Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Umakwana Selina uli super. Love you so much dear seli
Nkuluyu Bima mandizunguza mutu ine❤❤❤❤kkkk
Ali mmimba mwa mayake wabwelela😂😂😂😂😫🙌
Koma Tadala mpaka ali mmimba mwamayi ache 😂😂😂😂😂😂 kip fire berning guyz❤❤❤❤
Nayeso amandiwaza
Ambuye mundigayile mtima Gati wa Selina , mumandivetsa kukoma
Nzang sellinour mmmmmh kudzibisa et zachab et mpak kuvaliran panti ndi Bhima kkkkkkkkk
😂😂😂 Koma Tadara kuyankha kwa bwanji uko ati ali m, mimba mwa amayi ake wabwerera
Be honest l love this comedy koma simayivesesa or kuyisatila bho bho ma episode pomwe mwasiyila khan Ina muyambila Pena why l would like to know
Mwano uli mwa tadala😂😂😂
Bhima & Selina more fire! Each one of the entire actors are excellent in their lines. I love this comedy. Koma Selina ali ndi speed 😅😅😅! How she chases these MG2's is amazing❤ keep up.
M'makwana guys
❤
Bhima your number one ndipo zikanakhala kuti umachita zimenezi ai ndibwenzi uli player wake Ronaldo
It's Bhima's "beib" tone for me 🤣🤣🤣. The whole crew is just great and singularly, Selina amatha.
Sellina ndi one ,,,,mumakwanira guys keep it up🔥🔥🔥🔥
Selina you are number one keep it up sellina more 🔥🔥🔥
This crew is just amazing,,, keep it up 🔥🔥🔥🔥
Koma Selina iweyo uli bho ukupanga zithu modekha bhima ukhale osamala😂
Komatu phada wa selinayu I can't able mweee
N za malove is keeping us happy mwava
Umatha selina akazi akanati azipanga chochi bwezi amuna akugwidwa komaso ndiwe opangisa mamuna kuzimangirila iya koma muli bho
Best actor Selina dumbula part yomwe unatenga iweyo mmmmm I like it 😍😍😍
Km a tadala mwaunyatu mwano 😅😅😅😅😅😅😅
ikubwela bho🤣🤣though am commeneting before watching
Mumatimvesa kukoma ndi Dziko latu lanjalali😂
Ati wabwerela mmimba mwa mayeke😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Tadala.... Lol
Selina mpaka muram kumulowetsa kuchipinda Ali mkaz mzako😂😂😂😂😂
Kom selina ndi one zimenezo palibe angakwanitse
Ndpo Sellina aaaa ukupengadi fukwa sizoonatu😅
Selina ipase 🔥🔥🔥🔥😂
Cheating imadzuza Bhima uziona😅😅😅😅
Koma sellina iweyo ukumandiphunzitsa kuuleza mtima chan
Celina iweyo ayi thanks ndithu.kkkkkkkk
Sellina ndiolimba mtima
Drammer yi imasangalatsa koma mumayifupikitsa. Izithako or 25 minutes mbwenyeko
mkazi wa bhima amatha kupanga pretending 😂
Ka series aka mukuphika
Hahaha ati ndikajambula ndikutumizila😂😂
Selina iweyo simunthu wamba mbambande
😂Sellina km sutibaya ndi mpen kkkkk
Selina aakulingalira patali😂😂😂bhima samala ohooo , it's mulamu for me and the smile yomupatsa mulamuyo a Hanna akungoti mulamu koma uyuuu🤣🤣🤣
Kmatu Selina,ukundipweteketsa munthu zomachezetsa mkazi zamkozo,kkkkkkkkkkk eeeeeh can't wait for that day yomwe zizaziwike Kuti Bhima ndimamuna wako,,,,,oooh 😅
Welcome selina
Koma selina 😂😂😂😂
Guys i am not following you and can't miss any of your videos 😁😁😁😁😁😁
Koma Selina iweyo ndiwe olimba mtima aise Respect.................😊
Nice one guys
nyc guys
Selina ndiwe 1 ase. Atapezeka azikazi ngati iwe 10 mmmmmm sindikuziwa kuti amunafe tinamapange zozelezekazo. Kmso mkazi ameneyo akumudwa akachiziwa chilungamo chake kuti ndiwe mayi mkulu 😂😂😂😂😂 waiting for another one
Muphana ndi mulamu anuwo
More 🔥🔥
Ambuye mundipatse mtima ngati wa sellina😂❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkk guys ndinu moto❤❤❤❤❤
Koma Sellina. Walodzedwadi.
