Usauver S06 Intro Matope
Вставка
- Опубліковано 30 вер 2024
- USAUVER SEASON 6 INTRO
ENJOY
DON'T FORGET TO SUBSCRIBE TO THE CHANNEL
Watch My Other Videos 👇
• Playlist
#Langwani #Piksy #Asauver #Sangie #Music #Malawi #Comedy #Africa #Afro
Subscribe To My Channel 👇
/ @usauver_official
Watch My Play Usova👇👇🔥
• Playlist
#Langwana #Piksy #Usova #Music #Malawi #Comedy #Africa #Afro
PLEASE NOTE: Unauthorized upload of this video unto any UA-cam channel is prohibited. (C) 2022. #CCNB.
Bolako that takes malawian setting,,, sikuti nthawi nzonse nkazi azingoopedwa ai. 2mins ina yake akuchimuna amazayaka Moto. Mabwera😅💪
Patilisha zamuvuta,yes..
Koma watchena😂...
Nice work guys, we waiting for more
We don't like waiting tili kuno Ngozo
Mpaka tabwela kutola mtedza? Muli ndi mwano bwana Piksy kkkkkk
Lilangwe amolosoni mupezeka mwakhota kalomwe bodertu mozambique,tabwererani
Kafupika Ngozoo😂😂
Eeeee mwabwera angozo next week young k and nepman asazalepheremonso 🔥🔥🔥❤️
Patilisha zamuvautaa🤣🤣🤣
In Love with the graphics and angles, feeling sorry for patricia lol
Koma aMorson 🤣🤣🤣. Afika kale ku LL ko basi asauova💥🔥
Anyamata mukuyesetsa kuphuzitsa 😅😅😅😅😅😅😅🎉😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉😢😮😮😮😮😊😅😮
Ngozo kafupika kaya 😂🔥🔥🔥🔥
Tabwela kutola mtedza🤣🤣🤣🤣
Ati kutola ntedza😂😂😂😂😂
Hahaha koma umu muli complicated sangie alibe malo😂😂😂😂
♨♨♨❤
mwayamba ndi fireeeeeeeee. so far worth the wait, nde mwat kutola mtedza kutola mtedza mpaka, angozo simukupanga zabwinotuuu kkkk
Kkkkk Ngozo zanu zama slang munthu ali pa Linthipe pano 🤣🤣
Kkkkkkkkkk
Though bwana 🤣🤣🤣🤣
Aaaa too short 😂😂😂
😂😂😂😂 amangoyenera komabwezad moto kkk
Cool!
Kkkkk komatu mavuto kuvesesa ndikuva ndikosiyana
Ati tabwela kutola mtedza😂😂😂
more fire
Alamwanu eeh duwatu. Ganizani
Mmakwana 💪💪
Molson samamva😂😂😂😂
🤣😂🤣😂🤣🔥🔥🔥🔥
Koma kandiwaza😂😂
Yavuta ndi attention. Nice work guys 👏👏
😂😂
Too short abale
Kwavuta kkkkkkk
Lastly, and I thought Patricia ndi gangster oti Ali stable koma aah didn't know she could be hurt from being ignored 🤣😂🤣
Kkk! Koma apa nde Pat wakumana nazo. Nobody is sympathising with her, not even me LOL
Koma chomwe chikundiwa ndichokuti, Ngozo nde anayamba kubwezadi Moto eeeh😂😂🙌
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Iiiii iiii 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ngozo was like "tabwera kutola mtedza"? 😂😂😂
Aah ndi ineo ndikhoza kumapita kwathu tu nanga wina aliyese angopanga ignore 😂😂😂
Kkkkkkkkkkkkkkk sangie mukumuonjezatu tabwela kutola mtedza hahaha mumakwana inuyo
Iyidi inali ya matope😂
Sangie ndiye aliyense sakukufunatu pamuzipano ingosamukanipo kkkkk
🤣🤣🤣 Patricia yako ija
Mwatitola2 ngat mtedza komweko basi
Tikutole ndiwe mtedza 😂😂
Aaaaa mbambande
Nankaliza
This family palibeso🤣🤣🤣
Kkkkkkk mwabwera guys, 😂😂😂😂
Iiiiihhh Tachoka ndili pa Phone😂
Kkkkkk Km kutora tedza pakana
It's the hiiiiiiii tachoka Kaye ndili pa phone for me🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 me tooo
Too short aaah tadikila time yayitali
Angozo mpaseni attention nkazi kkkkkk
Am very happy to see you back guys😅
Koma nde kakafupi
Sangie amatha ❤
Fayaaaa
Munthu wankulu Piksy
😂😂😂a Molosoni nawo
Pikise ndiwe dolo
Timati piksy