Inu ndithudi mumatiimilira without fear or favour. Boma ili ladzadza ndi zitsiru monga Mr Nkhumba Chimwendo ndi Mr Galu wachabe chabe Kumkuyu. Pulezidenti Chakwera nayenso ndi chitsiru cheni cheni. Boma, Paliyamenti plus Judishare kuli corruption ya nyooooooooooo. Zomwe zikuyenda mdziko muno ndi Katangale ndi kukwera kwa zinthu basi.
Pokhapo poti history is the best teacher don't ever forget coz pamandiwaza❤❤❤
My brother wa kwiya kkkkk chimwendo abuyako 😂😂😂❤❤❤ I love you big brother
Katudu waboma wa bakili muluzi tv big up
Ndpo live
Pangolin wathu uyu❤❤❤❤❤❤
History is the best teacher
Ife kuno ku Ntcheu Central tikuti Mulungu Odziwa kuteteza apitilize kuteteza team yonse ya BMTV🙏
Welcome back 🎉 Koma musamasowe
chimwendo ndi galu mbava yakupaa😢😢that is true really
Fadah lero mwafika ndi mkwiyotu kkkkkk
The biggest fighter of all time
History is the best teacher Ngakhare chikangawa akuziwa izi
Bakili muluzi walero mood yake ndiyachabe kwambili,ndi okwiya ndipo kumuyandikila atha kuthyola khosi la nkhumba😂😂
History is the best teacher... loud and clear frm Pietermaritzburg,S.A
Watching with Moses Kumkuyu and Zikhale Kamajekete 🧥🧥🧥 ng'oma 😂😂😂
😢😢😢😢😢😢😢😢😢
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Apa nde amva ntidziitu😂😂
Ur best and true tv than chimwendo banda
Bakili muluzi tv ur the greatest ever
Number one tv in malawi that politicians listen to including Chimwendo himself.God protect you from harm bigman
Welcome back my brother ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Bakili muludzi tv iweyo mulungu akhale nanu ❤❤❤❤ tetezan malawi wathu please 🙏 😢 😀
Inu ndati history is the best teacher
Abwana kwiyani Zeni Zeni ifenso tatopa nawo ng,onazi
Respect to my king God bless you ❤❤❤❤❤❤
Brother we love you you always give us the true story
Best TV ever❤
History is a best teacher 💪💪💪
U are best bro kp update us
History is the best teacher ❤
😂😂😂😂 chimwendo uli madz unyamabindithu eshiii
Bravo bakili mulunzi tv God bless you
History is the best teacher Bakili muluzi tv its my best choice there no secret in the world
Wakwiyatu lero legend! You are number 1
Big man 💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯
May God be with you Bakili TV,🙏🙏🙏🙏
Watching from Johannesburg in south Africa we support you change is coming soon
Chakwera akutitora tizakumana 2025 muzamangidwa
Ndipo iwe broh mulungu akuthangatileni nthawi zonse
Your most welcome big man!! Keep on updating us !!
Zikomo muthu wakulu tinakusowan welcome back 🔙
Tikufuna mademo aziko lonse but opposition yathu aah they are not doing enough anthufe tikuvutika kwambiri
team BAKILI muliz tv woyeeee.
ma speech a political officials it gives Sense that amavelaso BM tv ndipo TV ndiyomweyi basi😂😂😂😂😂
Komadi zoona khumba iyi chimwendo Banda akutenga dziko la Malawi Ngati la abwiya e tiona 2025 Boma likangosintha owe o khumba iwe udzalafera Ku ndende
Nkhaniya mozambipwe Royal woyimira wotsutsa amupa rerotinari kumariro rero
Kkkkk chimwendo akumvela nawo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Akumveladi. Ndipo B Muluzi Tv amayitsata bwino bwino. Even Kumkuyu nayenso amayimvela
Our trusted TV, we love you so much
All the best Bakili Muluzi TV 🎉🎉
Mr khumba wazimvera yekha😂😂😂😂😂😂 iyi ndiye tv osati mbc
Munasowa boss man
Ulemu wanu bwana. 100% true Chakwera anaphadi Chilima. Ndipo pitirizani kuwaturutsira poyera.Akuona ngati ife dzitsiru.
