Highlights: Dedza Dynamos 1-1 FCB Nyasa Big Bullets

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 7

  • @StarJmond
    @StarJmond 9 місяців тому

    Talk to our goalKeeper asamakhale ndi pressure like that,...and i hope he learned a lesson from that mistake.

  • @mpha2653
    @mpha2653 9 місяців тому +1

    Ma goalkeeper trainer athu they're not doing well at all,, saphunzisa anthu positioning bwanji ma goalkeepers athu nthawi zambiri amachinyidwa coz of kuchoka pagolo nanga akufuna aputche mpira akugwa kuchedwaso kudzuka
    Ma reaction amavuta amakhala slow paziganizo ineyo i don't think Nyasulu will help us in with that problem coz with this goal he is below par yes amagwira ma penalty koma ngati akufuna improvement akhale odekha komaso osunga position

    • @solomonlungu2549
      @solomonlungu2549 9 місяців тому

      Exactly last season we had similar issues seems Vin ntchito ikumukanika ku senior team uku

    • @sungananichuzu9264
      @sungananichuzu9264 9 місяців тому

      Swadick abwerere

  • @olubocharle4367
    @olubocharle4367 9 місяців тому

    Kuyamba mpira kwa mtundu wanji kumeneko a Dedza? Kungofikira kupereka kwa adani

  • @WalikoMsutu
    @WalikoMsutu 9 місяців тому

    Komatu maulewa timawapopa nkhani ndikut ali ndindalama koma si ampila

  • @Jiahmk
    @Jiahmk 9 місяців тому

    Poor goalkeeping