🙌🙌🥳😊
Koma kuchema week ya mawa
munthu kuonera ngati isathe
Selina 🔥✊✊🔥✊
Muonjezelle nthawi koma gyz
These guys got talent but Selina ndi m😅re
Selina😂😂
Episod yafupika anthuinu mmmm zuchita kubeba mesa😂😂
Odii nkhale mkazi opilira ngt sellina
😂😂😂😂😂😂😂
Koma mukanatigaira mkazi mmodziyo chifukwa akuchulukirani
Patakhala akaz okwana only 10 the whole Malawi like Selina am sure Malawi atha kuposa America in 2 weeks
Sellina atha kupha munthu😂😂😂
😂😂😂😂😂bhima wakumana nazo kkkkkkk
Koma tadala kumeneko kuyankha 😂
Selina akulodzaaa iweee😂
Koma mzitalikisako Selina umakwana abima makan😂😂
Zamalove moto kûti Buuu
Kkkkk wina aziona
komatu Tadala Manda
Obebetsa ka sewero kameneka nde ndi atatu okha umu 😂😂 1. Selina2. Bhima3. Tadala ( The tom boy)
All of them they are very good
Mwayambapo mmmmmm sobwino
Kwashema😂
Hanna 🤣🤣🤣🤣
Selina ndiwapaise 😊
Kkkkkkk koma Tadala Manda
Zilinga bwino
selina akupepetula
kkkkkkkk
uku kuvuta
😁😁😁😁😁 km tadala
Ineyo kukhala Selina yu.. nkhoza kuiwala Kut it's acting nkumukuntha nkaz nzangayo ndithu😰🙄
mumakwana guys
Kma selina amakwan
koma selina umakwana
Selina iweyo ayi zikomo
😂😂😂
koma selina palibe mnzako
Koma Selina umakwana ine masewela amenewo singalonge😂😂😂😂😂😂
Umakwana Selina uli super. Love you so much dear seli
Nkuluyu Bima mandizunguza mutu ine❤❤❤❤kkkk
Ali mmimba mwa mayake wabwelela😂😂😂😂😫🙌
Koma Tadala mpaka ali mmimba mwamayi ache 😂😂😂😂😂😂 kip fire berning guyz❤❤❤❤
Nayeso amandiwaza
Ambuye mundigayile mtima Gati wa Selina , mumandivetsa kukoma
Nzang sellinour mmmmmh kudzibisa et zachab et mpak kuvaliran panti ndi Bhima kkkkkkkkk
😂😂😂 Koma Tadara kuyankha kwa bwanji uko ati ali m, mimba mwa amayi ake wabwerera
Be honest l love this comedy koma simayivesesa or kuyisatila bho bho ma episode pomwe mwasiyila khan Ina muyambila Pena why l would like to know
Mwano uli mwa tadala😂😂😂
Bhima & Selina more fire! Each one of the entire actors are excellent in their lines. I love this comedy. Koma Selina ali ndi speed 😅😅😅! How she chases these MG2's is amazing❤ keep up.
M'makwana guys
❤
Bhima your number one ndipo zikanakhala kuti umachita zimenezi ai ndibwenzi uli player wake Ronaldo
It's Bhima's "beib" tone for me 🤣🤣🤣.
The whole crew is just great and singularly, Selina amatha.
