Zomwe ayankhula a Chakwera polandira report la ndege

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 35

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 7 годин тому +7

    Mulungu akuona Inu achakwera olo muli akwathu kma ine simakhala mbali yopanda chilungamo

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 6 годин тому +3

    Ambuye mukanadzukatu Koma😭😭😭😭, anthuwatu zoti inu kumwambako muliko ayiwala, ndamulirira Malawi wanga 💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔, may you continue rest well our beloved ones 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @HandEllah
    @HandEllah 7 годин тому +5

    Ai Zikomo Mulungu azatiuza zoona Zake

  • @georgekamanyuzi108
    @georgekamanyuzi108 7 годин тому +5

    Useless president ever

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x 7 годин тому +2

    kulandila report Ngati wanzeru , Koma chilungamo Chake akuchidziwa kare , ayi zikomo kwambiri mulungu alipo kumwamba akulangani aliyense pa yekha payekha, judgement day will come one day is one day , kusogoza anzanu Ngati Kuti adakuuzani Kuti moyo atopa nawo , please god punish these fools ,

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 7 годин тому +3

    Kumalawi guys kulibeko president ichinditsilukobasi akumakambazosiyana

  • @TimothyvascoVasco-j6d
    @TimothyvascoVasco-j6d 8 годин тому +3

    Chakwela its useless plznt

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 6 годин тому +1

    Tangovomelezan abale inu mudya mudya bas zidikililan zilango zanu bas

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 7 годин тому +1

    Ndipo chilombo chotchedwa chakwela ichi ndichimuthu choipa m,tima ndipo mulungu sachedwa safulumila koma na iweyo chakwela mulungu afulumile ndithu inu muthu kumenyelani khondo lelo ndiwe osayamika koma m,malo momweza ulemu ndikumupha muthu uli ndi tsoka lalikulu kwambili ndipo suzaupeza m, tendele plesdent oipa ngati manyi

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 7 годин тому +1

    Koma a Kawale Koma a Kawale ndi ciani makamaka. Ndalama kapena chilungamo??? Munthu was Mulungu kudzinyadzitsa choncho!!!! Chitani manyadzi ngatidi mumakhulupilira Chauta inu. Aaaaaaaaah a Kawale ndilibe mau ine

  • @HumphreysBanda-e7g
    @HumphreysBanda-e7g 7 годин тому +1

    Azibusa okhutitsa MBA zao osati kutumikira mulungu Bolan mukudziwa Kuti masiku otsiliza zobisika zidzaulilika palibe chobisika pansi pa thbambo

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 7 годин тому +1

    Koma chakwela murungu akuyang,anisise mafuno athu ndiwoti iweso upeze soka

  • @BhoyoMamush
    @BhoyoMamush 7 годин тому +1

    Kumwamba kuli mulungu will now the truth one day

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood260 7 годин тому +1

    Umatha kumazitenga solo koma lomaliza limafika lokha

  • @RabbeccaChitimbe
    @RabbeccaChitimbe 7 годин тому +1

    Kuli yawe kumwamba akudziwa chilichonse chakwera usamare

  • @erickkhoko
    @erickkhoko 33 хвилини тому

    Akaweluza yekha... ife coyankhula chagweru mkati... ndipo satana alipodi kunja kuno.

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 7 годин тому +1

    Achakwera apa pokha munapangisa kt anthu masiku ano assma khurupirire azibusa km murungu basi or kutaza pezeka mtumiki weni weni kuzakhara kovuta kukhurupirira

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 3 години тому

    Jeremiah 22:17
    Musaphe munthu apanda chifukwa, uthenga uwu upite kwa chakwera ndi duna zanu zose, Mulungu akukantheni, Mulungu amaziwa zose zimene muchita ndi anthu 9 aja munampha, musanamize anthu chifukwa Mulungu anakuchasani kale papando

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 години тому

    Report loti unalandira kare kare nde apa ukut chan machende ako

  • @JackAmoss-zg2zw
    @JackAmoss-zg2zw 2 години тому

    God is watching everything

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 7 годин тому +1

    Anamupha yekha kuti Aimenso 2025, manyazi alibe chakwela, kulimbana ndichilima konse kuja kumalimba ntima kuti uimanso 2025 ufiti or misala?

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 3 години тому

      Ndipo zodabwitsa kwambiri, sindikuziwa kut chikumulimbitsa mtima ndichani. Komanso mene wazunzira amalawi mu ndie akufuna aimenso kut akazawina azatani nawo amalawi, kuwapha kapena???

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 5 годин тому

    The truth will come once you are out of power like the Mwanza case

  • @JaphetDevi
    @JaphetDevi 6 годин тому

    Yudas kaliyoti months oipa chakwela

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 6 годин тому

    Malawi is a drama on its own

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 7 годин тому

    I only feel very very sorry for the men of God who have resorted to be among the band wagon of cheating Malawians with the fake report. God have mercy on this issue.

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 5 годин тому

    Dzizungu ngati munthu wabwino
    Mfiti yachabechabe
    Ndisadzakuone ku Ntcheu kuno
    Galu

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda 7 годин тому

    Anthu oipa inu siku ndilimodzi muzaona nyenkhwe kunja kumada ndi kucha musazione kupambana pano

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 години тому

    Misonkho yathu yomweyo uziphera nayo anzako, ngat kut unachita invest?

  • @MaliGomani-z4k
    @MaliGomani-z4k 7 годин тому

    Unaphq zako galu iwe

  • @SteynMaduka
    @SteynMaduka 4 години тому

    Aziti English yopanda ntchitoyo

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x 7 годин тому

    Ndipo tizapanga inquiry mukazaluza , coz now your hiding the truth , Koma mudziwe Kuti " mwazi anthu Aja uzakuzunzani ndipo muzasowa mtendere pa moyo wanu, timaopa mulungu oti sitinamuonepo , inu muli busy kupha anzanu Ngati Kuti sadafune kukhala ndi moyo, report la bodza ife ayi even ananfedwa sangalandile report lopusalo, basi mutakhala pansi mudaganiza zotiuza manyi a report Ngati amenewa? kkkkkk mulungu azakulangani ndipo tikuona kuchedwa 2025, Kuti muchoke tizizagwira m'modzi m'modzi , ndipo mudzaululana ndizakufinyani ma battery ndipomwe muzadziwe Kuti mudapanga za ugalu.