ZOOPSATU! KODI ZOSOWETSANAZI NDE ZITI? CHIMWENDO BANDA WADODOMETSA ANTHU.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 195

  • @AlexanderBaluti
    @AlexanderBaluti 9 днів тому +3

    If anything happen to APM....chimwendo ....

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 6 днів тому +3

    Boma ndilomweli koma tingositha sogoleli basi chakwera anango zaza mamina mutu😂

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 9 днів тому +2

    Dziko lomvesa chisoni kwambiri. Zoona munthu wanzeru anganene kuti boma ndilomweli kulephera kwake kumeneku? Ndinu amphawidi ndithu.

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 3 дні тому +1

    Boma ndilomweli Boma ndilomweri anamupakulira beans zake zomwetu Dan Lu

  • @chimzymhashieroo4180
    @chimzymhashieroo4180 4 дні тому +1

    Chimwendo banda mutu ngati water melon Boma lomweli yakudowa kwanuko ife sitingavotele chakwera

  • @GeraldMukhuna
    @GeraldMukhuna 9 днів тому +2

    Kodi uyu ndiuja anathamangisidwa pamodzi ndi amake chifukwa cha Ufiti kkkk

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa 6 днів тому +1

    We will change a president only but boma ndilomweli

  • @PaulChibakuwa
    @PaulChibakuwa 8 днів тому +1

    Fearing Peter wa Mutharika. These guys are kawards.

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso 9 днів тому +2

    Anthu akudana ndi DPP basi koma chimwendo iweyo uzaziwona siku Lina iweyo siku Lina iwe ndinthudi

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl 9 днів тому +1

    Kod peter anamulakwira chan chimwendo ? Uyu ndi fiti ndi2 mbambadi nd2 dpp okiwaopsyadi nd2

  • @StanleyMunthali-s1d
    @StanleyMunthali-s1d 9 днів тому

    Si ndiye ! Akufunika Deliverance for him to come to his senses !

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 9 днів тому

    APM has along life, God is with APM

  • @NumeriChibowa
    @NumeriChibowa 7 днів тому +1

    Awa akuzinamiza kwambri mene Malawi wavutira akufunika ndi Peter bas osat akanganya osakaza zinthu bomawa
    Bon kalindo wakhala akunena kuti anangowona kuimbira manja fiti Bolaso Peter chisazo Achina mtambo anavutika pomeneyera ufulu boma limeneri lero akuti bwanji??
    Onse amene anayenda nawo akutuluka kuipidwa ndimomwe dziko likuyendera ndye wina ndi mkamwa mwake monunkha nkumati boma ndilomweri very shameful

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 8 днів тому +2

    Zopusa zaziiiii anthu osasamba agalu inu

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 5 днів тому +1

    Iwe ngalu kwambili chikangawa group

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 днів тому +1

    Achewa kupepelesedwa koma ndizoona zinthu zilili mmalawi muno wina aziti Boma ndilomweli ......achewa kuyimbila mfiti mmanja ....anthu awa ndi akuba koopsa

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 7 днів тому +1

    Kodi ukasutatu zonse umaona zabwino,nanga pali nzeru kuvoteranso zimenez

  • @JeffatNzeru
    @JeffatNzeru 8 днів тому +1

    That's why umamupopa kt nakhumwa kt peter asaima umazwa kt sumuima😂 apm woyeee

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 2 дні тому

    Ukunoma iwe my vote Dppp

  • @AbdulTepelunda
    @AbdulTepelunda 9 днів тому +1

    Kusowa zochita uku ndithu munthu wabwino bwino mkuvala sanza eshiiiii ndipo gulu ili ndiloti lija olo zinthu zikuvuta ati zilibwino

  • @MaxwellChabwera-y7x
    @MaxwellChabwera-y7x 9 днів тому +1

    Ndinu zitsiru kwambiri agalu anyani kwambiri ndi masapota anuwo ,chosecho anthu anuwo Alibe chakudya

