Ken Msonda - May 28, 2023

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 сер 2024
  • Ken Msonda speaking on May 28th, 2023
    A Ken Msonda Kuyankhula Pa May 28, 2023
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 15

  • @MitengoFrancis-sp9ox
    @MitengoFrancis-sp9ox Рік тому +1

    Mr msonda
    Mumazichula kuti ndinu munthu wanzeru komaso opemhera kwambiri
    Koma mwafuna kuzionesera kulephera kwanu kapena kuipa ntima kwanu
    Amutholo sanatukwane ai koma Ngati mau amene wayankhula mutholo akukukhuzani inu mungosintha basi
    Chifukwa mwina mumaona Ngati anthu samakuziwani. Kuti ndinu munthu osokoneza kwambiri.
    Inutu mr msonda muli Ngati Hule sakhala Malo amodzi .
    Paja pali mau oti mdima umadana ndi kuunika
    Sinthani akulu .

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Рік тому +1

    Mr chonde zipaseni ulemu ife tufuna adadi palibe chomwe munganene apa

  • @nelsonnyanja178
    @nelsonnyanja178 Рік тому

    Agree with you the Think tank
    Ndopusa akulu aja ati ndi munthu wamulungu koma zimatuluka pakamwa pawo phalala lokhalokha

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Рік тому

    Aaaaaa Mdala iwe ulibedi mzeru iwe ,Yesu ananyozedwa,kutukwanidwa ndie ka Chakwela ndindani kuti iyeyo asatukwanidwe?????

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 7 місяців тому

    Nkhope kunyasa ngat maliro agozi

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Рік тому

    Ken muliso chisilu ukuyambandala game changer

  • @user-df7yx8fw3v
    @user-df7yx8fw3v Рік тому +1

    Inuso ngati ali ma ARV mwatikwana mwanvaa?😂

  • @daltonjafali3856
    @daltonjafali3856 Рік тому

    Ken Msonda mbuzi ya munthu

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому

    Kodi iwe ukulankhula zichani apa
    Dausi 2
    Mdala wadyera iwe Kodi sunali wa PP iwe
    Ukuti sunayendepo kupita kunja kwa ziko , ndizoona uzikataniko ngati uli ndiphindu kumayikoko mdala osusuka iwe
    Game changer ndi dolotu

  • @CalistoRichard-it8ot
    @CalistoRichard-it8ot 8 місяців тому

    Musakambe za Ena ai kamban zanu ok

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Рік тому

    Ooooohhh ndie kupentako inuyo mukuona ngati sintchito????inuyo ndie mukupanga chani pakuti mwakalamba kale..

  • @felixntaika6201
    @felixntaika6201 Рік тому

    Iwe taziveleko chison even mawu anathaso galu iwe

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 Рік тому

    Umamuyamba dala akayankha walakwa wadyera iwe

  • @enerstmwitha392
    @enerstmwitha392 Рік тому

    Atsilu inu timwani ma RV

  • @user-qh5jo5qh3b
    @user-qh5jo5qh3b Рік тому

    Ukuputa Game changer
    Eish! Wayamba yolakwika sungaimalidze 👹
    Ndipo what u have to know ndiwe Nkhalamba yomvesa chisoni so take care alot😳😳