The Confession of Charles Ben Longwe (Part 1)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 29 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, former government critic Charles Ben Longwe, would like to make a confession. Let us tune in and listen together to what he has to say.
    Pa Nyasa VoiceBox, yemwe anali wotsutsa boma Charles Ben Longwe, akufuna kulapa. Tiyeni timvetsere limodzi zomwe akunena.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 70

  • @JeanGamah
    @JeanGamah 4 місяці тому +5

    do not mention the name of God in vain, better continue with your wayward business than take God and put Him in the business of hypocrites

  • @lyiemax
    @lyiemax 4 місяці тому

    Unatinyansa kale iwe kape, tinakutsika ife

  • @AndyMalikebu-pi7up
    @AndyMalikebu-pi7up 4 місяці тому +1

    Usatchule pachabe dzina la Ambuye Mulungu wako!

  • @JaffahSibuh-s1f
    @JaffahSibuh-s1f 4 місяці тому +1

    Wakuba uyu chisilu chachabe chabe longwe ndi tonse akuba

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 4 місяці тому +1

    Machende ako Ben Longwe anthu anakusika ngakhalenso Redson Munlo anakusika coz anakuona Kuti ndiwe Chisiru chamunthu

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 3 місяці тому

    Ben longwe ndiwe mbuz

  • @SamsonKunthani
    @SamsonKunthani 4 місяці тому

    BKodi chitsiru iwe ukuti chani mmphawi iwe? Unanalonjedzanso kuti usiya zolankhula za ndale.Lero ukuti chani?Akupatsa zingati galu iwe.?

  • @DavieLosani
    @DavieLosani 4 місяці тому

    Anthu ngati inuyo openphelanu mwahinyengo ngati inuyo ndamene mwaononga dziko,musavutike a bwana,, vote sidzasinthapo vote ndiyomweyija,kalimeni basi zinakuvutani, vinyo wakuthelani,a mcp ndiomwe aja komaso a dpp ndiomwe aja musamazinamize.

  • @Qiraa.m
    @Qiraa.m 4 місяці тому

    Uyu wayamba liti kulungama uyu chitsilu chachabe ichi

  • @GiboTakondwa
    @GiboTakondwa 4 місяці тому

    Wapenga misala ndizokoka zamayi yolamu utulusenso oudio yoti wasiya pano kukoka zokoka zamayi yolamu bwanawe iwetu wasungidwa pakona Koma sukudziwa samala

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 4 місяці тому +1

    Galu iwe tseka pakamwa ..tinakutuluka Kare kare mbanva bwera kuno udzarape course unathawa utaononga mzako ndi chakwera aneneri onyenga ..ukutithera data kagwere uko

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 4 місяці тому

    Ndiwe mbuzi kwambili ben mcp ndichotcho

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 4 місяці тому

    Iimbika kulankhula .. ngakhare part 2 uziphatikiza ziziveka zonse pakamodzi umpose ryiton iwe ulandire zambili

  • @Maxwell-e2d
    @Maxwell-e2d 4 місяці тому

    Ben machende ako

  • @Nyodzani123Jmlingz12
    @Nyodzani123Jmlingz12 3 місяці тому

    Amayi ako anafela ku bhala akunyengedwa dog style galu iwe

  • @mrsmoseskita9180
    @mrsmoseskita9180 4 місяці тому +2

    Mbuzi ya munthu galu ben longwe namachende weniweni komanso tinakutuluka kale kale mbava unaba galimoto ungati unzechani galu iwe patumbo

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 4 місяці тому +3

    . Mai yolamu mwamusiya kodi ben longwe anakutukwanani munaiwala

  • @BatsonChitseko
    @BatsonChitseko 4 місяці тому

    Umphawi komanso njala zimatha kumupanga munthu wamphamvu zake komanso nzeru kukhala chitsilu. Chitsanzo chabwino ndi Ben Longwe. Munthuyu wamukwapula ndi umphawi.

  • @EsterNyasulu
    @EsterNyasulu 4 місяці тому

    Ngati ukufuna kuti tidziverako ma audio Ako please stay away from this evil fortune seekers an opportunist who so called Ben Longwe.

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 4 місяці тому

    Kodi inuyo bwana DC akulilongwe mukungomuyang'ana galu ameneyu mene anakutukwanilani muja kukuyalutsani za kumaliseche pa air. Koma inuyo muli phee osamutengela ku khothi galu ameneyu bwanji.

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 4 місяці тому

    Suka Man,wena sikabengo wena,skeremu woba magalimoto ku Joni wathawa kuotchedwa akanakuveka nekilesi chimbava choka

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 3 місяці тому

    Ndiposo machende ako don't think we're stupid mesa Uli Kwa chakwela mbuz iwe

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 4 місяці тому

    😂😂😂pamusana pako iwe ine sindingakuveleko uphawi wakutaka ku Joni uko ndiye ubwere kuno uzatinamize pano galu iwe

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 4 місяці тому

    Kkkkkkk iweyo kuyankhulako wachimwa kale kuyankhulila boma kudzela mu BIBLE mutembedwa nazo

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 4 місяці тому

    Makape unkawanyoza aja akurandila 😢 naweso nd kape otheratu and uzingodya nao don't mention name of God coz Ur evil

  • @EsterNyasulu
    @EsterNyasulu 4 місяці тому

    Mai Yolamu mwamuyiwala galu uyu wotukwana uyu ndiku kumbutseni amati akoka zithu ndikutheka nthawi ija ndi imeneyi akufuna apange dzake zija.