  • @MaulanaIriyasa
    @MaulanaIriyasa 9 днів тому +1

    Mbuzi ya mun thu iwe chimwendo. Mutu ngati mango opondedwa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 днів тому +1

    My vote is for Dpp under Apm osati chisilu chilipochi chaononga ziko ......fuel kulibe ....njala ndi iyi....kukwela Kwa katundu tsiku ndi tsiku .....amalawi zoona kuyimbili mfiti mmanji

  • @AgrementShadreck
    @AgrementShadreck 9 днів тому +2

    Pepani akulu akulu koma sitose ochewa oyipa please tidikira 2025 on 16 st

  • @BeatriceSaulosi
    @BeatriceSaulosi 8 днів тому +1

    Kkkkk koma athu ena ndi ovetsa chisoni kwambiri 😢

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 8 днів тому

    Yes chikangawa azowa popani 2025 Apm is coming soon to be president of this country forget about chikangawa again dpp is my vote 🗳 😀 👍 😉

  • @TrasizioMlupwa
    @TrasizioMlupwa 8 днів тому +1

    Chimwendo amamuopa peter mutharika heavy 😂

  • @JamesSaiti-h1l
    @JamesSaiti-h1l 9 днів тому +1

    Mbuzi zikuyimba nyimbozo feteliza akugura bwanji 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @Kelvinbanda-c3x
    @Kelvinbanda-c3x 9 днів тому +1

    Ine ndichewa koma tisamanamizane kuti tose ndife aMCP

  • @kennymwanyongo8165
    @kennymwanyongo8165 5 днів тому

    Kusowa nfundo nditu...
    Nanga tinganene china chiti...?
    Munthu wanzelu zake sangamalankhule chonchi!!!

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 8 днів тому +1

    ACHIMWENDO MWAUZA DZIKO KUTI MUSOWETSA PETER MUTHALIKA MUKANA OLO MUVORA NDINU MUNAPHADI CHILIMA ZITSILU ZAWATHU

  • @patricksamson4852
    @patricksamson4852 9 днів тому +1

    Achimwendo akula ndi mantha mdala uja akukusegulisani mmimba masiku amathera kuchitseko mutu umenewo uzaonda ngati mafulufute within 2 weeks

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 9 днів тому +1

    Asowe ndi chimwendoyo osati adad.

  • @charlesmuwanya7845
    @charlesmuwanya7845 9 днів тому

    Obviously the last kicks of a dying horse. The aftermath of promises & lies.

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 9 днів тому

    Ndale za ku malawi zopusa kom ngat kuwina zitheka bwanji mcp kuwina after zaka 30 position guy's palibe asowe ndalezaoyimba tiona 2025 kumavoti basssss😮😮😮😮

  • @McfordKaunda
    @McfordKaunda 7 днів тому

    Kkk Peter Ali ndivuto lanji chimwendo iwe ndiomvesa chison kuyamba nyimbo ya ambuye mmkumaphatikiza ndi mau ogawa ziko

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 днів тому +1

    Mbuli zambili mmalawi muno zili ku Dowa .....anthu anakagonabe nyumba za mauzu
    ..
    Mbuli zenizeni angopusosidwa chifukwa palibe chomwe akuziwa

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 9 днів тому +2

    Ndipo peter simungamuphe agalu inu

    • @DoreenGwedeza
      @DoreenGwedeza 9 днів тому

      Zaoneka kut .mcp ili ndimantha ndi Dpp zipan zotsutsa zambiri koma wasankha Dpp dyerat mawa uzalira boma tikusintha mwatizuza pakwana

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 днів тому +1

    Richard chimwendo sago a tulo ndi Apm

  • @AdamMwamadi-p2j
    @AdamMwamadi-p2j 9 днів тому +1

    Boma ndilomweli koma president tisintha inu a mcp Mulungu akukanthani kwambiri ndipo Peter mukulimbana nayeyu mudzakhumudwa ali pampando chipani chamwazi ngati chimenechi mmmm shame on you chimwendo

