Wasowa zochita,,, adad anuwo musawanamize sadzalowaso m'boma, ngati ndi umphawi wakuvuta pitani kumunda mukalime mupeze zanu,,, km nkhalamba yanuyo ai,, kpn mukungofuna kuchulukitsa chiwerengero cha ma president omwalira ali pa mpando???? Nose adpp mboli zanu... Mufune musafune mcp ndi boma mpakana 2030 wooooooo
iyi ndiye nyimboya osati awa a Dan Lu 🙌🙌
Congratulations Mr akumenyelani bwino zidazo more 🔥
Nkhaniyi ndiyoona Adad woyeeeeeeeeee ❤ Dppiiiiiiiiiiiiii Booooomaaaa 🔥 munthu waphika nyimbo uyu🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Namakhwa ndi dolo❤❤❤ wayionera patali dpp 2025
Nkhani ndi iyiyi more 🔥 namakhwa
Mmmmm uyutu wabwerra basi nyimbo yokoma keep it up 💕
Koditu pano or mwana wa 3 years akumayimba avekere Dpp woyeee 😅😅😅😅😅😅
❤❤❤ ndipo zoona nyimbo koma izi ❤
Aku ndiye kuimba kuphulisa zenizeni❤❤❤❤❤❤❤❤
Chilichonse chokamba za ADADI..ndichabwino basi❤❤❤
nice song . osasitha namakhwa Abab bansi bpp woyee💃💃💃💃💃🔥🔥🔥💯💯💯🙏🙏🙏
Nkhani yabwino kwambiri Adadi woyeeee❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Za NYC zokha zokha adad woyeeeee my vote 🗳 ❤❤❤
Pamene dani lu wantha mulungu watipasa akamuna namamkhwa
Eshiii akulu awa apha nyimboi ili bomba❤❤❤❤❤
My vote namakwa ndili pambuyo pako
Mmmmm Mr Namakhwa simunathe ayii mulipo inu .
Nyimbo yabwno kwambri nice
Ndipo live 💙💙🥰🥰🥰
Ndipo mkulu ameneyu waganiza bwino poimba nyimbo imene ,chifukwa mulungu anakwiya mowalanda adadi boma mo fire namakwa
💯💥💥💥💥☝☝☝☝☝☝umakwana mn.kusowa kwabwino apa mwatikumbutsa nzambuyomu.kakkkkkkkk❤
Unalikuti neweso ❤
Zanyamata ozindikira izi dpp woyeeeee💙💙💙💙💙
Congratulations dasita namakwa ❤ countinue bring nice song good work ❤
Namakhwa u re namba 1 wow nice song adadi woyeeee ❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Nyimbo yabwino kwambiri namakwa woooye
Nyimbo iyi nditenga nayo matennda serious
We need more Mr ❤❤
Ilibwino kwambili osat zinazuja ilibho ❤❤❤❤
Yomweyo galu iwee ❤❤❤🎉😂
Nyimbo ya uthenga womveka komanso yovinika sizina zija zoti kumenya kugwetsa osadziwa kuti amugwetsera mkazi wake emwe
Good job my brother dus
Kwachema ndaikonda ❤❤❤
Umakwana kunyimba kwabh
Dad ndi dad basi🎉🎉🎉🎉
Size yabwino,nthawi yabwino Dustan woyeeee
Zili boo abwere munthalikabasi, osati izi zayamba kutenga fertilizer wa makuponi nkumayendanaye kupangira kampenizi ayi
Dustan namankwa mulungu azikudalisa pitiliza kutulusa nyimbo yina yokhudza peter isalekezele popa komado tiyimbileni nyimbo zokoma ife amalawi tikuvutika zed chikangawayu aaaaaaaa bola
😂😂😂😂😂 kwachematu
Ine kuno ku Mozambique yavuta namakhwa umatha DPP oyeeeeeeee 2025 boma
Dan Lu akulimbana ndi gulu😂😂😂
Tidyele mpukanga tambala busssss work apo mr
Nomber one uyuyu amatha
Chitedze chimayabwira muja😂😂😂😂😂wayipha Dpp woooooye namakhwa uku ndiye kuyimba uku... Ndikungovina ndili ku munda
Chilungamo ndichomwecho bas kulibe kuwavitela agaluwa mapeto ake atipha
Ndiyabwino kwambili kmaso ndiwe oganiza ndikusiyana ndikuyimbila chikangawa
Iyi nde nyimbo kaya ndaikonda
Yilibwino osati kusapota chikangawa cholinga dyera
Kkkkk umatha waimba bwino kwambiri❤❤
Hit mbambande
Nice one 🔥
Wasowa zochita,,, adad anuwo musawanamize sadzalowaso m'boma, ngati ndi umphawi wakuvuta pitani kumunda mukalime mupeze zanu,,, km nkhalamba yanuyo ai,, kpn mukungofuna kuchulukitsa chiwerengero cha ma president omwalira ali pa mpando???? Nose adpp mboli zanu... Mufune musafune mcp ndi boma mpakana 2030 wooooooo
Ndayikonda kwambili tiyivina kwambili tambala tidyele mpunga
Yomweyooooooooo!Namakhwa iweeeee!Adad omweyooooo!
