHAEL USI LERO WALANKHULA MOSASYATILA KU LILONGWE - KWACHEMA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 7

  • @DaimanAbwanja-h8h
    @DaimanAbwanja-h8h 4 дні тому

    Takumvani bwanawe, koma monga ngati ine mmodzi oyikonda MCP.ndikuti inu VP KOmanso adzanu achakwera ndi amene mukupyatsula dziko lino mudzimvere chisoni ngati mmapemphera

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 4 дні тому

    Zanu zimenezo makape inu aliyese amafuna Ndalama ntchito zimenezo muziwe usi ndi nthawi yake zikumuyendela amene zikumunyasa panyini pa make panyapano nose odana ndi usi

  • @EliousImedi-h5p
    @EliousImedi-h5p 4 дні тому

    Ine ndiye ndingonena kut mulibe mzeru ndi achakwera anuo

  • @DaimanAbwanja-h8h
    @DaimanAbwanja-h8h 4 дні тому

    Mau okomera anthu aganyu omwe satha kuganiza kumangokuwa ngati mulankhula zoona. Kodi ndiye manifesto anu muziti chani powanamiza awa osalirawa si ine oganiza ndikulikonda dziko chifukwa sindiyiwala,mukhoza litigation?

  • @dalitsokaelama360
    @dalitsokaelama360 4 дні тому

    ine maona ngati awa ndanzeru koma mmmmm

  • @DaimanAbwanja-h8h
    @DaimanAbwanja-h8h 4 дні тому

    Ndiye musayipise mbili ya anzanu koma mudziwe ichi mwayipisa MCP ndinuyo basi,kodi nanga mukuona ngati ife dzitsilu? (1)fetereza wa MK,4000 ali kuti?kodi tikudwa katatu?achinyamata 1000 000 alembedwadi Natchitoches? Tiuzeni zoona Ndiye mukudana ndimau akuti 2025 boma?sakusiyani mwakumana nazo ayise

  • @tmatabwa-z2b
    @tmatabwa-z2b 3 дні тому

    Very stupid : playing hide and seek