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr 9 днів тому

    These are the poorest people
    And they don't know those politicians are using them shame on you, chimwendo

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 9 днів тому

    Kusewera ndi Mulungu, Mulungu angasekerere iziiii, ozimuka inuyoooo😢

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 9 днів тому

    Izi ndiye mbuli zenizeni izi ....pamene alipo amagona nyumba za mauzu .....central region imeneyo

  • @EmmanuelGodfreynkhoma
    @EmmanuelGodfreynkhoma 9 днів тому +2

    Ine ndi mchewa wankonkuno ku dowa APM my vote achimwendo dziwani mbuzi ikakondwa amalonda ali pafupi ndiye iwe watsala madzi amodzi thawi imakwana

  • @KassimWilson-g6m
    @KassimWilson-g6m 9 днів тому

    😂😂😂😂 zopunya munya chimutucho chimwendo banda kuchikamwa

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 9 днів тому

    ndangopanga open ndikupanga pause kuti ndiwuze chamutu ngati khobwecho tikumangani pompano, mumandiseketsa kusewera ndidabwe😂zinyawu zaziwakulakhura vilombo

  • @JamesDismael-z4y
    @JamesDismael-z4y 5 днів тому

    Zitsiru zakupha izi koma zathera pa Chilima basi muwaona akusosorana okha mmodzi mmodzi

  • @DannisImkosi-j9r
    @DannisImkosi-j9r 5 днів тому

    Chimwendo asowa osati Big tifela dziko lathu

  • @Ybm-o5y
    @Ybm-o5y 8 днів тому

    Mukhaula ine vote yanga sindingakupaseni inu mwaononga dzikoli,,,munya muona kwanu kwatha,,APM MY VOTE 2025

  • @AminJumah-s9t
    @AminJumah-s9t 7 днів тому +1

    Kodi kulibe zipani zina kumangolimbana ndi Peter ndi DPP why???????

    • @IanChitsulo
      @IanChitsulo 7 днів тому

      Akudziwa kuti sangamake akuchepa 😂😂😂😂

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 7 днів тому

      Chimozimodz DPP ikulimbana ndi MCP

  • @ZekezekeNjala
    @ZekezekeNjala 9 днів тому +2

    Koma achewa inu ndi zisilu ndithu

  • @raffiklapelafShelif
    @raffiklapelafShelif 9 днів тому

    Ukufuna utsowetse muthalik akukuberatsokoneza mukaura ngat makwara ifetso tilipo tiye kungotsowa muthalika ine ndilipano chakwera atsowa mene angatsowere muthalika 😮

  • @PhilominaAustin
    @PhilominaAustin 7 днів тому +1

    Peter sakusowa utasowe ndiweyo chakwela

  • @KandayaCharles
    @KandayaCharles 9 днів тому +1

    MULUNGU Akulangani inu okupha chilima inuuu!

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 9 днів тому

    Cimwendo ndiwe wankhondo,,ukhaula Siwe Mulungu,,usowa wekha,,anakuputa cani Peter,,Moyo wa peter uli mmanja mwa Mulungu ndipo anawubisa poti iweyo ndi amzako sumungafikire

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 8 днів тому +1

    Kulitu Yehova kumwamba ku

  • @MakawaPartrick
    @MakawaPartrick 8 днів тому +1

    Kodi iwe uzingopha anzako iwe so ubzafa

  • @BilalAliyah-k1f
    @BilalAliyah-k1f 9 днів тому

    Nyimboyo apole moto APM nde chiyembekezo chathu

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 9 днів тому +1

    Chakwela asoweeeeee kukamwa kwake

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 9 днів тому

    Kodi anthu inu muti mukawona zonse zikuchitikazi zikutanthawuza chiyani? Kodi dzikoli liripobe kapena maso anu ndi wotsekeka? Mulungu akuyendeleni musatayike nonse akubwera posachedwapa

  • @KondwaniNedi
    @KondwaniNedi 8 днів тому +1

    Akuluwa chilipo chikuwasata.

