3 Quarters Ya NEC Ya MCP Sikuwafuna A Chakwera - Isaiah Sunganimoyo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 40

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms День тому +2

    Braz am with you and you talking the truth, no way chakwera he failed

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 22 години тому

    Nice speech brotherman

  • @JamesKalasa-s6s
    @JamesKalasa-s6s День тому +2

    MCP chomwe mukufuna simukuchiziwa zikambilanani koma DPP yatenga kale dziko

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi День тому

    Exactly 💯 zoonandi

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula День тому

    Big ndagwirizana nanu koma adzombe vuto lake akumakhalanso kumbuyo Kwa ulamuliro uwu sitinamvepo akudzudzula zoipa zomwe zikuchitikazi even asimbi angokhalanso chete nothing to contribute good voice for beter governors ndiye chomwe mupange musachikakamizire chipanichi pakati pokha onaninso zigawo zinazi chisakhale chipani chamtundu umodzi okha kamuzu sanaike chigawo zindikilani kuti kamuzu adamusiilapo gwanda chakuwamba nsena sanaone mtundu

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu День тому

    Mukuwaopa aChakqera...siziyenda choncho...zakunyumba kwanu izi

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 21 годину тому

    Koma ndikuona kuti si achewa onse amwe amaganiza mopepera alipo ena abwino ndithu chitsanzo ndi ichichi chakwera walephela

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje День тому +1

    Iwe usiyiletu nyasi zakozo MCP NDI mighty party anthu onse MCP simbi phiri NDI adzombe si a MCP ukunama chewa NDI MCP sizikugwilizana

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 5 годин тому

      Muli NDI vuto akulu...Chakwera wakanika kuyendesa chipani komanso dziko icho Nde chilungamo chake,,Tamaganizani bwinobwino inu usogoleri uwu ndi opanda tsogolo,,and chikhara kut MCP ili ngat zipani zinazi bwenz tikuti ndi mathero ake basi kusogoloku

  • @matthewnyozani6596
    @matthewnyozani6596 День тому +1

    It's too late

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani День тому +1

    Ku Nigeria munthu ukapha munthu sakulora kukhal or mfumu ife tinatenga munthu oti anapha m'busa mzake kumpasa usogoleri wadziko lero ndi izi Chakwera anapha m"busa lero ndichfukwa zawakanika chil chonse chamagaz manja chikakhal president

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    iweyo,ukatelo,ukufuna,anthu,adzavotele,ndani, panyapako

  • @FelixMboma-o5v
    @FelixMboma-o5v День тому

    Bravo braz 😂

  • @CarolineLiabunya-j8k
    @CarolineLiabunya-j8k День тому

    Mchewa aliyense ndi wa mcp?

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому

    Izi zikhoza kukhala zoona chifukwa mcp ndichipan chotembeleledwa wina aliyese amane angachitenge chizamuvuta kayendesedwe khulupililani

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    ngat,sim,maikonda,mcp,ife,timaikonda,chakwela,sakuchoka

  • @oswardzenizeni1458
    @oswardzenizeni1458 День тому +1

    Chakwera tula pansi udindo kodi sukuwona kuti mizimu ya athu yakwiya

  • @MirriamTongole
    @MirriamTongole День тому

    Machende ako iwe

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 День тому +1

    Zabodza izi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    kwanu,ndikuti,iweyo,anzako,akulima,fodya,iwe,, ., ungonyela kuntumboko

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    oloutati,chakwela,amanyela,pogona,pake,ifeyo , tizamvotelabe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    ngati,sukonda,mcp,usanamizile,anzako,umaona,ngati,chipani,cha,,mcp,ndichokhaulitsa,ngat,idakhaulitsila,bpp,kuisandutsa,yotsutsa,udf

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому

    Mcp ingothesedwa basi mizimu ya anthu kumanda ikulila inu

  • @GeorgeSathula
    @GeorgeSathula День тому +1

    Zoonadi suukunama achoke chakwera

  • @JimmyWChibwe
    @JimmyWChibwe День тому +1

    Unya ukhaula

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 21 годину тому

    palibe,wa,, mcp, angalankhule,, zakuntumbo,, ngati,,zimenezo,,ndiwe, otsutsa,, asawapake

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho День тому

    @ 100%

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i День тому

    Pangani zomwezo bigg cikangawa azipita ku kasiya azikayendesa mpingo osati dziko chifukwa dzikoli cikangawa yamukulira

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu День тому

    Cadet usatisokosere

  • @GeorgeSathula
    @GeorgeSathula День тому

    So now

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani День тому +2

    Confused generation abambo awa mmm namzimkambe weni weni

  • @PaulMhango-x3q
    @PaulMhango-x3q День тому

    Mutu wako unajama kalekale sumadziwaso chimene umapanga you need to visit Zomba

    • @afritouch4660
      @afritouch4660 День тому

      Kansete iwe ukagwere uko. Nyau zalepheradi apa.! 😢

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv День тому

    Komatu😂

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje День тому

    Kukumana NDI chakwera 2025 ife takonda olephera yemweyo mpaka 2030

  • @VeraVermaak
    @VeraVermaak День тому +1

    Cadet uvutika

  • @GoldenChirwa-iq3dm
    @GoldenChirwa-iq3dm День тому

    A Isaiah musaononge zinalanu kamba ka ndalama.maboza otele ndamene amayambisa nkhondo sizikhateke kuti mamembers 3/4 angakuimbileni foni yotele. Chilungamo chizakususani chokha.

  • @alfredpatel3984
    @alfredpatel3984 День тому

    Koma dzikoli mhuuuu. Uyu akuti Sunganimoyoyu anali.mmodzi mwa anthu omwe wakhala akukonza ziwembu za MCP
    Sizobisa ndipo Sunganimoyo mwiniwake akudziwa zomwe ndukambazi. The guy was useless for MCP.
    Inu zoti Chakwera alibe nzeru zoyendesela dziko simumadziwa?? Chakwera wazunza aMalawi kuphatikiza achewa eniake.
    Lero mukudziwa zinthu mochedwa. AMalawi Nsanje to Chitipa amadziwa kuti Chakwera sanayenele kukhala mtsogoleri wa dziko.
    Chakwera ndiopindeleza, odzikonda komanso osadziwa zopanga.
    Achewa anzeru sangasankhe Chakwera pomwe nchachidzindikile kuti alibe nzeru za umunthu olamula.
    Achewa dzukani. Chakwera wakuchititsani manyazi. Mchewa uyu Chakwera wakuyalutsani kuti mwainu mulibe nzeru posankha Chakwera munthu olephela.
    Chakwera analephela kuyendesa mpingo ndiye akayendese dziko??
    Mchewa amane amajiya za Chakwera ndi mchewa opanda nzeru yemwe safunila dziko zabwino.
    Chakwera ndi mchewa osakonda dziko.