  • @MahuwadrillingGroup
    @MahuwadrillingGroup 4 місяці тому

    Pitani ku assembles of God mukakhale m'busa mbuyakoyo akakulandila koma kukamba za mzikozi ndie utichimwisa

  • @emmanuelmtayisi
    @emmanuelmtayisi 4 місяці тому +1

    Choka iwe chimbava

  • @MajotiMpandasoni
    @MajotiMpandasoni 4 місяці тому

    Zimenezo bwana longwe wauzeni anthu okusatilani zomveka koma zomatipusisazo mulungu muzamuziwa

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 4 місяці тому

    Apa bwalo sakuchoka unkanenatu paja ukutukwana chakwera mayi yolamu paja ku Jon wapalamulako ayi limbikira akupatsa zambiri

  • @GiftMangwalala-d2b
    @GiftMangwalala-d2b 3 місяці тому

    Amwene mmene mmatukwanira muja lero mukuwerenga mawu amulungu mavuto ndithu inu ngati mukalowe inenso sindidzatsara ai

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 4 місяці тому

    Umphawi unawakwana achisiruwa adathawa Ku South Africa chifukwa chakuba galu alibe kanthu

  • @thommgombe7804
    @thommgombe7804 4 місяці тому

    Amwene mwasowa zochita sindimvamo mfundo iliyose umu, mfundoless

  • @thommgombe7804
    @thommgombe7804 4 місяці тому

    Mukalalikire ku church muli ndiluso osati mumapangazi

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 4 місяці тому

    Amphawi odyera pakamwa. Umphawi sizinthu

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 3 місяці тому

    Unatha galu iwe walandila ndalama pamtumbo pako

  • @MichaelMagombo
    @MichaelMagombo 4 місяці тому

    Chitsiru iwe wasowa zochita tsopano fisi iwe

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 3 місяці тому

    Achitsilu a ben logwe achitsilu yino

  • @SamKaposa-i5c
    @SamKaposa-i5c 4 місяці тому

    Umphawi utidziwitsa yesu😂😂😂

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 4 місяці тому

    Unali kale iwe

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 4 місяці тому

    Kutha maplanitu ukuu achitsiruwa

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 3 місяці тому

    Galu kape iwe mnakutuluka

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 4 місяці тому

    Achitsilu inu anthu anakutulukan kale

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 4 місяці тому

    suka mbudzi iwe machende ako

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 4 місяці тому

    Galu iwe

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 3 місяці тому

    Waunsilu iwe gwape

  • @StephanoMussa-q6d
    @StephanoMussa-q6d 4 місяці тому

    Shisilu Cha munthu

  • @HalordMlima
    @HalordMlima 4 місяці тому +1

    Mayi yolamu Ati akusungabe ma,audio ako uku ati usaone ngati ayiwala akungokudikira ufatse kaye

  • @HarrisonKalonga-k7p
    @HarrisonKalonga-k7p 4 місяці тому

    Mbudzi

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 місяці тому

    Nyero ya munthu

  • @AngelaMosimbwa
    @AngelaMosimbwa 4 місяці тому

    Ben machende ako

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 4 місяці тому

    Palibe chomwe kuyankhula iwe udzafa osauka remember udamangisa anthu utatuma kuti apange ma demo kodi anthu amenaja angamakuone bwanji udzafela mmanja mwawanthu galu iwe ungobwera konkuno uzizagwililira ana ako aja 😂😂😂😂

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 4 місяці тому

    Zazii

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi 4 місяці тому

    Inuyo mwayamba kutumiza za wusiru sopano

  • @BillyKalambo-jx3vf
    @BillyKalambo-jx3vf 4 місяці тому

    Kape Ben Longwe ukuuza ndani nyatsi zakozo

  • @TadalaPaul-dk6xi
    @TadalaPaul-dk6xi 4 місяці тому

    mwana opusa

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 4 місяці тому

    A ben longwe mukufuna mutathaudze kuti chani chisiru iwe amalawi anakusiyatu usalimbane ndi amalawi okuba galimoto iwe akupasa ndalama ndiye osamangodya achisiru

  • @violetmahachi7673
    @violetmahachi7673 4 місяці тому

    Achisiru inu

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira 4 місяці тому

    Kusintha kwanu kwapangitsa dzoyankhula dzanu kukhala dzongoseleura chifukwa simukhadzikika pa idzo

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 4 місяці тому

    Mumuuze Beni longwe asatinyanse ndipo mukutaya nthawi yanu pa Nyasa Voice

  • @louisgolden
    @louisgolden 4 місяці тому

    Inu simungawasinthe anthu zomwe amanga ndizomwezo mbuzi

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 4 місяці тому

    Eeeee tinakutulukani man kkkkk

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 4 місяці тому

    Choka iwe mukusokosa

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 4 місяці тому

    Ukuona ngati akukhululikira uziona ndi anthu ake mbale

  • @SusanHara-l1t
    @SusanHara-l1t 4 місяці тому

    Kkkkk😂😅 .......!!!!!

  • @francis12fombe54
    @francis12fombe54 4 місяці тому +1

    Mukuchedwa kutulusa bwana ben

  • @eliasMwamba-q5f
    @eliasMwamba-q5f 4 місяці тому

    Kodi ukulapa kapena ukutiuza chiyani?