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 9 днів тому +1

    Koma amalawi momwe zithu zafikira kumalawi ndikumasapota mcp.uchisiru basi.

  • @KandayaCharles
    @KandayaCharles 9 днів тому

    Azitsogoleli onsewa azipani osawatchula koma Peter mukumuwopa ndi katundu .

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 3 дні тому

    Koma kumeneko kuli chimanga eti anthu akumalawi ndi onvetsa chisoni momwe njala ilili u udzikautika ndi 2 pin zowona ulesi

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 6 днів тому +1

    Kumtumbo kwanu agalu a MCP anthu okupha komanso opanda chisoni zimachende zachakwera kunyini kwa Anabel mtalimanja konunkhako

    • @UniceSauli
      @UniceSauli 4 дні тому

      Kutukwana ngati ako anakubelekera mulumu

    • @AdamAhamad-k2i
      @AdamAhamad-k2i 4 дні тому

      @UniceSauli khala chete hule iwe

    • @MartinKapito
      @MartinKapito 19 годин тому

      Ndi chisiru musiyeni

  • @MuhammadAlie-u5n
    @MuhammadAlie-u5n 9 днів тому +1

    Zisilu izii zopanda manyaizi 😅😅

  • @MaxwellChabwera-y7x
    @MaxwellChabwera-y7x 9 днів тому +1

    Munazolewera kupha anthu inu

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 9 днів тому +1

    Mulungu akhale nafe ndithu

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 3 дні тому

    Olo atasowa koma inu mukufa ndi njala ndi mcp yanuyo anthu aulesi inu kuvala gule nkumapempha basi

  • @KandayaCharles
    @KandayaCharles 9 днів тому +1

    Zikuwonekatu kuti Peter muthalika mukumuwopa zedi .

  • @HawaHussein-d4l
    @HawaHussein-d4l 9 днів тому

    Adziwika okha okha akupha anthu adziulula koma ambye akuona zonsezi adzabweza yekha nkhondo iyi

  • @PhilbertoChaimah-l4p
    @PhilbertoChaimah-l4p 9 днів тому +1

    Ayaluka chimwendo wayamba kuulula yekha

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 9 днів тому

    Anthu sakufuna zophana, kapena kudya chiteze Ayi.Apasen Anthu zosowa zawo Monga mankhwala nzipatala,Kumanga Misewu,Chitetezo chokwanila, komanso Mafuta azipezeka nziko muno. Boma ndilomweli Mukuthandauza zinthu nziko muno zili bwino? Chimanga K50000 boma ndilomweli, Mafuta K4000 per litr Boma ndilomweli Anthu .Chitetezo kulibe Boma ndilomweli. Vomelezan nziko muno zinthu sizilibwino osat Boma ndilomweli Ayi.

  • @SamsonNyadan
    @SamsonNyadan 9 днів тому

    Ngati muzimva kuwina basi chosani smartmatic, imodzi ndi Anabel

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo 7 днів тому

    Kodi siyinu mumanga Ena aja nanga inuyo zachimwendo mupangidwe chani muliwu loti aspwe muthLika

  • @MaxwellKapalamula
    @MaxwellKapalamula 7 днів тому

    Boma ndilomweri, bwanji mukuopa manual vote, mukufuna smart matic kut muzabere vote pamene mukuzwa kut boma ndilomweri 2025.

    • @ebinazielkandomo7803
      @ebinazielkandomo7803 7 днів тому

      Kumaganizo anga ndi akuti, momwe a Chimwendo amafunsira anthu kuti Peter asowe asasowe . DPP isowe isasowe ndi mau adale wokometsa kapena kupsyipsyiritsa. Mauwa ndichimodzimodzi kunena kuti Peter awine asawine DPP iwine isawine. Pandale pamalankhulidwa zinthu zambiri zomwe zipani zimalankhula,zikamapangitsa misonkhano.

    • @McfordKaunda
      @McfordKaunda 7 днів тому

      Ndiye chikwanje amaphiphirisa kt chan ​@@ebinazielkandomo7803

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 9 днів тому

    Mmmm koma mpakana pamenepa? mmmm alibe manyazi a Chimwendo.

