Kutitsimikizira kt chipani cha mcp ndi chachewa basi cz onse omwe watchulawo ndachewa kusonyeza kt wamtundu wina sangaimire mwachidure there z no democracy in mcp
Chipani si chachewa nanuso apa mumasowa zokamba simbi phiri siwandale president amasakha ku convention akanafuna akanamuchosa kumeneko amasakha amene Ali ndi kuthekera palibe Cha nzeru apa anthu amaziwa chimene azachita musaganize kuti anthu azavota Cha zimene mukuyakhula pa social media
Mau onunkhawo ife ai koma mau enieni adachitika kale ku concession kuja. Amene akutumawo adalikuti panthawi Imene ija. Mwagenda katauluka Dikirani 2030
Ndakukonda aise that's true patriotism
Mulungu akudaliseni achimwene mupitilize mulungu akutetezani amen
😂😂😂 bravo!!!! Kunena mosapyatera. More fire.
Long live odala for speaking the very true may God protect you
😂😂
Zonadi munenazona wakulu iwende Malawi weniweni💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Sitikufunaso MCP Kumalawi kuno yatizuza kwakwana
True story ❤ brother
Respect warrior!...your naked opinion
Angomutulusamo muchipani chawo Cha MCP okuphayo😂😂
Man onetsani nkhope YONSE yanu osati kudula nkhope mungamenyetse munthu oti sizikumukhudza
Akupha dziko ndi asilikari ndi apolice 😢😢😢
Simukunama brother
Live comrade Isaiah
Mwayamba kugwesana nokha nokha😂😂😂😂 angobwela a dpp kugweselatu
Ndipo kuchoka chakwela ine ndizavotela mcp
MCP asayellekese nkubwelella boma lisamallry llawononga mallawi nkwambilli 👊👊👊👊🇿🇦🇲🇼
Ndipo iwe nde wayakhula moveka bwino kwambili
Mumakonda Dziko lanu bro
Ngati zilichoncho zizakhala bwino liti pazaka zonsezi Malawi akadali chimozimozi
Amayenera kumuchosa Ku Mkumano womwe unachitika wa Chipanichi ( CONVENTION ) Koma MCP yomweyo inabvomereza Kuti iyeyo akayimirebe.
Sinthani Mtsogoleri mwina zikuyenderani a MCP Koma mukakakamira wokuphayo mugwa nayoooo.
Ndipo sadzaupeza Mtendere Chakwera anaphera njiru kufuna Udindo.
CHAKWERA Chikangawa serial killer.
Kkkkkk koma akulu awa asinthaso zochita
Lero wayakhula zazeru kwambiri ndipo ukapitiliza izi ukhala ndi athu ambili okukonda
Ukunena chilungamo, Chakwera sali fit kukhala President wa dziko. Osavutika naye poti akuchoka kale next year.
ukunaama, sindiwe mchewa, , uzipusitsa, enawo, zinamiza, agulug
Kutitsimikizira kt chipani cha mcp ndi chachewa basi cz onse omwe watchulawo ndachewa kusonyeza kt wamtundu wina sangaimire mwachidure there z no democracy in mcp
Km zenzen kuika pampando anthu osauka szabwno cz amakhala kt Al nd njla pandalama
Bwana, mwalankhula chilungamo.
Akulu akuluwo,kukambilana ndi awa?😊😊😊😊,mtima subvala,sadza.kodi,chipani chawo chija chathela kuti? MCP ngati sichidathepo ngati makatani'chaka,chake ndi chamawa.akulankhulawa,chamba chimawapweteka,koma ali ndi kazi,amenewa?ndi ochititsa manyazi kwambili ngati chakwela.
Tayesani kuchotsa Chakwera muwone mmene anthu tidzavotere MCP, please kakambiraneni zimenezo mcp idazwina fair fair.
Atule pansi udindo mr chikangawa
MCP is not Chewa party. Was Orton Chirwa from the central region?
Vaya uko iwe kape usatibowe ukunyoza mcp chifukwa adakuthamangitsa ndi zibakera 😂.