Sellina ndi one ,,,,mumakwanira guys keep it up🔥🔥🔥🔥
Selina you are number one keep it up sellina more 🔥🔥🔥
This crew is just amazing,,, keep it up 🔥🔥🔥🔥
Koma Selina iweyo uli bho ukupanga zithu modekha bhima ukhale osamala😂
Komatu phada wa selinayu I can't able mweee
N za malove is keeping us happy mwava
Umatha selina akazi akanati azipanga chochi bwezi amuna akugwidwa komaso ndiwe opangisa mamuna kuzimangirila iya koma muli bho
Best actor Selina dumbula part yomwe unatenga iweyo mmmmm I like it 😍😍😍
Km a tadala mwaunyatu mwano 😅😅😅😅😅😅😅
ikubwela bho🤣🤣though am commeneting before watching
Mumatimvesa kukoma ndi Dziko latu lanjalali😂
Ati wabwerela mmimba mwa mayeke😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Tadala.... Lol
Selina mpaka muram kumulowetsa kuchipinda Ali mkaz mzako😂😂😂😂😂
Kom selina ndi one zimenezo palibe angakwanitse
Ndpo Sellina aaaa ukupengadi fukwa sizoonatu😅
Selina ipase 🔥🔥🔥🔥😂
Cheating imadzuza Bhima uziona😅😅😅😅
Koma sellina iweyo ukumandiphunzitsa kuuleza mtima chan
Celina iweyo ayi thanks ndithu.kkkkkkkk
Sellina ndiolimba mtima
Drammer yi imasangalatsa koma mumayifupikitsa. Izithako or 25 minutes mbwenyeko
mkazi wa bhima amatha kupanga pretending 😂
Ka series aka mukuphika
Hahaha ati ndikajambula ndikutumizila😂😂
Selina iweyo simunthu wamba mbambande
😂Sellina km sutibaya ndi mpen kkkkk
Selina aakulingalira patali😂😂😂bhima samala ohooo , it's mulamu for me and the smile yomupatsa mulamuyo a Hanna akungoti mulamu koma uyuuu🤣🤣🤣
Kmatu Selina,ukundipweteketsa munthu zomachezetsa mkazi zamkozo,kkkkkkkkkkk eeeeeh can't wait for that day yomwe zizaziwike Kuti Bhima ndimamuna wako,,,,,oooh 😅
Welcome selina
Koma selina 😂😂😂😂
Guys i am not following you and can't miss any of your videos 😁😁😁😁😁😁
Koma Selina iweyo ndiwe olimba mtima aise Respect.................😊
Nice one guys
nyc guys
Selina ndiwe 1 ase. Atapezeka azikazi ngati iwe 10 mmmmmm sindikuziwa kuti amunafe tinamapange zozelezekazo. Kmso mkazi ameneyo akumudwa akachiziwa chilungamo chake kuti ndiwe mayi mkulu 😂😂😂😂😂 waiting for another one
Muphana ndi mulamu anuwo
More 🔥🔥
Ambuye mundipatse mtima ngati wa sellina😂❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkk guys ndinu moto❤❤❤❤❤
Koma Sellina. Walodzedwadi.
🙌🙌🥳😊
Koma kuchema week ya mawa
munthu kuonera ngati isathe
Selina 🔥✊✊🔥✊
Muonjezelle nthawi koma gyz
These guys got talent but Selina ndi m😅re
Selina😂😂
Episod yafupika anthuinu mmmm zuchita kubeba mesa😂😂
Odii nkhale mkazi opilira ngt sellina
😂😂😂😂😂😂😂
Koma mukanatigaira mkazi mmodziyo chifukwa akuchulukirani
Patakhala akaz okwana only 10 the whole Malawi like Selina am sure Malawi atha kuposa America in 2 weeks
Sellina atha kupha munthu😂😂😂
😂😂😂😂😂bhima wakumana nazo kkkkkkk
Koma tadala kumeneko kuyankha 😂
Selina akulodzaaa iweee😂
Koma mzitalikisako Selina umakwana abima makan😂😂
Zamalove moto kûti Buuu
Kkkkk wina aziona
komatu Tadala Manda
Obebetsa ka sewero kameneka nde ndi atatu okha umu 😂😂
1. Selina
2. Bhima
3. Tadala ( The tom boy)