Yokoma kuvela galimoto 😂😂😂😂
Dpp tengen namakwa chifukwa wakwanisa kukulimbiza tima
Kkkkkkk ndawelenga ma comment okwana15 opanda onyoza onse oyamikira ndiye ine ndindani DPP YOMWEYI BASI 2025
Adya nawo basi😂😂😂
Nice one 😮😮😮😮❤❤
Number one song
Amenewo ndi akamuna uziiwa kuyimba
Welcome back into music industries and let God be God He will fight for us...
Ija ya vakabu ija unapha😂
A chakwera anatitengera Dan lu chilima abweresaso Dunstan namakwa 😂😂😂
Namakhwa umakwana ❤
My vote 🗳 💜
abig mumakwana🎉🎉
Adadi woyeeee nice song
Uzatha iweyo namakhwa❤
Nyimbo mbambande
Good job my brother
CHIKANGAWA OUT 2025 ANAPHA CHILIMA CHIKWANJE NDATENGA KUPHERA TAMBALA KUDYERA MPUNGA BASI DPP WOYEEEE
Nice song brother
Takulandlaniso bro mwakwanilani iunuyo
It's very nice song i love this ❤❤❤
Waipha aise Namankhwa osati xinazi tivine 🤹🤹🤹🤹
Ichi chimayimilira Lomwe belt 😅😅😅😅
Ikuchita kunveka kut ndiyoyimbidwa nd oziwa
Adad woyoooooooo umakwana namakhwa
Sor chikangawayu ndi mbola dustan uli pa one
More fire ❤❤❤
Welcome dustan namakhwa more 💥💥💥
Adad omwewo woyeeee
Adad never again. Ndipo imban nyimboyi pofuna kuwadyera adadiwo. Koma ife president watsankho adatikonda kuno. Ndipo sitikumufunaso. Tambala 2030 wooooooo. Boma sitikusintha
Machende abambo ako iweyo...Ife tinavotera mcp kumaganiza Kuti inasintha Koma lero kupha anthu tikuona...... Tivotera DPP uomweija...
Thanks Namakhwa for supporting dpp
More fire guys chakwera machende Ake 😢
Wabwela ndi moto
Tili limodzi adad woyeee 2025 mpoto yose hoyeee Agnes's Nyalonje woyeeee
Ndayikonda kwambili muli mfumdo umachedwa kuti namakhwa
Machini 😂😂😂apa zilibwinotu wakwapulatu
Tambala mu mpunga kkkkkkk
Dustan iwe more❤❤❤
Zilibwino kwambiri oyimba oganiza uyu
Namakhwa 5 pin ilipo ugule mayunitsi
Kumenekoooooooooooooooo!!!!!!!!!!
Nyimbo yabwino
DPP woyeeeee❤❤❤❤❤❤
Fire 🔥🔥🔥🔥
Tambala mupunga, Namakhwa more fireeee
Kwachematu chakachino