DR KABAMBE ATULUKA DPP | NKHANI MADZULO |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 сер 2024

КОМЕНТАРІ • 45

  • @chisomokawotcha1766
    @chisomokawotcha1766 Місяць тому +6

    Ayi ndi pamene mudzadziwe kuti ndale ndi zovuta kuti amusankhe kabambe running mate ku dpp bdi zovuta cause kueme kuja kuli mikhala kale nde apite ku utm cholinga akazapanga alliance kabambe azamutwnga ngati running mate wake fro m utm nde ndale zimenezo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Місяць тому +5

    Akabambe olo atachoka dpp iwinabe

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d Місяць тому

      Kabambe alibe chikoka alingati Mangacha sete zawo onse

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Місяць тому +2

    Chipani cha dpp chilibe vuto.zipani zambiri zilibe vuto koma vuto ndi anthu wofuna mawudindo sakufuna kulolelana kuti wina alamulire ndiye anthu wotuluka zipani musawalole azipani zina kulowa muzipani zanu ndiwomweo amazesa zisokonezo. Pali wina wayakhula kuti mcp yinawina zisakho ameneyo akunama tonse alliance ndiyimene yinawina. Koma chidukwa chaumbuli ndi kuzikonda ndichifukwa mcp yikuona ngati inawina. Kopanda alliance bwezi mcp ili kunja.

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Місяць тому +1

    Ku UTM kulibe munthu angakhale president ndiye akabambe awona kuti mwina ndi mwayi wake

  • @jomochirwa
    @jomochirwa Місяць тому +3

    Adalitso kupupulumatu uku.mwina amayembekezela kuti utm ichoke kaye ku tonse.

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7u Місяць тому +2

    Zoonadi kupupulumadi akuona ngati akatenga u prezidet koma kabambe zachisoni

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere Місяць тому +1

    Dyera kabambe koma akuluakulu anthu andale dyera kuteroku waona kuti ku DPP mpando wautsogoleri saupeza ndeapapa mpungwepungwe omwe uli Ku utm ndi Dr Usi iye watengerapo mwai ofuna kukatenga utsogoleri. Koma chipani cha DPP sikuti chipangidwa affect chifukwa kabambe tsogolo lake la ndale silinayambe kuoneka

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Місяць тому

    Achina khwangwala kadyera😊😊😊

  • @user-kc7sd3te3d
    @user-kc7sd3te3d Місяць тому

    Musiyeni kabambe apite but still more DPP yiwinabe whether you like it or not

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s Місяць тому +1

    Kabambe akuthamangira ku UTM akufunako akakhale President sakudziwa kuti President wa dziko lino ndi Mutharika

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Місяць тому

      Aaaaa iwe usavutike ndi ankhalamba yakoyo kagwere

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Місяць тому

    Iweyo Ndiye wasalira mu tonse alayansi, Nonse amene mwasala mu tonse alayansi musama lire,muphesanso a Malawi ena

  • @user-pk6vq1cr1b
    @user-pk6vq1cr1b Місяць тому

    Amenewo ndima setting andale muzazindikila pasogolo

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Місяць тому

    Akabambe akufuna upulesidenti ku UTM

  • @AndrewSimakweli
    @AndrewSimakweli Місяць тому +1

    Boma lilibe masompsenya

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Anthu akutuluka mwa alliance chifukwa chakwela akutenga ngati mpandowu anawupeza mwa iye yekha 2 alliance sakupeza mmphindu la alliance chakwela wangopanila yenkha zabwino zonse ndichifukwa UTM yatuluka yawona kuti wina wake wa phangila zose

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Місяць тому

    Munapha mesa Chilima nde a UTM atuluka musanamalize koma akusiyilani Kamanganya ka yudas😅

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому

    Ife a UTM tatuluka chifukwa Chakwera anapha Chilima

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Місяць тому +1

    Phuma koma silabwino.

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Місяць тому

    Mbava zokha zokha.

  • @MagaLassi-tg7lj
    @MagaLassi-tg7lj Місяць тому

    Asatiphe mutu uyoyo akapume Ife nganga APM

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому +1

    MCP ndi Chakwela ndi yakupha

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому

    Kabambe alibe chikoka

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika Місяць тому

    Akanakhara chaponda tikanadandaula km munthu oti sungatipindulire ulibenso ntchito tikangokusunga monga osowa chochita

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj Місяць тому

    Kod anali a dpp sindimaziwa ine

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb Місяць тому

    Musiyeni atuluke akuuza anthu chifukwa chiyani??

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Місяць тому

    Mumasuleni Nkasa

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Місяць тому

    Achoke basi siofunikila

  • @PeterKasakula
    @PeterKasakula Місяць тому

    Nkhalamba ija akuthawa kambakokakamila udindo chipan chachibanja ngatiufumu😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Місяць тому +1

    DPP yatha bas😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 Місяць тому

    Amutalika.amutuma kabambe kuti apite ku utm

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x Місяць тому

    Awa a umozi ndi achitsilu .mcp sinatengepo boma

  • @Yanjanani
    @Yanjanani Місяць тому

    Oipa athawa yekha popanda omuthamangitsa

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt Місяць тому

    Zabhobho

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Місяць тому

    Farewell

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Місяць тому +1

    Asiyeni akabambe analindicholinga

  • @user-xu9rh1lm8o
    @user-xu9rh1lm8o Місяць тому

    Kodi anali ndi udindo wanji ku Dpp

  • @user-kc7sd3te3d
    @user-kc7sd3te3d Місяць тому

    Musiyeni kabambe apite but still more DPP yiwinabe whether you like it or not

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Anthu akutuluka mwa alliance chifukwa chakwela akutenga ngati mpandowu anawupeza mwa iye yekha 2 alliance sakupeza mmphindu la alliance chakwela wangopanila yenkha zabwino zonse ndichifukwa UTM yatuluka yawona kuti wina wake wa phangila zose

  • @user-kc7sd3te3d
    @user-kc7sd3te3d Місяць тому

    Musiyeni kabambe apite but still more DPP yiwinabe whether you like it or not

  • @user-kc7sd3te3d
    @user-kc7sd3te3d Місяць тому

    Musiyeni kabambe apite but still more DPP yiwinabe whether you like it or not