Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
What a lovely song is this , grace defeat our enemies , far away in mud we are coming from, ena namondwe, ena mu madzi , ena mumoto
You are a great worshiper mama, Mulungu apitilize kukugwirisani ntchito
Who else sees grace Chinga in daughter of zion's songs?Nyimbo zoti ukamvera kumanva relief.......God bless you my favourite musician.
Mam,God bless you mumanditsitsimusa with your songs🎉🎉🎉🎉🎉
Thank you for your message 🙏🙏🙏
Eeee muliphamvu mu nyimba zamai awa kwambiri mumatitsisimusa kwambiri 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌💯
Amen and amen mama 🎉🎉Mulungu amakhala nafe nthawi zonse ❤❤
Powerful song
Mumatilisendeza pafupi ndi Mulungu mama Ambuye akudalitseni Amen Amen
This woman bless me so much
Hallelujah 🙏
Amen mwainu timadalisika
Na ine nyimbo zanu mom zimandidalitsa ambuye akuze malire anu ndithu❤❤❤
Mulungu atitsogolera God of power I worship u mumatitsogolera without u nothing can not work , thank u Mami for this song
Ambuye akudalitseni abusa. Mutipangileso nyimbo yomweyo koma ikhale more than 30 minutes ngati kukhatheke.
Powerful song ndipo ndimadalitsika nazo nyimbo zanu mamie
Matidalitsa ndi nyimbo zanu mami
Powerful nice song
❤❤❤❤
Mulungu apatsa nyimbo Monsey mmavuto
Amen mama
Amen 🙏
Amen ❤
Amen
Ameeeen woman of God
Nyimbo ilibwino kwambiri ndipo mulungu apitilize kukupatsani nyimbo zatathauzo Ngati Zimenezi mama
Tikapsa chifukwa Cha kusava kwathu ,koma inu Mami mutizuzula komaso kutiphuzitsa,mulungu akuze malile anu
Tikudalitsika ndinthu❤
🙏🙏🙏
Powerful
Amen And Amen
0😅😅😅😅😅😅😅😅
Tathokoza mumatidaritsa
Taponyani ma lyrics
Zamphamvu