Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Masha Allah
Eh nyimbo ikuvuta kuimva iyi. Poti timamva kuti akuti ma nashid oimbira ng'omawa "Mtumiki analoleza chifukwa ndi njira yopelekera ulaliki", choncho ulalikiwo ngati sukumveka omvera timayenera kufunsa:1. Chemina (ndikhulupilira ndi Aamina bint Wahab Mai a Mtumiki) akutchulidwa kuti atusalire ... anapanga da'wah mChisilamu?2. Wamaa umiru .... Ya Rabbanaa ... Wamaa umiru Muhammad ... Wamaa umiru Allah. Mau awa sindikumvapo malinga ndi nyimboyi (وما أمروا إلا ليعبدوا الله)
That's good, maa shaa Allah
Good gospel
Nambotu nimwana kutaganya
Nice song
Masha Allah
Eh nyimbo ikuvuta kuimva iyi. Poti timamva kuti akuti ma nashid oimbira ng'omawa "Mtumiki analoleza chifukwa ndi njira yopelekera ulaliki", choncho ulalikiwo ngati sukumveka omvera timayenera kufunsa:
1. Chemina (ndikhulupilira ndi Aamina bint Wahab Mai a Mtumiki) akutchulidwa kuti atusalire ... anapanga da'wah mChisilamu?
2. Wamaa umiru .... Ya Rabbanaa ... Wamaa umiru Muhammad ... Wamaa umiru Allah. Mau awa sindikumvapo malinga ndi nyimboyi
(وما أمروا إلا ليعبدوا الله)
That's good, maa shaa Allah
Good gospel
Nambotu nimwana kutaganya
Nice song