Chakwera chinangokula mutu nzeru chilibe chinangopha munthu wanzeru chilima mmalo moti chife ichocho
Chichoseni mchipani chikangawa munthu opanda pake
Chipani si chachewa nanuso apa mumasowa zokamba simbi phiri siwandale president amasakha ku convention akanafuna akanamuchosa kumeneko amasakha amene Ali ndi kuthekera palibe Cha nzeru apa anthu amaziwa chimene azachita musaganize kuti anthu azavota Cha zimene mukuyakhula pa social media
Koma Zinthu zimasinthadi eti...nkuru mmene amathera mawu kunyodza APM kumayamikira chakwera ndi chipani Cha mcp
😂😂😂😂😂 athu mukufuna kuntchuka
Akutchuka pachulungamo
@DalitsoMatope aa ase chakwera or umuze chilungamo samava
Mutu ngati phwala la ngamira Iwe ayiseye...
ukamat, mcp yatizuza, amadzakukoka, machende,kunyumba, kunyumba kwako
Sitikuwafunadi dala tasiya kulima chifukwa cha usogoleri wa chakwerayu eeeesh guys Chi chewa ndi chilankhulidwe si vote ayi muziwona ulendo wuno
Siyeni napoleon dzombe guys musachimwise munthu muzilimban nd chakwela kapena simbiyo
Convention ya MCP inachitika, ndiye inuyo mukuti kubwerenso convention ya chikhalidwe cha chichewa? Kodi MCP paja ndi tribal party eti?
Apo mwene takanukana ndi inuyo achakwera ndi APM ndiye Bola APM Ali BHO kwambiri timapanga geni yatu bwino zedi osati manyakawa ayi tiyeni kaye tibwezere kaye adad kwinako tikusaka munthu wina posogolopo mwene
Sunganimoyo ukufunika ku Mental mankgwala aja amazunguza mutu and iweyo unapengaaa mvula yagwa tayesani kudzala Mbatata kupewa kuzelezeka ngati ukuuuuu
Athu enanu nzeru mulibe khani SI DPP or MCP koma khani ndi president yemwe angapange control economy osati zomangogwetsa kwacha ngati mwaledzela
Kod uyunxo ndiye uti???
Ndavetsatu,kuti ngakhale makoswe atachuluka bwanji sangamasuke nkufika posankha mphaka kuti awatsogolele njira ,chifukwa m'modzim'modzi adzathatha phsyiitii
Amutuma adpp ofoila koma pitalryu akukupusitsani kusauka ndiufiti
Machendiyako iweyo sukuziwa kut ziko lasokonekela chifukwa cha chakwera angokweza zinthu dairy
Kodi ndi Malawi congress part kapena Malawi congress party?
😂😂😂😂😂
achewa ndi zitsiru za anthu kuphatikiza chitsiru chakwera
Mcp idilitidwe ithrtsedwe basi
Nanga mumausakhilanji za ziiii
kubwela koma kumeneko
Man kayambeni kulima mbatata ndaona mumfuna udindo
Now your talking brother!!
Eni ake amcp ndi amenewa osati mchimwendoh
Kulephera ndiye kuti Dala
Tathokodza achewa poyiona game chakwera ndi odzikonda
Iwe sungamoyo ukunenadi chilungamo chakwera kuno ku Dowa sitikumufuna pachilungamo
Zoona
Fundo zabwino
Achewa tapangani mademo pilizi(please) ombolani dziko
Iweyo ndi galu kwabasi pamodzi ndi mcp yakoyo
Kodi malamulo amatichiani titati tisithe?
Nthawi Ina yake mudabwela mukulila ine ndimakutsatilan kwambili kma ndidakumvelani chiso kmabe ndathokoza kut mmatsatila amalawi ambili ndiye akatsutsa zimenezo asiyen akalila yamsatsi asemelen iwafotela mmanja chikatuluka apapa sichidzalowaso
Wadya zamunthu uyu kkkkkk
Iwe nd in ndan?
Ndi Jetu
Isn't you people go for convention?
HE Chakwera is great among Chewa leaders support him
Machimo mcp kkkkkkkkkk
Mau onunkhawo ife ai koma mau enieni adachitika kale ku concession kuja.
Amene akutumawo adalikuti panthawi Imene ija.
Mwagenda katauluka
Dikirani 2030
IWEYO WAYANKHULA BWINO KOMA CHOTI UDZIWE MCP SIKULOLEDWANSO MDZIKO MUNO MCP PAMENE IKUPITA KOKATHA BASI TIKUFAFANIZA SIDZAPEZEKANSO KUMALAWI AMENE AZIZAYAMBIRA KUIMIRA MCP KU MALAWI AKUDZATHAMANGITSIDWA
Mcp mphwanga sikufunika mu dziko lamalawi or mungasinthe munthu kulibe kulibe