Ife timakhulupilira inu King wathu
Thanks my brother more love from machinga ❤
Bakili muluzi tv my best tv 📺
Mmmmm good work biggy umakwanira
Bakili TV number one ❤
Best TV in malawi 🔥🔥🔥🔥
Bakili muluzi tv is the best
The best TV 📺 history is the best tc
More years to this best tv
History is the best teacher all the way
😂😂😂😂 Inadzadza yambwiyako😂😂😂😂 I love bakili muluzi TV wth chilungamo chake
Mumakwana boss ❤❤❤❤❤
Best of the best TV ❤
Chitchola kukamwa Ngati kuthako😂😂😂😂😂😂
Mulungu akudalitseni a bakili muluzi tv
Long live BML tv
Bakili Muluzi fans let's gather here 💯 💥
Ulemu ukhale pa bakili muluzi tv
ALWAYS GOD BE WITH YOU ALL THE TIME
Number one inuyo big man
Munasowa fada ingaluleni😂😂😂
Bakili muluzi TV ❤❤❤
bakiri muluzi TV it is the my best TV
More fireeeee
Chimwendo yondiletsa kumvera Bakili muluzi TV
Peza khan ina😂😂
I think iyi yakupezanso
Ndpo live
Apatu abigy lerolino mwayiphulisatu
Well done wa bakili tv
Ndiwe namalamba basi bm TV Wal llah☝️
Inu ndithudi mumatiimilira without fear or favour. Boma ili ladzadza ndi zitsiru monga Mr Nkhumba Chimwendo ndi Mr Galu wachabe chabe Kumkuyu. Pulezidenti Chakwera nayenso ndi chitsiru cheni cheni. Boma, Paliyamenti plus Judishare kuli corruption ya nyooooooooooo. Zomwe zikuyenda mdziko muno ndi Katangale ndi kukwera kwa zinthu basi.
numbar one iweyo mwana wa amayi ukhalise
A MCP ena akuyenera kuphedwa physically, it's not good kuti muphe chilima ndi ena for the sake of presidency.
Iwe chonde brother pitiliza kutimenyela khondoyi timadalila chilungamo chako ndithu.
Chonena ndilibe Bakili siwolimbana naye.......wawapanikidzatu mcp azipani ena muphudzile ku malawi zibwana ayi mukuwona mcp yapanika kusowa choyakha....
Best TV in Malawi
Munasowa brother ❤
We love you Bakili Muluzi Tv ❤❤❤❤
Umakwana b m tv auze amana ameney
Bmtv ndi 1 ife timavera zimenezi sungatiletse iwe kachimutu komanso iwe kamajekete. Kodi iwe kunkuyu wittika unamupheranji 😢😢😢😢😢
Big man kulakhula😊
Mawulemu anu king 🤴
Bakili muluzi tv 💯💯💯❤❤❤
Best TV
Sitizasiya kuvera bakiri muruzi tv paka 2025 chakwera achoke
You are number one
Fire
My best TV❤❤
Bweresani chilungamo pa khani ya chilima apumbwa inu
Ulemu wanu boss
Big Up brother ❤❤
Uyuyu ndikatundu😂😂
Bakili tv stay safe,we love 💕 you 💝
Tiyuzeni zoyona❤❤❤
Nthawi izakwana Malawi 🇲🇼 azakwiya ndipo sitizavasa zamunthu cz timavutika ndifeyo pamane chakwela chimwendo Kaya nkukuyu savutika nawo. amalawi nthawi zina tizizimvera chisoni zoona munthu wanzeru ungalandise ) kapena kugulisa ufulu wako ndi k2000 kwazaka 5 no lets be serious when we come to make decisions
Home of history Bakili Muluzi tv ❤❤❤❤❤😊