  • @apostledavismsosa
    @apostledavismsosa 9 днів тому

    Mwati peter mufuna sowe???? Anakhala wina mutamumangatu apa anthu akupha awa aziulura lero amakana chani chimwendo wakupha uyu

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d 9 днів тому

    Nde mcp yatsanduka dambwetu. Zangokumanako dzitsiru zokhazokha. Basi kumaganiza zachitukuko chopha anthu Basi

  • @DumiMhango
    @DumiMhango 8 днів тому +1

    Asowa ndiyeyo ndamake

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 9 днів тому +1

    Ukugona ndinjala boma lomweri nyamako

  • @BonzoSolomon
    @BonzoSolomon 9 днів тому

    Kodi pa five years imene mwalamulai ndichani chomwe mwatipangila amalawi

  • @georgekamanyuzi108
    @georgekamanyuzi108 9 днів тому

    They can't win next year I bet

  • @MussahCassim-o6u
    @MussahCassim-o6u 9 днів тому +1

    Samba isi kom athuwa amaganiza kom

  • @InessRobart
    @InessRobart 8 днів тому +1

    Utasowe ndi iweyo ndi mcp yakoyo

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 8 днів тому +1

    Ndichifukwa wamkwela nkadzi wa Dan lu

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 9 днів тому

    Ine ndizabwela konko ku malaw ndizaponye moto ku gule wawoko

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 9 днів тому +1

    Kupusa kwabasi,zidyelen zagalu zmez

  • @DavieChiyepa-e5v
    @DavieChiyepa-e5v 8 днів тому

    Anthu amenewo ndi misala imeneyo paja osayiwala muthalika ananena kale kuti anawakhululukila osada nkhawa dzikoli silingabwelelenso Ku one party akunamizana chakwela akuziwa koma sangawauze omusatila ake chifukwa naye akuziwa kuti amasatilidwa ndi zisilu sizimamuuza zofunika ku ntundu wa amalawi

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga 9 днів тому

    Koma.mcp ndichipani gyz mmmm iyi basi singaluze momphweka

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 9 днів тому

    Chimwendo Banda ndi mbuzi yamuthu crocodile team imeneyo onse a mcp ndi mbuzi zasatanic

  • @EsterManiya
    @EsterManiya 9 днів тому

    Kambani fundo zanu zisiyen za dpp hahaha mayazi bwa😊

  • @VeronicaMatiyaBanda
    @VeronicaMatiyaBanda 9 днів тому

    Akuziwa kut 2025 akugwa bas sangawine azathawa awaw nde tione ngat angamangidwe zasiyana chani ndi adaud chikwanje aja

  • @NowahopeChirwa-t1c
    @NowahopeChirwa-t1c 4 дні тому +1

    Tisitha chipani

  • @StephanoKaunda
    @StephanoKaunda 8 днів тому

    Chimwendo akulila😂😂😂😂😂kuwopa apm hhhhh

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 9 днів тому

    Koma za Boma ndiye sitimasinthatu mwina simudziwatu koma zipani ndiye timatsintha please awuzeni anthu za chipani sitisintha wosati Boma kkkkkkkkk Boma ndi Malawi Boma osati chipani Boma kulibe mau ngati amenewa achimwendo Banda

  • @LoyceMhango
    @LoyceMhango 9 днів тому +1

    Kuzolowela kusowesa anthu

  • @LonexKachepa
    @LonexKachepa 9 днів тому

    Mmmmm sakuziwa chimene akuchita alamufuse trump

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 7 днів тому

    Amalawi amnzanga chonde osatenga vote kuwapaza a mcp ndikuphempha izi chifukwa kuli mavuto tikupitaku

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 8 днів тому

    Koma umaliza onse. Chilima munampanga chikangawa mukufunanso musowetse Peter. Nthawi yako yatha utapsotedwe ndi iweyo. Watsala madzi amodzi.