Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Ndekut kuthandiza aziyamba kukaona athu akamadya chiteze chakwela simuthu wabwino
Admark kulichimanga??
Akudikira cha Ukraine. Anthu ndiopusa kuvomera kumawauza kuti akudziwa zanjala ngati wanva kumene. Pamene anadziwa kalekale mmalo mowauza kuti chimanga ndabwera nacho
Kuno ku dedza kwakafele china chita kudzadza adzatengek kt tikagulitse china
Zipani zose ndi amalawi msamangotukwana munthu futo latigwela ndi zipani zose zitengepo gawo mkuwona busshili satukwana munthu amangothandiza basi
Achihana nsabwe yoyenda yenda yinakumana ndi chala inuyo simkuufuna asog tamachitani chitukuko chokwatila azimayi ambiri mbiri mkwanisatu 10 kkkkkk
ine ndikungofuna kuthokoza mhomviwa kaya koma dzina lake akuti given or gift she did interview with brian banda nkoona achita manyazi for chakudya and chitukuko
Mbava kukana ubusa kufuna kutibela
Kugwa mmanja mwa Yehova nkowopsa mwina sadziwa, agalatiya wataya chipangano
Lies anthu akudya chiteze chakwera angodya money
Lazalo mache.....ake
Chakwera koma amadziwa kunama eeeeeh super liar.